Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live

Dziko la Yemen Lili pa Mavuto a Njala

Dziko la Yemen lapempha chithandizo kwa maiko akufuna kwabwino pamene likukumana ndi vuto la njala. Malipoti a wailesi ya BBC ati ngakhale dzikolo linali losauka ndi kale, nkhondo ya pachiweniweni...

View Article


Unduna Upempha Alimi Asagulitse Mbewu Mwachangu

Unduna wa zaulimi, ulimi wa m’thilira ndi chitukuko cha madzi wapempha alimi kuti ayambe kugulitsa mbewu zawo boma likakhazikitsa mitengo ya m’bewu-zo ya mbewuzo. M’modzi mwa akulu-akulu mu unduna-wu a...

View Article


Maternity Worldwide Ipereka Njinga 8 M’boma La Zomba

Bungwe la Maternity World Wide lapereka njinga za ambulance zokwana zisanu ndi zitatu 8 ku dera la gulupu Village Headman Kathebwe kudera la mfumu yaikulu Mwambo m’boma la Zomba. Bungweli lachita izi...

View Article

Papa Ayamikira Akuluakulu a Papal Foundation

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wayamikira akuluakulu omwe amayendetsa bungwe la Papal Foundation kaamba ka ntchito yomwe  akugwira. Papa wayamikira akulu-akulu-wa lero...

View Article

Msungwana Afa Atagundidwa ndi Galimoto M’boma la Ntchisi

Msungwana wina wa zaka zisanu ndi chimodzi 6wafa atagudidwa ndi galimoto pa msika wa Khuwi m’boma la Ntchisi. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomali Sergeant Gladson M’bumpha watsimikiza za nkhaniyi...

View Article


Ophunzira a CHANCO Achita Ziwonetsero za Bata

Ophunzira ku sukulu ya ukachenjede ya Chancellor mu mzinda wa Zomba achita ziwonetsero za bata pomwe anakapeleka chikalata cha madandaulo awo kwa bwanamkubwa wa boma la Zomba chopempha m’tsogoleri wa...

View Article

Atolankhani Awayamikira Kamba Kovumbulutsa Zinthu Zobisika

Atolankhani m’dziko muno awayamikira kamba kodzipereka pa ntchito zofalitsa mauthenga othandiza pa chitukuko cha miyoyo ya anthu m’dziko muno. Ena mwa anthu omwe athilira ndemanga pa za momwe ntchito...

View Article

Mpingo wa Anglican Ukusowa Thandizo la Ana Amasiye

Mpingo wa Anglican m’boma la Kasungu wapempha anthu akufuna kwabwino kuti athandize malo osamalirako ana amasiye ndi ovutika omwe mpingowu uli nawo ku Nthunthama m’bomalo. Mpingowu wati ukusowa...

View Article


Amayi a Mpingo wa Katolika Ayenera Kusamalira a Mndende

Bungwe la amayi a mpingo wakatolika la Catholic Women Organisation (CWO)mu dayosizi ya Zomba lati amayi ali ndi udindo wosamalira anthu a m’ndende za mdziko muno. Mlembi wa bungweli mayi Catherine...

View Article


Ma Episkopi Adandaula Kamba ka Kusowa Kwa Ntchito

Bungwe la ma episikopi a mpingo wakatolika mchigawo cha m’mayiko a ku m’mwera kwa Africa la Southern Africa Catholic Bishops Conference, lati ndi lokhudzidwa ndi mavuto a kusowa kwa ntchito omwe...

View Article

Papa Achita Chotheka Kuthetsa Nkhondo Mdziko la Venezuella

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati achitapo kanthu pofuna kuthetsa nkhondo ya pachiweniweni yomwe ikuchitika mdziko la Venezuela. Papa amalankhula izi lamulungu pa bwalo...

View Article

Anthu Awiri Afa pa Ngozi ya pa Msewu Mboma la Zomba

Anthu  awiri afa ndipo ena 33 avulala m’boma la Zomba galimoto lomwe anakwera litagubuduzika pa malo ena otchedwa Chikupila m’bomalo. Malinga ndi wofalitsa nkhani za apolisi mchigawo chakuvuma...

View Article

Akhristu Apemphelere Mtendere

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha akhristu a mpingowu kuti apempherere mtendere pa dziko lonse pansi. Malingana ndi malipoti a wayilesi ya Vatican Papa Francisco...

View Article


Achinyamata Akhale ndi Mtima wa Utumiki

Achinyamata a mpingo wakatolika mdziko muno ati akuyenera kukhala ndi mtima wa utumiki komanso akhale okonda kupemphera. Episkopi wa dayosizi ya Mzuzu Ambuye John Ryan ndi omwe apereka pempholi ku St...

View Article

Apempha Boma Liwamangire ma Hostel

Ophunzira achitsikana pa sukulu ya sekondale yoyendera ya Changali m’dera la a Senior Chief Chimwala m’boma la Mangochi apempha boma kudzera mu unduna wa za maphunziro kuti uwamangire Hostel pa...

View Article


Papa Francisco Ayendera Dziko la Portugal

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wanyamuka kupita mdera la Fatima mdziko la Portugal komwe akakhale nawo pa chikondwelero chakuti padutsa zaka 100 chiwonekereni amayi Maria...

View Article

Archdayosizi ya Lilongwe Ikhazikitsa Ntchito Yotolera Thandizo Lomangira...

Akhristu a mpingo wakatolika mu Archdayosizi ya Lilongwe awapempha kuti agwirane manja pa ntchito yomanga cathedral yatsopano mu Archdayosiziyo. Mkulu woona za chuma mu Archdayosiziyi bambo Gerald...

View Article


Chiwerengero cha Anthu Opezeka ndi Kachilombo ka HIV Chatsika Mdziko la Malawi

Bungwe la National Aids Commission NAC lati ndi lokondwa kamba koti chiwerengero cha anthu omwe ali ndi kachilombo koyambitsa matenda a Edzi ka HIV mdziko muno chikutsika. Mmodzi mwa akuluakulu ku...

View Article

Akuba Aba ku Parishi ya Ntcheu

Anthu anayi omwe sakudziwika aba katundu osiyanasiyana  ku parishi ya mpingo wa katolika ya Ntcheu mu dayosizi ya Dedza. Wofalitsa nkhani za apolisi m’boma la Ntcheu Sub-Inspector Hastings Chigalu...

View Article

Radio Maria Yayamba Masiku Atatu Othamanga Mwakathithi ndi Amayi Maria

Radio Maria Malawi molumikizana wayilesi zina za Maria za pa dziko lonse lero zayamba ulendo wa masiku atatu wothamanga ndi amayi Maria mwa kathithi  ndi cholinga chofuna kupeza thandizo la ndalama...

View Article
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>