Wachiwiri Kwa Mtsogoleri wa Dziko la Iran Atula Pansi Udindo
Wachiwiri kwa pulesident wa dziko la Iran a Eshaq Jahangiri watula pansi udindo wake ndipo kuti sayimananso pa udindo wa Pulezidenti patangotsala masiku ochepa kuti chisankho cha Pulezidenti wa dzikolo...
View ArticleCRECCOM Ikuphunzitsa Anthu Maufulu a Ana
Ngati njira imodzi yoonetsetsa kuti zinamwali sizikusokoneza kalendala ya maphunziro,bungwe lomemeza anthu pa chitukuko la CRECCOM kudzera mu project ya Aspirelikuphunzitsa adindo za maufulu a wana...
View ArticleKiir Wachotsa Marchar pa Udindo
M’tsogoleri wa dziko la South Sudan a Salva Kiir wachotsa paudindo wachiwiri wake a Riek Machar potsatira kumenyana kwa mphamvu komwe kunabuka pakati pa anthu otsatira atsogoleri-wa mu m’dzinda wa...
View ArticleAnthu 10 Afa ndi Bomba Mdziko la Somalia
Anthu khumi (10) afa ndipo ena avulala anthu ena ataphulitsa mabomba awiri pa chipata cholowera kubwalo la ndege mu mzinda wa Mogadishum`dziko la Somalia. Malinga ndi malipoti awailesi ya BBC, anthu...
View ArticleAnthu Oposa 50 Athawa ku Ndende Mdziko la DRC
Mkulu wa mpingo wina pamodzi ndi anthu makumi asanu 50 ati atuluka ku ndende ina mu mzinda wa Kinshasa mdziko la Democratic Republic of Congo DRC potsatira zamtopola zomwe anthu otsatira mpingowu...
View ArticleRadio Maria Itsekera Masiku Atatu Othamanga ndi Amayi Maria Mwakathithi
Radio Maria Malawi lamulungu yatsekera masiku ake atatu othamanga ndi amayi Maria mwakathithi omwe inayamba lachisanu. Ntchitoyi ayitsekera lamulungu usiku ndi mwambo wa nsembe ya misa ndipo polankhula...
View ArticlePapa Apempha Mtendere mdziko la CAR
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha mtendere mdziko la Central African Republic potsatira zamtopola zomwe zikuchitika mdzikolo. Papa amalankhula izi lamulungu ku...
View ArticleParish Ya Bango Ku Mulanje Ichita Chaka Cha Zaka 50 Za Parishi-yi.
Mwambo wokondwelera kuti parish ya Bango ku Mulanje mu arch-dayosizi ya Blantyre kuti yakwanitsa zaka 50 chiyikhadzikitsileni udzachitika pa 3 mwezi wa June chaka chino. Wapampando wa komiti yomwe...
View ArticlePapa Francisco Atsindika Zakufunika Kolankhula Mwa ufulu.
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse papa Francisco wauza ma episikopi a mpingowu m’dziko la Italy kuti ndi bwino kulankhula mwa ufulu ngakhale zolankhulazo zitakhala kuti sizingakondweretse...
View ArticleBambo wina Ku Mangochi Amupeza Ndi Mlandu Wopezeka Ndi Mankhwala Opanda...
Bwalo la milandu m’boma la Mangochi lalamula bambo wina wa zaka 50 zakubadwa kuti apereke ndalama zokwanira 1 miliyoni 8 hundred 64 sauzande 3 hundred and 86 kwacha kulephera apo akakhale ku ndende kwa...
View ArticlePapa Francisco Wakumana Ndi Mtsogoleri Wadziko La America A Donald Trump.
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse papa Francisco lero anakumana ndi m’tsogoleri wadziko la United States of America a Donald Trump. Malingana ndi malipoti a BBC atsogoleriwa anakumana ku...
View ArticleMabomba Awiri Apha Apolisi Atatu
Apolisi atatu afa ndipo anthu wamba khumi avulala mu mzinda wa Jakarta mdziko la Indonesia kaamba ka mabomba awiri omwe anaponyedwa pa malo ena okwelera bus mu mzindawo. Malipoti a wailesi ya BBC...
View ArticleAnthu 200 Aphedwa Mdziko La Syria
Anthu wamba oposera 200 ndi omwe afa mdziko la Syria kaamba ka mabomba ochokera mu ndege za asilikali a mdziko la America kuyambira pa 23 April kufikira pano. Malinga ndi malipoti a News 24 bungwe...
View ArticlePapa Akhumudwa ndi Mchitidwe waChiwembu
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati ndi okhumudwa ndi chiwembu chomwe chachitika mu mzinda wa Manchester ku England chomwe chaphetsa anthu oposera makumi awiri ndi...
View ArticleAtsutsa Kuti Pulezidenti Akunyoza Anthu Osawona
Bungwe la Malawi Union of the Blind latsutsa malipoti akuti mtsogoleri wa dziko lino Professor Peter Mutharika akumanyoza anthu osawona pa misonkhano ya ndale ngakhalenso ya boma. Wapampando wa...
View ArticleApempha Khonsolo Kuchita Zitukuko Poyera
Akulu-akulu oyang’anira ntchito za chitukuko m’ma WARD amu mzinda wa Zomba apempha khonsolo ya mzindawu kuti ikafuna kuchita ntchito zachitukuko iziyamba yauza akulu-akuluwo za momwe ntchitozo...
View ArticleAchinyamata Omwe Anakayimilira Mpingo Wakatolika M’dziko Muno Ku Chaka Cha...
Polankhula moyimira achinyamata-wa bambo Frank Mwinganyama omwe ndi mlangizi wa achinyamata mu Arch-Dayosizi ya Blantyre omwenso anali nawo pa ulendowu ati ndi okhutira ndi momwe chakachi chayendera....
View ArticleAnthu 14 Akuyembekeza Kunyongedwa Mdziko La Indonesia
Dziko la Indonesia lapereka chilango chakupha kwa anthu khumi ndi anayi (14) omwe anapezeka olakwa pa mlandu wopezeka ndi makhwala ozunguza bongo. Anthuwa omwe atatu ndi mzika za mdziko la Nigeria...
View ArticleCatholic Charasmatic Renewal Movement Ikondwelera Zaka 25
Mwambo wa msembe ya misa wokondwelera kuti bungwe la Catholic Charasmatic Renewal Movement (CCRM) lampingo wakatolika lakwanitsa zaka 25 chilikhazikitsileni m’dziko muno wachitika ku Maula Cathedral mu...
View ArticleAnthu Azikanena Ku Khonsolo Akachitiridwa Nkhanza
Khosolo ya mzinda wa Blantyre yapempha anthu malonda mu mzindawu kuti azikanena ku khosoloyi pa nkhanza zina zili zonse zomwe angachitiridwe ndi anthu ogwira ntchito kukhosoloyi. Wofalitsa nkhani ku...
View Article