Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live

Dziko la South Sudan Lalengeza Madera Omwe Akhudzidwa ndi Njala

Dziko la South Sudan lalengeza kuti mmadera ena a mdzikolo anthu akuvutika ndi njala. Malinga ndi boma la dzikolo komanso bungwe lowona za mgwirizano wa maiko a pa dziko lonse la United Nations UNanthu...

View Article


Afa Atawombedwa ndi Galimoto ku Ntchisi

Bambo wina wafa ataombedwa ndi njinga ya moto m’boma la Ntchisi. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo, Sergeant Gladson Mbumpha wati a Bruno Malithano a zaka 38zakubadwa anakwezana njingayo yomwe ndi...

View Article


Atolankhani Atenge Mbali Poteteza Anthu Achikulire

Bungwe lomenyera ma ufulu a anthu achikulire, la Malawi Network of Older People (MANEPO) lati atolankhani ndi ofunika pa ntchito yoteteza maufulu a anthu achikulire mdziko muno. Mkulu wa bungweri a...

View Article

Bwanamkubwa wa Balaka Apempha Mgwirizano

Khonsolo ya boma la Balaka yapempha kuti pakhale ubale wabwino pakati pa adindo ndi makomiti a za chitukuko m’bomalo. Bwanamkubwa wa bomalo, Rodrick Mateauma ndi yemwe wanena izi potsatira mphekesera...

View Article

Anthu 70 Afa pa Nyanja ya Atlabtic

Matupi oposera 70 a anthu akufa akuti apezeka akuyandama kudera lina mu nyanya yayikulu ya Atlantic m’dziko la Lybia. Akatswiri pa ntchito zopulumutsa anthu pa ngozi zochitika  pamadzi akuti ndi amene...

View Article


Amayi Awiri Akayankha Mlandu Wopha Kim Jong-Nam

Amayi ena awiri akuyembekezeka kukawonekera ku bwalo la milandu mawa ndi kukayankha mlandu wokhudzana ndi kuphedwa kwa mchimwene wake wa mtsogoleri wa dziko la North Korea,Kim Jong-Nam. Malipoti a...

View Article

Anthu Atatu Amangidwa Kamba Koba Katundu ku CADECOM

Apolisi m’boma la Balaka agwira anthu atatu omwe akuwaganizira kuti ndi amene akukhudzidwa ndi mulandu wakuba ku malo a mpingo wakatolika a CADECOM ku Ulongwe ndi ku malo a zaulimi wa nthilira a...

View Article

Chipani cha MCP Sichikudziwapo Kanthu pa “Antchito”

Chipani cha Malawi Congress(MCP) chati sichikudziwapo kanthu kwa achinyamata omwe akuti anabwera ku likulu la chipanichi m’chigawo cha ku m’mwera kudzafuna malipiro awo a ntchito. Wapampando wa chipani...

View Article


MACRA Ikondwelera Tsiku Lokumbukira Wailesi pa Dziko Lonse

Dziko laMalawimawa ligwilizana ndi mayiko pa dziko lonse pochita mwambo wa tsiku loganizira nyumba zoulutsira mawu padziko lonse (World Radio Day). Mwambo wa ukulu woganizira tsikuli unachitikira ku...

View Article


Anthu 26,000 Athawa Mu Mzinda Wa Mosul

Anthu okwana 26 sauzande a m’dziko la Iraq athawa kum’mvuma kwa mzinda wa Mosul pa masiku okwana khumi 10 potsatira kumenyana komwe kunabuka pakati pa asilikali a dzikolo ndi zigawenga za Islamic State...

View Article

Gogo Afa Khoma la Nyumba Litamugwera

Mayi wina wafa khoma la nyumba litamugwera m’boma laNtchisi. Malingana ndi ofalitsa nkhani za apolisi m’bomaloSergeantGladson Mbumpha,malemu mayiMelina Felix akuti khudzidwa ndi imfayi pa nthawi imene...

View Article

Tsvangirai Wamwalira

Mtsogoleri wa zipani zotsutsa boma ku nyumba ya malamulo mdziko la Zimbabwe, Morgan Tsvangirai wamwalira. Malipoti  a wailesi ya BBC ati Tsvangirai wamwalira pa chipatala china cha mdziko la South...

View Article

Sam Mpasu Wamwalira

Mtsogoleri wa chipani cha New Labour, a Sam Mpasu apezeka atafa ku nyumba kwawo. Mneneri wa ku banja a Stanly Wasi, ati akukhulupilira kuti a Mpasu omwe anakhalaponso sipikala wa nyumba ya malamulo...

View Article


Zuma Atula Pansi Udindo

Mtsogoleri wa dziko la South Africa, Jacob Zuma watula pansi udindo wake. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC, Zuma wati akuchoka pa udindowu mwa kufuna kwake osati kaamba kokakamizidwa ndi chipani...

View Article

Apha Msuweni Kaamba Kogona ndi Mkazi Wake

Apolisi m’boma la Mchinji amanga mamuna wina kaamba komuganizira kuti anapha msuweni wake atamugwira akuchita zadama ndi mkazi wake. Malinga ndi wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo, Inpector Kaitano...

View Article

Browsing all 1875 articles
Browse latest View live