ANA ATATU AFA KUDOWA PA NGOZI ZOSIYANASIYANA
Ana awiri ku Mponela m’boma la Dowa afa chipupa cha nyumba yomwe anagona chitawagwera. Mneneli wa apolisi ku Mponela a Kondwani Kandiado atsimikiza za nkhaniyi ndipo ati ,anawo ndi Angella Hastings...
View ArticleMAGANIZO A ANTHU PA ZA KUPUMA UDINDO WA APAPA
Pamene anthu akupitiliza kuthilirapo ndemanga pa ganizo la mtsogoleri wa Mpingo waKatolika pa dziko lonse, Papa Benedikito wachi 16 lopuma pa udindowu mwezi uno,anthu mdziko muno ayamikira papayu...
View Article"PAPA AKHONZA KUKHALA WA KU AFILIKA", KADINALA TURKSON
Kadinala Peter Appiah Turkson wa m’dziko la Ghana wati mtsogoleri watsopano wa Mpingo wakatolika pa dziko lonse akhonza kukhala wa ku Afilika. Kadinalayu ndi mmodzi mwa makadinala atatu aku Afilika...
View ArticlePAPA APEMPHA MAPEMPHERO KWA AKHRISITU
Mtsogoleri wa Mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Benedikito wachi 16 wapempha akhrisitu kuti amupempherere pamodzi ndi Papa yemwe adzalowe m’malo mwake mtsogolomu. Papayu walankhula izi kwa...
View ArticleMPINGO WA KATOLIKA KOMANSO ANGILIKANI ALOWA M'NYENGO YA LENT
Akhrisitu a Mpingo wa Katolika komanso Angilikani pa dziko lonse lapansi ayamba nyengo yokumbukira masautso a Yesu Khrisitu. Nyengoyi imayamba ndi mwambo wa nsembe ya misa ya phulusa, pomwe...
View ArticleDONGOSOLO LA KUTULA PANSI UDINDO KWA APAPA
Mneneli wa Mpingo wa katolika ku VatiKani Bambo Federico Lombardi apereka dongosolo la momwe zikhalire pomwe mtsogoleri wa Mpingowu akhale akupuma komanso mmene asankhire papa wina kumapeto a mwezi...
View ArticlePAPA BENEDIKITO WA CHI 16 ATHOKONZA BUNGWE LA PRO-PETRI-SEDE ASSOCIATION OF...
Mtsogoleri wa Mpingo wa Katolika pa dziko lonse Papa Benedikito wachi 16, wayamikira bungwe lina la m’dziko la Belgium, chifukwa cha thandizo landalama lomwe limapereka ku likulu la Mpingowu. Papa...
View ArticleAPEMPHA BOMA KUTI LICHITEPO KANTHU PA ZAVUTO LA NJALA
Anthu a m’dera la mfumu yaikulu Katuli m’boma la Mangochi apempha boma kuti liwathandize msanga pobweretsa chimanga ku Admarc ya Katuli komwe chinatha kalekale. Pempho la anthuwo, ladza pomwenso misika...
View ArticleALAMULIDWA KUKAKHALA KU NDENDE ZAKA ZINAYI KAMBA KOBAYA MUNTHU
Bwalo la milandu la magistrate m’boma la Dowa lalamula mwamuna wina kuti wa kumalo osungira anthu othawa kwawo a Dzaleka kuti akakhale kundende zaka zinayi kamba kovulaza mnyamata wina wa zaka 16...
View ArticleM'BUSA AGWIDWA KAMBA KOGWILIRA MZIMAYI WA MISALA
Apolisi ku Dowa amanga m`busa wina yemwe ndi mzika ya dziko la Democratic Republic of Congo wa kumalo osungirako anthu othawa kwawo a Dzaleka m’bomalo kamba komuganizira kuti adagwirila mzimayi...
View ArticleAKHRISTU ATSANZIKANA NDI PAPA BENEDIKITO WA 16
Akhristu pafupifupi 100 sauzande anasonkhana kunja kwa tchalitchi la likulu la St Peters Square pofuna kuona komanso kutsanzikana ndi Papa Benedicto wa 16 yemwe akhale akutula pansi udindo wake...
View ArticleAKHRISTU ALANDIRA MADALITSO KUCHOKERA KWA PAPA
Akhristu zikwizikwi anakhamukira ku likulu la Mpingo wakatolika ku Vatikani kukalandira madalitso ochokera kwa mtsogoleri wa Mpingowu pa dziko lonse Papa Benedikito wachi 16 pa umodzi mwa miyambo yake...
View ArticleMSONKHANO WOSAKHA PAPA WATSOPANO UCHITIKA MWEZI WA MARCH
Likulu la Mpingo wakatolika ku Vatikani lati msonkhano wapadera wosankha Papa watsopano udzayamba pa 15 kapena pa 19 mwezi wa March. Mneneli wa Mpindo wa Katolika ku Vatikani Bambo Federico Lombard...
View ArticleCHANJELANI NDI BODZA LA A DEMONI
Ulaliki titled Chenjelani ndi Bodza la a Demoni by Fr.E. Mwinganyama
View ArticleANTHU 1 SAUZANDE AKUMATENGA MATENDA A EDZI PASABATA
Mlembi wamkulu mu ofesi yoona za madyedwe ndi matenda a Edzi Mai Edith Mkawa ati ndiwokhudzidwa ndi kufala kwa kachilombo ka matenda oyambitsa Edzi ka HIV ngakhale Boma likuyesetsa kupeza njira...
View ArticleBOMA LIFUFUZA ANTHU OMWE ANATUMA ANA KUTI ACHITE ZIONETSERO
Boma la Malawi lati lifufufuza ndi kumanga anthu omwe adatsogolera ana a sukulu omwe adachita ziwonetsero zokwiya ndi kuima kwa maphunziro pamene aphunzitsi mumzinda wa Blantyre amachita nawo...
View Article"MUKHALE ZITSANZO ZABWINO", BAMBO MULAVA
Abwenzi a Radio Maria awapempha kukhala zitsanzo zabwino pokondana ndi kulimbikapogwira ntchito zothandiza wayilesiyi. Wachiwiri kwa wamkulu owona za ma Pulogalamu ku wayilesiyi, Bambo Medrick Mulava...
View ArticleDZIKO LA TANZANIA LIFUFUZA ZA KUPHEDWA KWA WAMSEMBE
Pulezidenti wa dziko la Tanzania a Jakaya Kikwete walamula apolisi m’dzikolo kuti afufuze mwansanga za kuphedwa kwa wamsembe wina wa Mpingo wa Katolika m’dzikolo. Pulezidenti Kikwete walamula izi...
View ArticleOPHWANYA LAMULO, LAMULO LIDZAMUPWANYA
Ulaliki titled Ophwanya Lamulo, Lamulo lidzamuphwanya
View ArticleKUTUMIKIRA MULUNGU KUMASOWA CHIKONDI
Ulaliki titled Kutumikira Mulungu Kumasowa Chikondi by Father Mwinganyama
View Article