MWAMUNA ADZIPHA PODZIMANGILIRA ATAKANGANA NDI MKAZI WAKE
Bozyolo Chigwenembe wa zaka 22 zakubadwa wadzipha podzimangilira pambuyo pokangana ndi mkazi wake kwa mfumu yaikulu Dzoole m’boma la Dowa. Mneneli wa apolisi ku Mponela m'bomalo a Kondwani...
View ArticleMSONKHANO OYAMBA OKHUDZA KUSANKHA PAPA WATSOPANO
Likulu la Mpingo wa Katolika ku Vatikani lalengeza kuti msonkhano oyamba wa makadinala okonzekerakusankha Papa watsopano uchitika pa 4 March 2013. Malinga ndi Chikalata chomwe mkulu wa makadinala omwe...
View ArticleBAMBO HENLY CHAONA ALOWA M'MANDA LERO
Mwambo woyika m’manda thupi la Malemu Bambo Henry Chaona omwe adamwalira pa 2 March kuchipatala cha Malamulo mu mzinda wa Blantyre uchitika pa 4 March 2013. Likulu la diocese ya Zomba ndi lomwe...
View ArticlePAGOLOGOTA
Lent track titled Pagologota by ST Peters Choir Doviko Church Tsangano Parish
View ArticleDEMOKALASE KAPENA DEMONI KALASI?
Ulaliki titled Demokalase kapena Demoni Kalasi? by Father Mwinganyama
View ArticleMBUYE YESU NDI ZINGWE ZIJA
Lent track titled Mbuye Yesu ndi Zingwe Zinja by ST Simon and Jude Catholic Choir
View ArticleASEMINO 55 A CHAKA CHOYAMBA ALANDIRA MIKANJO
Asemino 55 ochokera m’madayosizi asanu ndi atatu a Mpingo wa Katolika m'dziko muno alandira mikanjo ku sukulu yosula ansembe ya Kachebere ku Mchinji mu arkidiocese ya Lilongwe. Episkopi wa...
View ArticleALIYENSE ABWERE NDI CHACHIKHUMI KUNYUMBA KWANGA
Ulaliki titled Aliyense Abwere ndi Chachikhumi Kunyumba Kwanga by Father Nthalika
View ArticleGWIRITSANI NTCHITO NDALAMA
Ulaliki titled Gwiritsani Ntchito Ndalama by Father Nthalika
View ArticleMWAMBO OSANKHA PAPA WATSOPANO ULI M'KATI
Makadinala a Mpingo wa Katolika akupitiliza mwambo osankha Papa watsopano atalephera kupeza yemwe wapambana pachisankho chawo pa 12 March 2013. Makadinala 115 ndiomwe akusankha Papa yemwe alowe...
View ArticleKODI MPHAMVU ZANU MUMAZITENGA KUTI?
Ulaliki titled Kodi Mphamvu Zanu Mumazitenga Kuti? by Father Kimu
View ArticlePAPA FRANSIS SAGWIRIZANA NDI MAUKWATI AMUNA KAPENA AKAZI OKHAOKHA
Malipoti a catholic World News ati ngakhale kuti mtsogoleri wa mpingo wakatolika Papa Fransis ali omasuka mu zambiri, sakugwizana kwambiri ndi maukwati a pakati pa amuna kapena akazi okhaokha....
View ArticleMPINGO WA KATOLIKA ULI NDI PAPA WATSOPANO
Kadinala George Mario Bergolio wa m’dziko la Argentina ndiye mtsogoleri watsopano wa Mpingo wa Katolika pa dziko lonse lapansi. Kadinalayu wasankhidwa pa 13 March 2013 patangotha tsiku limodzi...
View ArticleBOMA LICHITEPO KANTHU PANKHANI YOKWEZA MAPHUNZIRO
Mpingo wa Katolika wati ukufunitsitsa kuti boma la Malawi liwunikenso bwino njira zomwe zidakhazikitsidwa poyendetsa ntchito zamaphunziro pofuna kuti maphunziro apite patsogolo m’dziko muno. Mkulu...
View ArticlePAPA FRANSIS ALIMBIKITSA CHIKONDI PAKATI PA OSAUKA-JAKAYA KIKWETE
Mtsogoleri wa dziko la Tanzania a Jakaya Kikwete ati kusankhidwa kwa Papa Fransis kuthandiza kwambiri kupititsa patsogolo chikhulupiliro pakati pa a Katolika komanso anthu onse kaamba koti moyo wa...
View ArticleA VUWA KAUNDA AMANGIDWASO POMWE AMAFUNA KUPITA KU ULAYA
M'modzi wa akuluakulu a chipani cha Democratic Progressive DPP a Symon Vuwa Kaunda omwe anatulutsidwa pa belo sabata yangothayi awamanganso pa 17 March 2013 pomwe amafuna kukwera ndege kupita ku...
View ArticleANTHU 5 500 AFA NDI MATENDA A MALUNGO CHAKA CHATHA
Unduna wa za umoyo wati anthu 5 miliyoni ndi omwe anadwala matenda a malungo chaka chatha ndipo mwa anthuwa 5 Sauzande 5 handirede adamwalira ndi matendawa ngakhale kuti matendawa ndi opeweka komanso...
View ArticlePAPA FRANCIS AYAMIKIRA NYUMBA ZOFALITSA NKHANI
Mtsogoleri wa Mpingo wa Katolika pa dziko lonse lapansi Papa Francis wayamikira nyumba zofalitsa nkhani pa dziko lonse kaamba kotsatira ndi kulengeza bwino zonse zomwe zimachitika ku likulu la...
View ArticleBUNGWE LA RED CROSS LAYAMBITSA NTCHITO YOLIMBIKITSA UCHEMBERE WABWINO
Bungwe la Malawi Red Cross layambitsa ntchito yolimbikitsa uchembere wabwino m’maboma a Kasungu ndi Ntchisi. Ntchitoyi yomwe ndi ya ndalama zokwana 600 million kwacha ikuyembekezeka kuthandiza...
View Article