Ntchito Zoweruza Milandu Ziyamba Kuyenda Mwachangu
Ntchito zoweruza milandu mmabwalo osiyanasiyana mdziko muno ati ziyamba kuyenda mwachungu potsatira kusintha kwa zipangizo zogwilira ntchitoyi zomwe mabwalo aakulu alandira mdziko muno. Mmodzi mwa...
View ArticlePapa Francisco Apepesa Mabanja omwe Ataya Abale Mdziko la China
Mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco wapereka uthenga opepesa ku mabanja omwe ataya abale awo pangozi yomwe yachitika mdziko la China makina a fakitore ina ataphulika mchigawo...
View ArticleKadinala Njue Wapempha Anthu a Mdziko la Kenya kuti Akhale a Makhalidwe Abwino
Kadinala John Njue wa m’dziko la Kenya wapempha m’zika za dziko la kwawo zomwe zikukhala m’dziko la America kuti zisamatengere makhalidwe oyipa omwe mzika zina zimachita m’dzikomo. Kadinala Njue...
View ArticleMayi wa Zaka 50 Wadzipha
Mayi wina wa zaka 50 m’boma la Ntchisiwadzipha podzimangilira ku mtengo kamba koti anapezeka ndi matenda a khansa. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomali Sergent Gladson M’bumpha watsimikiza za...
View ArticlePulezidenti Kiir Asayinira Pangano la Mgwirizano
Mtsogoleri wadziko la South Sudan A Salva Kiir wati asayinira mgwirizano odzetsa mtendere pakati pa iye ndi magulu owukira boma mdzikolo. Pulezidenti Kiir lolemba analonjeza kuti asainira panganoli...
View ArticleBungwe la MEC Lichititsa Chisankho Chapadera
Bungwe loyendetsa zisankho mdziko muno la Malawi Electoral Commission (MEC) lachiwiri lichititsa chisankho chapadera cha makhansala mmadera asanu momwe mulibe makhansala pazifukwa zosiyanasiyana...
View ArticleApolisi m’boma la Dowa Agwira Mzika za Mdziko la Ethiopia
Apolisi m’boma la Dowa amanga mzika zisanu ndi zinayi za mdziko la Ethiopia zomwe zalowa mdziko muno popanda zitupa zoyenera. Apolisi m’bomalo agwira anthuwa usiku wa lamulungu lapitali atawapeza...
View ArticleZigawenga Zisanu za Boko Haram Zaphedwa
Anthu asanu a mgulu la zigawenga za Boko Haram aphedwa ndi asilikali a boma mdziko la Nigeria. Asilikaliwo apha zigawengazo zitachitira chiwembu mdipiti wa galimoto za asilikali zomwe zimaperekeza...
View ArticleDziko la France Lipereka Ulemu kwa Omwe Ateteza Sitima ku Zauchifwamba
Dziko la France lolemba lapereka ulemu wapadera kwa mzika zitatu za mdziko la America ndi ina yaku Britain chifukwa cholepheretsa munthu wina wamgulu la zaufwamba yemwe amafuna kupha anthu mu sitima...
View ArticleBoma Likhazikitsa Malo a Achinyamata Ophunziliramo Ntchito ZamanjaBoma...
Mlangizi wa pulezidenti pankhani za mabungwe a Mavuto Bamusi atsimikizira mabungwe omwe siaboma m’boma la Zomba kuti boma likhazikitsa malo oti achinyamata aziphunziliramo ntchito za manja m’boma...
View ArticleBungwe la UN Lawopseza Dziko la South Sudan
Bungwe la United Nations (UN) lawopseza kuti lichitapo kanthu ngati mtsogoleri wa dziko la South Sudan a Salva Kiir sasayina pangano la mtendere ndi magulu omwe akuwukira dzikolo. Pa msonkhano wa...
View ArticleDziko la USA Lachenjeza Dziko la South Sudan kuti Lisaphwanye Pangano
Dziko la United States lachenjeza atsogoleri a dziko la South Sudan kuti asaphwanye pangano lomwe asayinira lomwe cholinga chake ndi kuthetsa nkhondo ya pachiweniweni yomwe yakhala ikuchitika...
View ArticleDziko la Iraq Lakhazikitsa Komiti Yodzetsa Chitetezo
Nduna yayikulu ya dziko la Iraq yakhazikitsa komiti yomwe izigwira ntchito yoteteza akhristu komanso madera ena omwe amayang’aniridwa ndi boma m’dzikolo. Ndunayi yakhazikitsa komitiyi potsatira...
View ArticleMaepiskopi Mdziko la France Adzudzula Anthu omwe Atentha Mzikiti Mdzikolo
Bungwe la maepiskopi mdziko la France ladzudzula anthu ena omwe atentha mzikiti mtauni ina kum’mwera chakumvuma mdzikolo masiku apitawa. Muuthenga omwe bungweli latulutsa maepiskopiwo ati zomwe achita...
View ArticleAnthu Oposera 100 Afa mu Nyanja ya Mediterranean
Anthu oposera 100 akuwaganizira kuti afa mdziko la Libya mabwato awiri omwe anakwera atamila munyanja ya Mediterranean pomwe amapita mmayiko aku ulaya. Malinga ndi akuluakulu a boma mdziko la Libya...
View ArticleBungwe la Eye of the Child ndi Lokhudzidwa ndi Imfa ya Mwana wa Zaka Zisanu
Bungwe la Eye of the Child lati ndi lokhudzidwa kwambiri ndi imfa ya mwana wazaka zisanu yemwe waphedwa masiku apitawa mumzinda wa Lilongwe pofuna kugwiritsa ntchito ziwalo zake ngati zizimba...
View ArticleDziko la Egypt Lidzudzula Kazembe wa M’dziko la Britain
Dziko la Egypt linayitanitsa kazembe wa dziko la Britain mdzikolo John Casson, chifukwa chodzudzula bwalo la milandu mdzikolo lomwe lalamula atolankhani atatu a wailesi ya kanema ya Al-Jazeera kuti...
View ArticleAsilikali a Dziko la South Sudan Aphwanya Pangano
Asilikali owukira boma mdziko la South Sudan adzudzula asilikali a boma mdzikolo chifukwa chophwanya pangano la mtendere lomwe atsogoleri ambali ziwirizi asayinira masiku apitawa asilikaliwo...
View ArticleAnthu Awiri Afa ndipo Ena 9 Avulala pa Ngozi ya Galimoto M’boma la Zomba
Anthu awiri afa ndipo ena asanu ndi anayi avulala minibus yomwe anakwera itagubuduzika dalaivala wake atalephera kuwongolera m’boma la Zomba. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomali a Patricio Supriano...
View ArticleAnthu Khumi Afa ndi Moto Mdziko la France
Anthu khumi afa ndi ena anayi avulala kodetsa nkhawa ndi moto omwe unabuka mwadzidzi mu nyumba ina mu mzinda wa Paris mdziko la France. Malinga ndi malipoti a wayilesi ya BBC chomwe chinayambitsa...
View Article