Papa Ayamikira Bungwe la ma Episkopi a Mdziko la Poland
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wayamikira bungwe la ma episkopi a mdziko la Poland kamba ka chisamaliro chabwino chomwe anamuwonetsera pa mwambo wa chaka cha achinyamata...
View ArticlePapa Francisko Apemphelera Mwapadera Anthu Okhudzidwa ndi Chiwembu Mdziko la...
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Fransiskolamulungu anachita mapemphero a padera opemphelera anthu onse omwe akhudzidwa ndi chiwembu cha mabomba chomwe chachitika ku m’mwera kwa...
View ArticleApempha Gwirizano Pofuna kulimbana ndi Matenda a EDZI
Anthu mdziko muno ati akuyenera kugwirana manja polimbana ndi kufala kwa kachilombo koyambitsa matenda a Edzi komanso kupewa mchitidwe wosalana. Polankhula ku mwambo woyatsa makandulo pokumbukira anthu...
View ArticleAlimbikitsa Akhristu Kulemekeza Sacrament la Ukaristia
Akhristu a mpingo wa katolika ati akuyenera kuzindikira kuti atha kuzamitsa chikhulupiliro chawo mwa Mulungu kudzera mu sacrament la Ukaristia. Polankhula pambuyo pa m’bindikiro omwe bungwe la...
View ArticlePapa Fransisko Wayamikiridwa ndi Chipembezo cha Chisilamu
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco amuyamikira kamba kothilirapo ndemanga ponena kuti chipembedzo cha chisilamu si chofanana ndi magulu omwe amakhala akuchita za uchifwamba....
View ArticlePAC Ikuphunzitsa Amayi Luso Lobweretsa Mtendere
Bungwe la mgwilizano wa mipingo ndi zipembedzo laPublic Affairs Committee(PAC)lati likufuna kulimbikitsa kuphunzitsa amayi luso lothandiza kubweletsa mtendere pa nkhani zosiyanasiyana zochitika m’dziko...
View ArticleAletsa Mchitidwe Woletsa Anthu Kulandira Thandizo laku Chipitala
Akuluakulu a khonsolo ya boma la Mzimba achenjeza atsogoleri a mpingo wa Ziyoni m’dera la Chikangawa kuti asiye m’chitidwe woletsa anthu a mpingiwo omwe ali ndi kachilombo koyambitsa matenda a Edzi...
View ArticleApempha Ubale Wabwino Pothana ndi Umbava
Anthu a m’boma la Mulanje awapempha kuti amange ubale wabwino ndi apolisi pofuna kuthana ndi m’chitidwe wa za umbanda ndi umbava m’bomalo. A Isaiah Mlowoka omwe ndi mkulu wa apolisi m’bomalo alankhula...
View ArticleAwapempha Kuti Adzitumiza Ana awo ku Sukulu za Mkombaphala
Makolo a m’boma la Zomba awapempha kuti adzikhala ndi chidwi chotumiza ana awo osachepera zaka zisanu ku sukulu za mkomba phala. Mmodzi mwa akuluakulu ku Estate ya Gala m’boma la Zomba mai Meria Milli...
View ArticleDeath Announcement
The Diocese of Mangochi regrets to announce the death of FR. BARTHOLOMEW PHWERUWA of Mangochi Diocese. Fr. Phweruwa has passed on today, 28th August 2016 at Mlambe Hospital in Blantyre. Brief History...
View ArticleMpingo Ulimbikitsa Mabanja Kukhala Olimba, Okhazikika mu Chikhristu
Mpingo wakatolika m’dziko muno wati udzipereka polimbikitsa mabanja opezeka mu mpingo-wu kukhala olimba ndi okhazikika pa chikhristu chawo. Mkulu wa kuofesi yoona za mabungwe a utumiki wa a Papa ku...
View ArticleMaiko a Palestine ndi Israel Akhale Pansi ndi Kukambirana
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati pakuyenera kukhala kukambirana kwabwino pakati pa dziko la Israel ndi Palestine potsatira zamtopola komanso kuphedwa kwa anthu a...
View ArticleZigawenga za Taliban Zapha Anthu 24 ndi Kuvulaza Ena 42 Mdziko la Afghanistan
Anthu ogwira ntchito m’boma makumi awiri ndi anayi 24 afa ndipo ena makumi anayi ndi awiri 42 avulala bus yomwe anakwera itaphulitsidwa mu mzinda wa Kabul lomwe ndi likulu la dziko la Afghanistan....
View ArticleAnthu Alondoloze Zitukuko Zawo
Bungwe la achinyamata la Titani lati mafumu akuyenera kulimbikitsa anthu kuti azilondoloza ntchito za chitukuko zomwe zikuchitika mmadera awo. Mkulu wa bungweli a Charles Cholopi ndi omwe alankhula izi...
View ArticleAkhristu Azilowa Bungwe la Awerengi
Akhristu a mpingo wa katolika mdziko muno awapempha kuti azikonda kulowa bungwe la awerengi chifukwa ndi bungwe lomwe limazama kwambiri pa kuwerenga mawu a Mulungu. Wapampando wa bungwe la awerengi pa...
View ArticleMabungwe Agwiritse Ntchito Radio Maria Malawi Ngati Chida Chofalitsira...
Bungwe la Legio Ya Maria lochokera ku Kachebere mu arkidayosizi ya Lilongwe lapempha mabungwe osiyanasiyana mu mpingo wa katolika kuti azigwiritsa ntchito Radio Maria Malawi ngati chida chofalitsira...
View ArticleMphunzitsi wamkulu Afa Pozimangilira.
Mphunzitsia wamkulu wa pa sukulu ya pulaimale m’boma la Dowa wazipha pozimangilira kudenga la nyumba yake. Malinga ndi ofalitsa za apolisi m’bomalo Sergent Richard Kaponda wati mphunzitsiyu ndi Briay...
View ArticleMaphunziro A M’mera Mpoyamba ndiofunika Kwa Ana.
Bungwe la Future Vision Ministry lapempha makolo a mdera la Sub T/A Ngwelero m’boma la Zomba kuti azikhala ndi chidwi chotumiza ana awo sukulu za m’mera mpoyamba. Mkulu wa bungweli a Newton Sindo ndi...
View ArticleAkhristu Azilowa Bungwe la Awerengi
Akhristu a mpingo wa katolika mdziko muno awapempha kuti azikonda kulowa bungwe la awerengi chifukwa ndi bungwe lomwe limazama kwambiri pa kuwerenga mawu a Mulungu. Wapampando wa bungwe la awerengi pa...
View ArticleMabanja Awalimbikitsa Kulembetsa Maina Awo.
Akhristu a mu Arch-Dayosizi ya Blantyre awapempha kuti alembetse maina awo kuti azatenge nawo mbali pa sonkhano waukulu wa mabanja omwe uzachike kuyambira pa 4 ndi kutha pa 5 August mu Arch-Dayosizi ya...
View Article