Anthu Khumi Ndi Asanu (15) Afa Mu Mzinda Wa Nairobi.
Anthu khumi ndi asanu afa nyumba ina itawagwera usiku wa lolemba mu mzinda wa Nairobi mdziko la Kenya. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC bungwe la Kenya Red Cross lati anthu omwe amathandiza anthu...
View ArticleMaofesi A Mkulu Woona Za Chitukuko Ndi Ntchito Zina Atsekedwa.
Makhansala a m’boma la Zomba atseka ma ofesi a mkulu woyang’anira mapulani ndi ntchito za zitukuko komanso ofesi ya mkulu woyang’anira ntchito zosiyanasiyana za m’bomalo kaamba kosakondwa ndi momwe...
View ArticleAmai a Mpingo Wakatolika Athandiza Seminare Ya St Peter’s.
Amai a bungwe la Catholic Women Organization (CWO) m’dayosizi ya Zomba apereka katundu osiyanasiyana ku seminare yaikulu ya St Peter’s m’bomalo. Poyankhula ndi Radio Maria Malawi wapampando wa...
View ArticleAnthu 7 Afa Pa Ngozi Ku Ntcheu
Anthu asanu ndi awiri 7 afa ndipo ena avulala basi yomwe anakwera itagwa pa Mlangeni m`boma la Ntcheu. Wofalitsa nkhani za apolisi m`bomali a Gift Matewere atsimikiza zankhaniyi ndipo ati basiyi...
View ArticleCOOPI Ikulimbikitsa Kudzidalira Kwa Anthu Amene Akhudzidwa Ndi Ngozi Zogwa...
Bungwe la Cooperazione Internazionale (COOPI) lati liwonetsetsa kuti likupititsa patsogolo kudzidalira kwa anthu amene akhudzidwa ndi ngozi zogwa mwadzidzidzi mdziko muno. Wamkulu wa bungweli mdziko...
View ArticleAlangiza Ophunzira Kukonzekera Bwino Mayeso
Episikopi wa dayosizi ya Uppershire ya mpingo wa Anglican Ambuye Brighton Malasa analimbikitsa ophunzira a folomu folo pa sukulu ya sekondale ya Malosa m’boma la Zomba kuti akonzekere bwino pomwe...
View ArticleApempha Mabanja Achikhristu Kuthandiza Anthu Osowa
Mabanja achikhristu m’dziko muno awapempha kuti adzithandiza anthu osowa ngati njira imodzi yoonetsa chifundo komanso chikondi kwa anhtuwa. Banja la a Mapemba lomwe limapezeka ku parishi ya St Johns,...
View ArticleAwayamikila Kamba Kolondoloza Ntchito Zachitukuko
Bungwe la Association for Prograssive Women (APW) m’boma la Neno layamikila anthu a m’dera la mfumu Symon m’bomalo kamba kotenga nawo mbali polondoloza ntchito za zichitukuko zomwe zikuchitika...
View ArticleAdzipha Kamba Kokhumudwa Ndi Imfa Ya Mwana Wa Mchemwali Wake
Mnyamata wina wadzaka pafupifupi 27 zakubadwa anadzipha podzimangilira ati kamba kokhumudwa ndi imfa ya mwana wa mchemwali wake yemwe anamupatsa dzina. Malingana ndi malipoti apolisi mnyamatayu dzina...
View ArticleMatenda A Fistula Avuta Kwambiri
Chiwerengero cha anthu odwala matenda a Fistula chikukwera kwambiri kuchigawo chaku m’mawa kwa dziko lino. Mkulu woona zamatenda a Fistula pachipatala cha boma la Mangochi a Ramzy Zinganindi omwe anena...
View ArticlePapa Francisco Alonjeza Kuthandiza Dziko La South Sudan
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco walonjeza kuti apereka ndalama pafupifupi 5 handred sauzande dollars ku dziko la South Sudan. Malinga ndi malipoti a wayilesi ya Vatican,...
View ArticleAwayamikira Kamba Kothandiza Odwala
Akuluakulu a chipatala chaching’ono cha Lumbadzi ayamikira akhristu a m’phakati wa Saint Michaels kuchokera ku parish ya Saint Matias ku Lumbadzi kamba kothandiza odwala apa chipatalacho. M’modzi mwa...
View ArticleMa Dalaivala A Minbus Anyanyala Kugwira Ntchito Yawo
Madalaivala a ma Minbus ku Zomba ayamba ayima kugwila ntchito potsatila kukhadzikitsidwa kwa lamulo latsopano loti asamanyamule matumba olemera 50 kilogalamu komanso kuti asamatenge anthu anayi pa (4)...
View ArticleAlonjeza Kuthandiza Kampani Ya EGENCO
Aphungu a kunyumba ya malamulo ati athandiza kampani yopanga magetsi ya EGENCO kuti ikwanilitse ntchito zake zochulukitsa mphamvu za magetsi mdziko muno. Komiti ya aphunguwa yoona za makampani a boma...
View ArticleAkondwela Ndi Sabata Ya Ulangizi Wa Ulimi
Bungwe loona za ulimi m’dzino muno la MALAWI FORUM FOR AGRICULTURAL ADIVISORY SERVICES lati ndi lokonda ndi momwe sabata ya ulangizi wa ulimi yayendera m’boma la Lilongwe. Musabatayi bungweli linachita...
View ArticleAtsutsa Malipoti Oti Apolisi Akumakolezera Ziwawa
Apolisi m’dziko muno atsutsa zomwe anthu ena akunena kuti akumakolezera ziwawa zomwe zakhala zikumachitika m’dziko muno. Mneneri wapolisi m’dziko muno a James Kadadzera ati apolisi sangalekelere anthu...
View ArticleApempha Akhristu Kuti Adzithandiza Ma Choir
Mkulu woona mapologalamu ku Radio Maria bambo Joseph Kimu wapempha akhristu akatolika kuti adzikhala ndi chidwi chothandiza ma choir achikatolika mdziko muno. Bambo Joseph Kimu apereka pemphori pa...
View ArticleBoma Liyamba Kugawa Chakudya Posachedwapa
Boma lati liyamba kugawa chakudya posasedwapa m’maboma onse omwe akhudzidwa ndi vuto la njala m’dziko muno. Nduna ya zofalitsa nkhani ndi kuphunzitsa anthu wolemekezeka mayi Patricia Kaliati anena izi...
View ArticleAlangiza Achinyamata Kulingalira Za Moyo Wachikhristu
Achinyamata m’dziko muno awalangiza kuti akuyenera kumalingalira mozama za moyo wawo wachikhristu. Bambo Francis Lekaleka omwe ndi bambo mlangizi mu ofesi yoona za mabungwe aPapa ya PONTIFICAL MISSION...
View ArticleAdzipha Kamba Koyambana Ndi Mwamuna Wake
M’mayi wina wa zaka 24 zakubadwa wadzipha kaamba koti anayambana ndi mwamuna wake kwa Bvumbwem’boma la Thyolo. Wachiwiri kwa mneneri wapolisi ku Limbe a Widson Nhlane watsimikiza za nkhaniyi ndipo wati...
View Article