AMBUYE ZIYAYE ASANKHA AKHRISTU OTHANDIZIRA ZOKONZEKERA MSONKHANO WA AMECEA
Arki episikopi wa Arki dayosizi ya Lilongwe Ambuye Tarcisius Ziyaye asankha gulu la akhristu oposa 75 omwe athandize pozokonzekera zansonkhano wa bungwe la aepiskopi la Association of Member Episcopal...
View ArticleCCJP YAKHAZIKITSA NTCHITO YOCHEPETSA KUTHINANA MNDENDE
Mkulu wa ma Jaji Justice Anastanzia Msosa wayamikira bungwe la Catholic Commission for Justice and Peace [CCJP]mu Arki dayosizi ya Lilongwe chifukwa chokhazikitsa pulojekiti yolimbikitsa kuti milandu...
View ArticleA MALAWI SITIKUKHWIMA PA NDALE
Mtsogoleri wa mpingo wa Anglican mdziko muno Bishopu Brighton Vita Malasa ati ziwawa zomwe zinachitika pa 8 march kwa Goliati mboma la Thyolo zawonetsa poyera kuti anthu mdziko muno sakukhwima pa...
View ArticleA KATOLIKA ATSANZIKANA NDI MONSINYO VAN MEGEN
Wapampando wa bungwe la Episcopal Conference of Malawi ECM wolemekezeka Ambuye Joseph Mukasa Zuza ayamikira yemwe anali woyimira Papa kuno ku Malawi Monsinyo Hubertus Maria Van Megen kamba ka ntchito...
View ArticleMAANJA 30,000 AKUPINDULA NDI CADECOM KU DEDZA
Maanja oposa 30,000 akupindula kudzera ku pulojekiti yothandiza anthu kuti azikhala ndi chakudya chokwanira yomwe inakhazikitsidwa ndi bungwe lampingo wakatolika la Catholic Development Commission in...
View ArticleAKHRISTU ATSOGOZE MULUNGU MMAUDINDO AWO PA NDALE
Akiepisikopi wa Akidayosizi ya Lilongwe ya mpingo wakatolika Ambuye Tarcizius Ziyaye apempha akhristu kuti alimbikitse ndi kupempherera anzawo omwe akupikisana nawo pa chisankho cha pa 20 May ponena...
View ArticleMWAMUNA ADULA ZIWALO ZOBISIKA ZA MKAZI WAKE
Mayi wazaka 26 ali pa ululu waukulu mwamuna wake atamudula ziwalo zobisika mboma la Machinga. Mayiyu yemwe anachitiridwa za nkhanzazi pa 8 mwezi uno māmudzi mwa Ellioti mfumu yayikulu Nkula mboma la...
View ArticleCADRINAL NJUE AFIKA KU MALAWI
Cardinal John Njue wafika ku Malawi kuzakhala nawo pa msonkhano wa nambala 18 wa bungwe la atsogoleri ampingo wakatolika māmaiko amchigawo cha AMECEA omwe ukuyamba pa 16 july mpaka 26 July ku Bingu...
View ArticleMA EPISKOPI AKU AMERICA AYAMIKIRA AMECEA
Mpingo wa katolika mdziko la United States ndi bungwe la Catholic Relief Services[CRS] ayamikira bungwe la Association of Member Episcopal Conferences in Eastern Africa [AMECEA] kamba kodzipeleka pa...
View ArticleAMECEA IYAMIKIRA MUTHARIKA POKHALA PULEZIDENTI
Bungwe la Association of Member Episcopal Conferences in Eastern Africa (AMECEA) layamikira Pulezidenti wa dziko la Malawi Prof Peter Mutharika chifukwa chakupambana kwake pa chisankho chomwe...
View ArticleAmbuye Ziyaye alandira PALLIUM
Akiepiskopi wa Akidayosizi ya Lilongwe Ambuye Tarcisius Ziyaye athokoza mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Fransisko chifukwa chowapatsa Pallium yatsopano chomwe ndi chizindikiro...
View ArticleAepiskopi aku Amecea alandira chilimbikitso cha Papa
Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Fransisko wafunira mafuno abwino nthumwi za ku nsonkhano wa atsogoleri a mpingowu mdera la AMECEA omwe uli mkati ku Bingu International Conference...
View ArticleAmbuye Mtumbuka atsindika za udindo wa sukulu za ukachenjede mu mpingo
Episkopi wa dayosizi ya Karonga ya mpingo wa katolika Ambuye Martin Mtumbuka omwe akuchita nawo msonkhano wa bungwe la Association of Member Episcopal Conferences in Eastern Africa (AMECEA) mumzinda wa...
View ArticleAmbuye Ziyaye alandira PALLIUM
Akiepiskopi wa Akidayosizi ya Lilongwe Ambuye Tarcisius Ziyaye athokoza mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Fransisko chifukwa chowapatsa Pallium yatsopano chomwe ndi chizindikiro...
View ArticleChikondwelero Cha Maimbidwe Cha Radio Maria Choir Festival
Komiti yomwe ikuyendetsa chikondwelero cha mayimbidwe cha Radio Maria Choir Festival chomwe chichitike loweruka pa 22 November yati zokonzekera zonse za mwambowu zili kumapeto. Chikondwelerochi...
View ArticleAnthu anayi amwalira ndi matenda a Ebola mdziko la Mali
Pafupifupi anthu mazana asanu ndi limodzi (600), ali pakawuniwuni wa matenda a Ebola mādziko la Mali. Anthuwo akuwunikidwa ndi azaumoyo pamene dzikolo likupitiliza kuyesetsa kuti matendawa omwe apha...
View ArticleChisankho Chapadera Cha Pulezidenti Mdziko la Zambia Chichitika Mwezi wa January
Chisankho cha pulezidenti chapadera mdziko la Zambia chichitika pa 20 January chaka cha mawa pofuna kupeza mtsogoleri yemwe alowe mmalo mwa mtsogoleri wakale wa dzikolo malemu Micheal Sata. Mtsogoleri...
View Article