Nyumba zofalitsa nkhani mdziko muno azipempha kuti zizilemba zoona zokhudza...
Nyumba zofalitsa nkhani m`dziko muno azipempha kuti zizilemba nkhani zoona zokhazokha zokhudza matenda a EDZI. Mkulu wogwilizira udindo woona za mapologalamu ku bungwe la National Aids Commission (NAC)...
View ArticleMpingo wakatolika mdziko la South Sudan udzudzula za mchitidwe wakupha
Mpingo wakatolika mdziko la South Sudan wadzudzula achiwembu omwe apha meya wa mzinda wa Yei womwenso ndi likulu la dayosizi ya mpingowu mdzikolo. Mai Cecelia Tito anasankhidwa kukhala meya wa mzindawo...
View ArticleAkuluakulu a Bungwe la Utumiki wa Apapa Ayamikira Akhristu a Mpingo...
Akuluakulu a bungwe la utumiki wa apapa la Pontifical Missionary Societies PMS mmaiko a Britain ndi Ireland ayamikira akhristu a mpingo wakatolika mdziko muno kamba ka chidwi chawo pankhani...
View ArticleMutharika Awonetsetsa kuti Ndalama ya Kwacha Isapitilire Kugwa
Pulezident wa dziko lino Professor Arthur Peter Mutharika wati boma lake lichita chotheka powonetsetsa kuti mphamvu ya ndalama ya kwacha isapitilire kugwa. Mtsogoleriyu amalankhula izi lachitatu pa...
View ArticleAsilikali Achita Ziwonetsero Mdziko la Ivory Coast
Nduna ya zachitetezo mdziko la Ivory Coast a Paul Koffi Koffi alamula asilikali mdzikolo kuti abwelere mmalo awo ogwilira ntchito kamba koti achitapo kanthu pa zomwe asilikaliwo akudandaula....
View ArticleDotolo Amwalira Atadwala Matenda a Ebola
Dotolo wina wa mpingo wakatolika amene wakhala akudzipeleka kwambiri pothandiza anthu odwala matenda a Ebola mdziko la Siera Lione akuti wamwalira atapezeka ndi matendawa. Dotoloyo Martin Saliya yemwe...
View ArticleKusamvana Kwakula Pakati pa Dziko la Israel ndi Palestine
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco wapempha atsogoleri a mayiko a Israel ndi Palestine kuti athetse kusamvana komwe kwakhala kukuchitika pakati pa mayiko awiriwa. Kusamvana...
View ArticleBeam Trust Yakonzeka Kulimbikitsa Amayi pa Chuma
Bungwe la Beautify Malawi (BEAM) TRUST lati posachedwapa liyamba kulimbikitsa amayi komanso asungwana kukhala odzidalira pachuma pamwamba pa ntchito zake zowonetsetsa kuti mdziko muno muli ukhondo....
View ArticleSt Patricks Mangochi Cathedral Itenga Chikho cha Radio Maria Malawi Choir...
Kwaya ya St Patricks yochokera ku Mangochi Cathedral mu dayosizi ya Mangochi, ndi yomwe yatenga chikho cha chaka chino cha chikondwerero cha mayimbidwe cha Radio Maria Malawi Choir Festival 2014....
View ArticleBungwe la CADECOM Lilimbikitsa Alimi Kukhala Odzidalira
Bungwe lowona za chitukuko mumpingo wa katolika la Catholic Development Commission in Malawi (CADECOM) m`boma la Dedza lakhazikitsa ntchito ya zaka zitatu yotchedwa Zuze Intergrated Food Security...
View ArticleChipani cha Patriotic Front Chayimika Pulezidenti Scott Kukhala Membala wa...
Chipani cholamula mdziko la Zambia cha Patriotic Front chayimika Pulezidenti wadzikolo Guy Scott kukhala membala wachipanicho kwa miyezi iwiri. Chipanicho chayimika Pulezidenti Scott yemwe...
View ArticleMonsinyo Tamani Ayamikira Akhristu a ku St Cecilia Sigerege
Akhristu a ku St Cecilia ku St James Catholic Parish ku Chilomoni a mpingo wakatolika mu Akidayosizi ya Blantyre awayamikira kamba kochitapo kathu pomanga tchalitchi lawo modzidalira. A Vicar General...
View ArticleMafumu Apemphedwa Kuchitapo Kanthu pa Ngozi Zogwa Mwadzidzidzi
Bungwe la zachitukuko mu mpingo wakatolika la Cadecom mu Dayosizi ya Chikwawa lapempha mafumu onse opezeka mu dayosiziyo kuti achite zomwe angathe kuti ateteze anthu awo ku ngozi zogwa mwadzidzi zomwe...
View ArticleMnyamata Wina Aphedwa ndi Mfuti Yosema
Bambo wina wa zaka 61 zakubadwa ali m’manja mwa apolisi m’boma la Neno kamba komuganizira kuti wapha m’bale wake pomuwombera ndi mfuti yochita kusema. Ofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo a Raphael...
View ArticleAchinyamata Apemphedwa Kukhala Odzisunga
Dayosizi ya Mangochi ya mpingo wakatolika yapempha achinyamata mudayosiziyo kuti adzisunge pofuna kuti adzathe kukwaniritsa utumiki wawo mtsogolo. Mlembi wamkulu wowona za chiyitanidwe mu dayosiziyi...
View ArticleNthumwi za Bungwe la Utumiki wa Apapa Ziyamikira Mpingo wa Katolika ku Malawi
Nthumwi zoyimilira mabungwe a utumiki wa a papa la Pontifical Missionary Soceties (PMS) zochokera m’mayiko a Ireland ndi England zati zakhutira ndi momwe mpingo wakatolika mu Diocese ya Zomba...
View ArticleMalawi Angatukuke ndi Miyala ya Mtengo Wapatali
Boma lati lili ndi chikhulupiriro chakuti mdziko muno muli miyala yambiri ya mtengo wapatali yomwe ingathe kugwiritsidwa ntchito potukulira chuma cha dziko lino. Wachiwiri kwa mkulu wowona...
View Article