Kapani ya candlex yankhazikitsa makina atsopano wopangila katundu.
Kapani ya candlex mdziko muno yankhazikitsa makina atsopano wopangira katundu ngati njira imodzi yofuna kuti mitengo ya katundu wawo inkhale yotsika mtengo. Mkulu woona zopanga ndikugula katundu...
View ArticlePapa Franscico Wavomeledza Nthumwi Zamabungwe ku Msonkhano Wonkhudza Mabanja.
Mtsogoleri wampingo wa Katolika padziko lonse Papa Francisco wavomereza nthumwi za mmabungwe pafupifupi makumi anai a maepiskopi zomwe zikuyembekezeka kudzakhala nawo pamsonkhano wachiwiri wa...
View ArticleMwambo Wansembe Ya Ukalistia Opemphelera Akhristu Opita ku Yerusalemu...
Mwambo wa Nsembe ya Ukaristia opemphelera ulendo okayendera malo oyera mdziko la Israel wachitika lachitatu ku Parish ya St Patricks mu Arkdayosizi ya Lilongwe. Akhristu oposa makumi anayi ndiwomwe...
View ArticleBoma likuyembekezeka kukhazikitsa Bugwe loona za Bata ndi Mtenderee dziko Muno
Boma likuyembekezeka kukhazikitsa nthambi yapadera yowonetsetsa kuti anthu mdziko muno akupitiliza kukhala mwa bata ndi mtendere. Mmodzi mwa akuluakulu a mabungwe omenyelera ufulu wa anthu mdziko muno...
View ArticleBungwe la Episcopal Conference of Malawi Liri ndi Mlembi Watsopano.
Mlembi watsopano wabungwe la maepiskopi mdziko muno la Episcopal conference of Malawi Bambo Henry Saindi ati apitiliza kudzipereka potumikira Mulungu pogwiritsa ntchito mphatso zomwe ali nazo pofunanso...
View ArticleMA EPISKOPI AKU AMERICA AYAMIKIRA AMECEA
Mpingo wa katolika mdziko la United States ndi bungwe la Catholic Relief Services[CRS] ayamikira bungwe la Association of Member Episcopal Conferences in Eastern Africa [AMECEA] kamba kodzipeleka pa...
View ArticleAMECEA IYAMIKIRA MUTHARIKA POKHALA PULEZIDENTI
Bungwe la Association of Member Episcopal Conferences in Eastern Africa (AMECEA) layamikira Pulezidenti wa dziko la Malawi Prof Peter Mutharika chifukwa chakupambana kwake pa chisankho chomwe...
View ArticleAnthu Achiwembu Avulaza a Polisi Mdziko la Burundi.
Apolisi khumi ndi mmodzi avulazidwa mu mzinda wa Bujumbura mdziko la Burundi pachiwembu chomwe anthu ena anachita. Anthuwo akuti anachita zachiwembu za mtunduwu mmalo osiyanasiyana ogwilira ntchito a...
View ArticleMa Sisiteli Apereka Zipangizo pa Chipatala Chaching’ono cha Mayaka .
Asisteri achipani cha daughters of wisdom lolemba anapereka zipangizo zosiyanasiyana zothandizira pachipatala chaching’ono cha Mayaka m’boma la Zomba. Polankhula ndi Radio Maria Malawi Sister Ireen...
View ArticleVuto lakusowa kwa Chipatala Chachikulu Cha Boma Likupitilira Mboma la Phalombe.
Khonsolo ya boma la Phalombe yalonjeza kuti ipereka kuboma madandaulo aanthu am’bomalo omwe atopa ndi vuto lakusowa kwa chipatala chachikulu. Akuluakulu akukhonsoloyi anena izi lolemba atalandira...
View ArticleZokonzekera Chikodwerero Choti Dayosisi ya Chikwawa Yatha Zaka 50 Zikuyenda...
Zokonzekera chikondwerero choti Dayosisi ya Chikwawa yatha zaka 50 chiyikhazikitsileni mdziko muno akuti ikuyendabwino. Ambuye Musikuwa amu Dayosisiyi anena izi poyankhula ndi Radio Maria ndipo...
View ArticleBungwe la Episcopal Conference of Malawi Layamba Zokambirana Zapachaka...
Msonkhano wachiwiri wapachaka wa bungwe la maepiscope a mpingo wa katolika la Episcopal Conference of Malawi (ECM) wayamba mudzinda wa Lilongwe. Malinga ndi chikalata chomwe bungweli latulutsa...
View ArticleMavuto a Mmbanja Amavutitsa Ana.
Popitiliza kusinkhasinkha nkhani zokhudza banja, mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco wati ndi okhudzidwa ndi mavuto omwe amachitika mmaanja maka amene amaika ana pamavuto. Iye...
View ArticleRadio Maria Malawi Iyamikira Akhristu Pothandiza pa Mariatona
President wa Radio Maria Malawi a Nicholus Chonde wayamikira akhristu omwe akhala akuchitapo kanthu pothandiza Radio Maria Malawi m’masiku a Mariatona kuyambira pa 15 May mpaka pa 27 June 2015 yomwe...
View ArticleMunthu Yemwe Wapha Anthu Ena Mdziko la Tunisia Anachita Kuthandizidwa
Malipoti ochokera mdziko la Tunisia ati munthu yemwe wapha anthu 38 pa malo ena okopera alendo lachisanu lapitali mdzikolo anathandizidwa ndi anthu ena omwe sakudziwika kuti achite chiwembucho....
View ArticleNtchito Yoponya Voti Mdziko la Burundi Siyidayambe Bwino
Ntchito yoponya voti pa chisankho cha aphungu ndi makhansala mdziko la Burundi siyidayambe bwino, anthu omwe sakudziwika ataponya mabomba mmalo oponyera voti mumzinda wa Bujumbura ndinso mmadera ena...
View ArticleUlendo wa Papa Francisco Mdziko la USA Udzakhala Wopindula
Maepiskopi a mpingo wa katolika mdziko la United States ati akuyembekezera kuti ulendo wa Papa Francisco mdzikolo womwe uchitike mmwezi wa September udzakhala wopindula. Malipoti a Catholic News...
View ArticlePapa Francisco Ayendera Papa Benedicto Wopuma
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco lachiwiri anakachezera mtsogoleri wakale wa mpingowu wopuma Papa Benedicto wa XVI yemwe wapita ku nyumba ya Papa ku dera la Castel Gandolfo...
View ArticleAtsikana 170 Awotchedwa Mdziko la Sudan
Asilikali a kummwera kwa dziko la Sudan awotcha asungwana pafupifupi 170 kamba ka nkhondo ya pa chiweniweni yomwe ikuchitika mdzikolo. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC asungwanawa atagwidwa ndi...
View ArticleMakampani Opanga Zakumwa Mdziko Muno Apereka Katundu Osiyanasiyana ku...
Makampani opanga zakumwa a Carsberg Malawi komanso Southern Bottlers apereka katundu osiyanasiyana othandizira pachipatala chachikulu cha Zomba. Popereka katunduyu mneneri wa kampani ya Southern...
View Article