Khansa ya Khomo la Chiberekero, Chiwopsezo Cha Miyoyo ya Amayi
Nthenda ya khansa ya mchiberekero akuti ndi imodzi mwa matenda omwe akupitilira kutenga miyoyo ya amayi kamba koti amayi ambiri samapita kukayezetsa kuti adziwe ngati ali ndi matendawa kapena ayi....
View ArticleMzimayi Afa ndi Nthaka Yogumuka
Mayi wa zaka 62 wamwalira ndipo ena awiri awagoneka pachipatala cha Dowa atavulala kwambiri nthaka itawagumukira m’boma la Dowa. Mneneri wa apolisi m’bomalo Sergent Richard Kaponda watsimikiza za...
View ArticleDziko la Zimbabwe lati Libweza Malo omwe Lidalanda kwa Azungu
Dziko la Zimbabwe lati libweza malo omwe lidalanda azungu zaka khumi ndi zisanu zapitazo pofuna kubwezeretsa phindu lomwe dzikolo limapeza paulimi omwe azungu amachita mmalowo. Malipoti a News24 ati...
View ArticlePulezidenti Museveni Adzetsa Mtendere Mdziko la Burundi
Mtsogoleri wa dziko la Uganda Yoweri Museveni wayamba zokambirana zofuna kudzetsa mtendere pakati pa boma ndi magulu otsutsa mdziko la Burundi pomwe magulu otsutsawo sakugwirizana ndi mfundo yoti...
View ArticlePapa Benedicto Abwelera ku Vatican
Mtsogoleri wopuma wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Benedicto wa 16 wabwelera ku likulu la mpingowu ku Vatican atakhala sabata ziwiri ku nyumba ya a Papa ya Castel Gandolfo mdziko la Italy....
View ArticleVuto la Madzi Lakula Mdera la Mchesi
Anthu okhala ku Mchesi m’boma la Lilongwe apempha boma kuti liyambe msanga kupereka madzi awukhondo pogwiritsa ntchito mipopi yomwe idamangidwa kale mderalo. Malinga ndi m’modzi mwa anthu okhudzidwa...
View ArticleAtsogoleri Mmadera Akhale Patsogolo Pokhwimitsa Chitetezo
Apolisi m’boma la Balaka apempha atsogoleri a mmagulu osiyanasiyana kuti atengepo gawo lalikulu pantchito yokhwimitsa chitetezo m’bomalo. Mkulu owona ntchito za apolisi akumidzi m’bomalo Sub-Ispector...
View ArticlePapa Francisco wati Ntchito za Migodi Zikomere Anthu Okhala Moyandikana ndi...
Mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco,wapempha mayiko kuti adziwonetsetsa kuti ntchito za migodi zomwe zikuchitika mmayiko awo zikuchitika mokomera anthu onse maka oyandikana ndi...
View ArticleAtsogoleri a Zipani Zotsutsa Sapikisana Nawo pa Chisankho cha Pulezidenti...
Pamene chisankho cha pulezidenti mdziko la Burundi chikuyembekezeka kuchitika lachiwiri, mtsogoleri wa dzikolo Pierre Nkurunziza ati akuyembekezeka kupambana pa chisankhochi zomwe zichititse kuti...
View ArticleMutharika Wati Boma Lake Silatsankho
Mtsogoleri wadziko lino Professor Arthur Peter Mutharika wati sizowona zomwe anthu ena akumanena zoti boma lake limapanga tsankho posankha anthu m'maudindo. Mutharika amayankhula izi lamulungu...
View ArticleMayi Banda ndi Okhudzidwa ndi Imfa ya a Nyondo
Pamene atsogoleri osiyanasiyana pandale akupitiliza kusonyeza kukhudzidwa kwawo ndi imfa ya mtsogoleri wachipani cha National Salvation Front NASAF a James Nyondo, mtsogoleri wakale wa dziko lino mayi...
View ArticleAnthu 15 Afa ndipo 10 Avulala Atawomberedwa
Anthu khumi ndi asanu aphedwa ndinso ena khumi avulala atawomberedwa ndi anthu ena omwe anakwera ngamila mdziko la Sudan. Mmodzi mwa anthu omwe avulala pachiwembucho wawuza atolankhani kuchipatala...
View ArticleNthambi za Chitetezo Zidzudzula za Imfa ya Msilikali
Nthambi za chitetezo mdziko muno za Polisi ndi Army zadzudzula imfa ya msilikali wa Army yemwe anaphedwa ndi apolisi loweruka pa 22 November nthawi ya 11 koloko usiku mumzinda wa Zomba. Akuluakulu...
View ArticlePapa Frascisco Asayina Mgwirizano Woteteza Chilengedwe ndi Kuthetsa Mchitidwe...
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francis wasayinirana mgwirizano ndi akuluakulu a m’mizinda ochokera mmaiko osiyanasiyana wofuna kuteteza chilengedwe komanso kuthetsa mchitidwe...
View ArticleBanki Yaikulu pa Dziko lonse Ithandiza Dziko la Nigeria
Banki yaikulu pa dziko lonse ya World Bank, yalonjeza kuti ipereka ngongole ya ndalama zokwana 2.1 biliyoni za America zothandiza kukonzera madera ena omwe gulu la zauchifwamba la Boko Haram...
View ArticleAnthu 40 Afa pa Nyanja ya Mediterranean
Anthu pafupifupi makumi anayi amila mu nyanja ya Mediterranean mdera lina lomwe lili kufupi ndi dziko la Libya bwato lomwe anakwera litamila. Panthawiyi anthuwo ati anali paulendo opita mmayiko...
View ArticleDayosizi ya Mangochi Ichita Chikondwelero cha Nkhoswe Yake
Ntchito yokonzekera mwambo wokondwelera nkhoswe ya Dayosizi ya Mangochi yomwe ndi Augustino woyera ikupitilira. Polankhula ndi Radio Maria Malawi mkulu woona zautumiki mu dayosiziyi Bambo Raphael Nkuzi...
View ArticlePulezidenti Obama Ayendera Dziko la Kwawo
Mtsogoleri wadziko la America Barrack Obama wafika mdziko la Kenya paulendo wake ocheza mdzikolo, pomwenso akuyembekezeka kukambirana ndi atsogoleri a dzikolo pa nkhani zosiyanasiyana. Paulendowu...
View ArticleA ku Banja Adzudzula Madonna Polephera Kusunga Lonjezo
Katswiri woyimba nyimbo za chamba cha POP wa mdziko la America Madonna, amudzudzula kamba kolephera kusunga lonjezo lomwe anapereka kwa makolo a mwana yemwe anamutenga mdziko muno kuti akamulere mdziko...
View ArticleBuhari Akumana ndi Pulezidenti wa Dziko la Cameroon
Mtsogoleri wa dziko la Nigeria Muhammadu Buhari lachitatu akuyembekezeka kukakumana ndi mtsogoleri wa dziko la Cameroon a Paul Biya kuti akakambirane mfundo zofuna kuthetsa gulu la zauchifwamba la Boko...
View Article