Ophunzira a YCS Akhale Owonetsa Makhalidwe Abwino-Bambo Mwakhwawa
Ophunzira a mpingo wa katolika msukulu za sekondale mdziko muno awapempha kuti akhale owonetsa makhalidwe abwino. Mkulu wa ku ofesi yoona za utumiki wa apapa ya Pontifical Missionary Societies (PMS) ku...
View ArticleNtchembere Zandonda Zawononga Kwambiri Mbewu mu Machinga ADD
Ofesi yoyang’anira ntchito za ulimi m’maboma a m’chigawo cha ku m’mawa cha dziko lino ya MachingaADDyadandaula kaamba ka zilombo zina zomwe zikuwoneka ngati ntchembere zandonda zomwe ati zakhudza mbewu...
View ArticleAnthu Khumi Afa pa Ngozi ya pa Nyanja ya Indian
Anthu khumi afa ndipo ena asanu ndi awiri apulumutsidwa boti lomwe anakwera litagubuduzika pa Nyanja ya Indian mdziko la Sri Lanka. Anthu omwe anali mu botili ati anakachita nawo chikondwelero cha...
View ArticleAchinyamata Alimbikitsidwe pa Moyo wa Uzimu-Bambo Kalasi
Achinyamata ati akuyenera kulimbikitsidwa pa umoyo wao wachikhristu kaamba koti amakhala akukumana ndi zinthu zambiri zowabweza mmbuyo pa nkhani ya chikhulupiliro. Mkulu woyang’anira bungwe la...
View ArticleBungwe la FAWO Lati Amayi Amasiye Akhale Odzidalira
Bungwe lomenyela ufulu wa amayi ndi ana amasiye mdziko muno la Foundation for Widows and Orphans (FAWO) lati nthawi yakwana yoti amayi amasiye akhale odziyimira pawokha pa nkhani za chuma. Polankhula...
View ArticlePapa Alimbikitsa Ubale wa Mpingo wa Katolika ndi Anglican
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse papa Francisco waonetsa chitsanzo cha ubale wabwino pakati pa mpingo wakatolika ndi wa Anglican. Papa wachita izi atakayendera akhristu a mpingo wa...
View ArticleBwanamkubwa Ayamikira Sukulu ya Ukachenjede ya DMI
Bwana-mkubwa wa boma la Mangochi a James Manyetera ayamikira sukulu ya ukachenjede ya DMI yomwe imayendetsedwa ndi amsembe a mpingo wakatolika mu chipani cha Missionaries of Mary Immaculate(MMI) kamba...
View ArticleApempha Akhristu Azipemphelera a Sisteri
Ophunzira a mpingo wa katolika msukulu za sekondale mdziko muno awapempha kuti akhale owonetsa makhalidwe abwino. Mkulu wa ku ofesi yoona za utumiki wa apapa ya Pontifical Missionary Societies (PMS) ku...
View ArticleDziko la South Sudan Lalengeza Madera Omwe Akhudzidwa ndi Njala
Dziko la South Sudan lalengeza kuti mmadera ena a mdzikolo anthu akuvutika ndi njala. Malinga ndi boma la dzikolo komanso bungwe lowona za mgwirizano wa maiko a pa dziko lonse la United Nations UNanthu...
View ArticleNyumba Zosindikiza Ndi Kuwulutsa Nkhani Zizilemba Mwaukadaulo Nkhani Zokhudza...
Nyumba zotsindikiza ndi kuwulutsa nkhani mdziko muno azilimbikitsa kuti zizifufuza mokwanira komanso kulemba mwaukadaulo nkhani zokhudza anthu olumala. Wachiwiri kwa mkulu wa nthambi yophunzitsa...
View ArticleBungwe la PACHI Likulimbikitsa Uchembere Wabwino
Bungwe la Parent and Child Health Initiative (PACHI) lapempha amayi kuti azipita ku chipatala msanga akakhala oyembekezera pofuna kuchepetsa imfa zokudza kaamba ka uchembere. Mkulu woona za ma...
View ArticleAnthu Atatu Amangidwa Kamba Koba Katundu ku CADECOM
Apolisi m’boma la Balaka agwira anthu atatu omwe akuwaganizira kuti ndi amene akukhudzidwa ndi mulandu wakuba ku malo a mpingo wakatolika a CADECOM ku Ulongwe ndi ku malo a zaulimi wa nthilira a...
View ArticleMpingo Wakatolika Wati Pasakhale Lamulo Lakupha Munthu Wopha ma Alubino
Mpingo wa katolika mdziko muno wati ukugwirizana ndi ganizo la boma loti pasakhale lamulo lakupha munthu wopezeka olakwa pa mlandu wosowetsa komanso kupha anthu a mtundu wa chialubino. Mlembi wa mkulu...
View ArticleAnthu 70 Afa pa Nyanja ya Atlabtic
Matupi oposera 70 a anthu akufa akuti apezeka akuyandama kudera lina mu nyanya yayikulu ya Atlantic m’dziko la Lybia. Akatswiri pa ntchito zopulumutsa anthu pa ngozi zochitika pamadzi akuti ndi amene...
View ArticleMpingo Wakatolika Wati Pasakhale Lamulo Lakupha Munthu Wopha ma Alubino
Mpingo wa katolika mdziko muno wati ukugwirizana ndi ganizo la boma loti pasakhale lamulo lakupha munthu wopezeka olakwa pa mlandu wosowetsa komanso kupha anthu a mtundu wa chialubino. Mlembi wa mkulu...
View ArticleYCW Ikutolera Thandizo la Seminale Ya St. Peters
Bungwe la achinyamata mu mpingo wakatolika m’dziko muno la Young Christian Workers (YCW) lati likutolera thandizo pofuna kuthandiza seminale yaikulu ya St. Peters mu dayosizi ya Zomba yomwe padakali...
View ArticlePRO-LIFE Yati Kupha ma Alubino ndi Kutsutsana ndi Cholinga cha Mulungu
Bungwe loteteza miyoyo ya anthu la mpingo wa katolika la PRO-LIFE lati kupha anthu a mtundu wa chialubino ndi kutsutsana ndi cholinga cha Mulungu kaamba koti iye analenga munthu aliyense m’chifaniziro...
View ArticleAmayi Awiri Akayankha Mlandu Wopha Kim Jong-Nam
Amayi ena awiri akuyembekezeka kukawonekera ku bwalo la milandu mawa ndi kukayankha mlandu wokhudzana ndi kuphedwa kwa mchimwene wake wa mtsogoleri wa dziko la North Korea,Kim Jong-Nam. Malipoti a...
View ArticleAna Ochoka Mdziko la Libya Kupita Italy Ali pa Chiopsezo- UN
Bungwe lowona za mgwirizano wa maiko a pa dziko lonse la United Nations UNlachenjeza kuti ana ochuluka othawa kwao ochoka mdziko la Libya kupita mdziko la Italy ali pa chiopsezo. Malinga ndi malipoti...
View ArticleMa Episkopi Apempha Mayiko Athandize Anthu a Njala Mdziko la South Sudan
Ma episkopi a mpingo wa katolika mdziko la South Sudan apempha maiko akufuna kwabwino kuti athandize anthu amene akuvutika ndi njala mdzikolo. Malinga ndi chikalata chomwe ma episkopiwa alemba,...
View Article