Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live

Anthu 13, 000 Aphedwa Pa Ndende Ya Saydnaya Mdziko La Syria

Anthu oposa 13, 000 ati ndi omwe aphedwa mwachinsinsi pa ndende ya Saydnaya mdziko la Syria. Malinga ndi lipoti lomwe bungwe la Amnesty International latulutsa, anthu akhala akuphedwa pa ndendeyi...

View Article


ECM Yasankha Bambo Likutcha Kukhala Mlangizi wa Apolisi

Bungwe la ma episkopi mdziko muno la Episcopal Conference Of Malawi [ECM] lasakha Bambo Steven Likhucha kukhala  mlangizi wa apolisi  mumpingowu m’dziko muno. Bungweli  lanena izi kudzera muchikalata...

View Article


Dayosizi ya mangochi Ikhazikitsa Ntchito Yobzala Mitengo

Dayosizi ya mpingo wa katolika ya Mangochi yati ili ndi chidwi chofuna kubwezeretsa chilengedwe mchimake. Episkopi wa dayosiziyi Ambuye Montfort Stima ndi omwe anena izi pa mwambo omwe anawatsogolera...

View Article

Papa Wati Anthu a Mdziko la Myanmar Akufunika Mapemphero

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha anthu kuti apemphelere anthu a mdera la Rohingya mdziko la Myanmar omwe akuphedwa komanso kukakamizidwa kuti achoke mnyumba zao....

View Article

kubisala mvula yamphamvu yomwe imagwa ku delaro. Dziko Silingasangalatse...

Mtsogoleri wa mpingo wa Katolika pa dziko lonse Papa Francisko wati popanda amayi dziko silingasangalatse konse. Iye amalankhula izi ku mwambo wa nsembe ya Misa ku Santa Marta mu mzinda wa Vatican....

View Article


MOAM Ipempha Boma Liwunikenso Misonkho

Bungwe la eni minibus m`dziko muno la Minbus Owners Association of Malawi(MOAM) lapempha boma kuti liwunikenso  misonkho pofuna kuti ikhale yokomera anthu  ochita malonda ang’onoang’ono omwe ambiri...

View Article

Afa Atawombedwa ndi Mphenzi ku Dowa

Bambo wina wafa m’phenzi itamuomba m’boma la Dowa. Malingana ndi wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo SergeantRichard Kaponda, bambo-yu ndi Dalitso Jose yemwe anali wa zaka 38zakubadwa ndipo amachokera...

View Article

Trump Akulingalira Zosintha Pang’ono Lamulo Loletsa Mzika za Maiko a Chisilamu

Mtsogoleri wa dziko la America Donald Trump wati ali ndi malingaliro ongofuna kusintha pang’ono ganizo lake loletsa nzika za mayiko ena achisilamu kulowa mdzikolo. A Trump alengeza izi pomwe khoti lina...

View Article


MOAM Ipempha Boma Liwunikenso Misonkho

Bungwe la eni minibus m`dziko muno la Minbus Owners Association of Malawi(MOAM) lapempha boma kuti liwunikenso  misonkho pofuna kuti ikhale yokomera anthu  ochita malonda ang’onoang’ono omwe ambiri...

View Article


Anthu 7 Afa pa Chiwembu Mdziko la China

Anthu asanu ndi atatu afa ndipo ena asanu avulala potsatira chiwembu cha mipeni chomwe chinachitika mdera la Xinjiang mdziko la China. Mwa anthu omwe afawo ndi kuphatikizapo atatu omwe akuwaganizira...

View Article

Papa Francisco Wapempha Akhristu Azikhala Okondwera mu Chikondi cha Mulungu.

Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha akhristu kuti azikhala okondwera nthawi zonse mu chikondi cha Mulungu. Papa amalankhula izi lero ku likulu la mpingowu ku Vatican...

View Article

Achinyamata Azigwiritsa Bwino Ntchito Luso la Makono Pofalitsa Uthenga wa...

Achinyamata a bungwe la Young Christian Workers (YCW) mumpingo wa katolika  awalangiza kuti azigwiritsa  bwino ntchito maluso atsopano omwe akubwera mdziko muno  monga ma computer komanso internet...

View Article

Akatolika Mdziko La India Apempha Boma Litenge Gawo Mpaka Bambo Tom Apezeke

Akhristu a mpingo wakatolika mdziko la India apempha boma la dzikolo kuti likambirane ndi maiko a mchigawo chapakati chakuzambwe ndi cholinga choti atulutse bambo Tomomwe anagwidwa mdziko la Yemen ndi...

View Article


Kulowa ma Bungwe Awiri a Nkhonya ndi Kuphwanya Malamulo-MPBCB

Bungwe lalikulu loyang’anira akatswiri omenya nkhonya mdziko muno la Malawi Professional Boxing Control Board lati ndi lokhumudwa kaamba ka mchitidwe wa omenya nkhonya ena omwe akugwira ntchito ndi...

View Article

Arkidayosizi ya Blantyre Ipempha Akhristu Abwezeretse Chilengedwe

Arkidayosizi ya mpingo wa katolika ya Blantyre yalimbikitsa akhristu a mpingowu kuti abzale mitengo ngati njira imodzi yobwezeretsa chilengedwe mdziko muno. Vicar General wa arkidayosiziyi bambo...

View Article


Mwana Afa Atamira M’madzi M’boma la Mangochi

Mwana wina wa chaka chimodzi wafa atamira m’madzi m’boma la Mangochi. Izi zachitika m’mudzi mwa Chipoka mfumu yaikulu Mponda m’bomalo. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo Inspector Rodrick Maida wauza...

View Article

Kuthetsa Matola Kwachepetsa Ngozi M’boma la Mangochi

Kuletsa kwa galimoto za matola m’boma la Mangochi ati kwathandiza kubweretsa bata pa nsewu komanso kuchepetsa ngozi za pansewu m’bomalo. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo inspector Rodrick Maida...

View Article


Bambo wina wadzipha Podzimangilira

Bambo wina wa zaka 49 zakubadwa wa mmudzi mwa Steven mdera la mfumu yaikulu Chowe m’boma la Mangochi wafa kaamba kodzimangilira mu mtengo. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo Inspector Rodrick Maida...

View Article

Anthu Omwe Akuthandizidwa ndi CADECOM Akhale Odziyimira Pawokha-Ambuye Stima

Episkopi wa dayosizi ya mpingo wa katolika ya Mangochi Ambuye Montfort Stima apempha anthu omwe akuthandizika ndi bungwe lowoona za chitukuko mu mpingowu la CADECOMkuti akhale odziyimira pawokha...

View Article

Misa ya Mwezi ndi Mwezi Ikuthandiza Amayi a Katolika Kuzama pa Chikhristu

Amayi a mpingo wa katolika mu parishi ya Chisitu mu arkidayosizi ya Blantyre ati miyoyo yawo ya chikhristu ikuzama pomwe akumakhala ndi mwambo wa nsembe ya ukaristia  mwezi ndi mwezi. Mkhalapampando wa...

View Article
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>