Monsinyo Tamani Apempha a Malawi Azithandizana pa Nkhani ya Njala
Arkidayosizi ya Blantyre ya mpingo wakatolika yalimbikitsa a Malawi kuti azithandizana okhaokha pamene anthu ena akhudzidwa ndi vuto la njala. Vicar General wa Arkidayosiziyi Monsinyo Boniface Tamani...
View ArticleBoma Lipempha Anthu Asamalire Nkhalango ya Dzalanyama
Boma lapempha anthu omwe amakhala malo ozungulira nkhalango ya Dzalanyama mu mzinda wa Lilongwe kuti asunge mitengo ya mu nkhalangoyi ndi cholinga chofuna kuchepetsa vuto la kuvuta kwa madzi mu...
View ArticleAnthu 26,000 Athawa Mu Mzinda Wa Mosul
Anthu okwana 26 sauzande a m’dziko la Iraq athawa kum’mvuma kwa mzinda wa Mosul pa masiku okwana khumi 10 potsatira kumenyana komwe kunabuka pakati pa asilikali a dzikolo ndi zigawenga za Islamic State...
View ArticleAtumiki a Radio Maria Malawi Awapempha Akhale Olimbikira Pofalitsa Uthenga wa...
Anthu omwe amagwira ntchito modzipereka ku Radio Maria Malawi awalimbikitsa kuti asamabwelere m’mbuyo pomwe akukumana ndi zovuta pa nthawi yomwe akutumikira. Bambo Edwin Lambulira alankhula izi...
View ArticlePresident Hosni Mubarak Wapezeka Wosalakwa
Bwalo lalikulu lamilandu la apilo mdziko la Egypt lapeza osalakwa yemwe anali mtsogoleri wakale wa dzikolo a Hosni Mubarak pa mlandu ozunza ndi kupha anthu mazanamazana pa ziwonetsero zomwe zinachitika...
View ArticlePapa Alimbikitsa Kubwezeretsa Chilengedwe
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wagwirana manja ndi bungwe la ma Episkopi a mpingo wakatolika m’dziko la Brazilpa ntchito yobwezeretsa chilengedwe. Papa wati mpingo...
View ArticlePatron Akondwera ndi Bungwe la YCS mu Arkidayosizi ya Lilongwe
Patron wa bungwe la ophunzira a chikatolika msukulu za sekondale la Young Christian Students (YCS) a Phillip Nsinawana Mwale ayamikira momwe ntchito za bungweli zikuyendera mu arkidayosizi ya Lilongwe....
View ArticleWapolisi Wosowa Wapezeka Atafa Atazimangilira
Wapolisi yemwe anasowa ku Police College mu mzinda wa Zomba wapezeka atafa atadzimangilira ku minda ya ku Chancellor College mu mzindawo. Mkulu wofalitsa nkhani mchigawo cha kummawa cha dziko lino...
View ArticleAsilikali Apirikitsa Zigawenga za IS mu Mzinda wa Palmyra Mdziko la Syria
Asilikali a mdziko la Syria mogwirizana ndi a mdziko la Russia alanda ndi kupirikitsa zigawenga za chisilamu za Islamic State IS mu mzinda ya Palmyra mdziko la Syria. Malinga ndi malipoti a wayilesi ya...
View ArticlePapa Wapempha Ansembe Akhale a Chiyembekezo, Chikhulupiliro
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati ansembe akuyenera kukhala a chiyembekezo chabwino mmoyo wao pokumbukira zimene Mulungu anawalonjeza komanso pokhala a chikhulupiliro....
View ArticleAsilikali a Iraq Alanda Mlatho wa Tigris ku Zigawenga za IS
Asilikali a mdziko la Iraq ati alanda mlatho wa ufulu wa mtsinje wa Tigris mu mzinda wa Mosul ku zigawenga za chisilamu za Islamic State IS. Malipoti a wailesi ya BBC ati mlathowu ndi wachiwiri pa...
View ArticleMBS Itseka Golden Peacock, Pacific Hotel
BungweMalawi Bureau of Standards (MBS) layamba latseka nyumba zogona alendo za Golden Peacock komanso Pacificmu mzinda wa Lilongwe kaamba koti zikusowa zinthu zina zolimbikitsira ntchito za ukhondo....
View ArticleJonathan Watsutsa Kuti Analetsa Boma la America Kugwira Ntchito ndi Boma Lake
Mtsogoleri wakale wa dziko la Nigeria Goodluck Jonathan watsutsa malipoti akuti anakana kuti asilikali a mdziko la America athandize pa ntchito yopulumutsa atsikana oposera 200 omwe anagwidwa ndi...
View ArticleAsisteri Anayi Afa pa Ngozi mdziko la Ethiopia
Asisiteli anayi afa ndipo ena atatu avulala modetsa nkhawa pa ngozi ya galimoto mdziko la Ethiopia. Malingana ndi malipoti a Catholic News Agency (CNA), a sisiteliwa omwe ndi achipani cha Daughters of...
View ArticleAnthu 20,000 a Mdziko la Myanmar Athawira Mdziko la China
Anthu othawa kwawo oposa 20 thousand a mdziko la Myanmar ati alowa mdziko la China pothawa zamtopola zomwe zinabuka kummwera cha kummawa kwa maiko a mchigawo cha Asia. Malinga ndi malipoti padakali...
View ArticlePapa wati Munthu Akuyenera Kukumana ndi Zovuta pa Moyo wake
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati munthu sangakule popanda kukumana ndi zovuta zosiyanasiyana mu chikhulupiliro chomwe ali nacho mwa Mulungu. Papa amalankhula izi ndi...
View ArticleDziko la Guatemala Litaya Atsikana Makumi Awiri pa Ngozi ya Moto
Dziko la Guatemala lakhazikitsa masiku atatu okhudza maliro a atsikana makumi awiri omwe amwalira kaamba ka moto omwe unabuka pa malo ena osungirapo ana mdzikolo. Malipoti ati atsikana omwe amwalirawa...
View ArticleDziko La Japan Lipereka 112 Sauzande Dollars Zomangira Sukulu M’boma La...
Boma la dziko la Japan lapereka ndalama zokwana 112 thousand 984 za America ku boma la dziko lino zothandizira kumangira sukulu ya sekondale yoyendera ya Chikangulu m’boma la Chiradzulu. Polandira...
View ArticleApempha Amayi Azitanganidwa Kukweza Dziko, Miyoyo Yawo
Amayi ochokera m’mipingo yosiyanasiyana m’dziko muno awapempha kuti azikonda kutanganidwa ndi zinthu zomwe zingathandize pa chitukuko cha miyoyo yawo ndi dziko lino. Mayi Trizer Masauli omwe...
View ArticlePMS Yapempha Asemino Akhale Patsogolo mu Utumiki wa Apapa
Bungwe la utumiki wa a Papa mdziko muno la Pontifical Mission Socities PMS lati asemino akuyenera kukhala patsogolo kudziwa zomwe bungwe la utumiki wa apapa limachita. Mkulu wa bungweli mdziko muno...
View Article