Quantcast
Channel: Radio Maria Malawi
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live

Anthu 20 Afa Pa Chiwembi China M’dziko La America

Anthu makumi awiri (20) afa ndipo ena oposera zana limodzi (100) avulala modetsa nkhawa bomba litaphulika pa hotela ina mu m’dzinda wa las Vegas m’dziko la United States Of America. Malipoti a BBCati...

View Article


President Muthalika Wafika Mdziko Muno.

M’tsogoleri wa dziko lino Professor Arthur Peter Mutharika wafika m’dziko muno kuchokera mu m’dzinda wa New York , m’dziko la United States of America, komwe anachita nawo msonkhano wa ukulu wa bungwe...

View Article


Cardinal Filon Wafika Mdziko Muno

Cardinal Fernando Filoni wafika m’dziko muno lero kuti adzakhale  nawo pa mwambo wokhazikitsa Cathedral ya dayosizi ya Karonga loweruka likudzali, m’malo mwa mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko...

View Article

Ambuye Tambala Ayamikira Parish Ya St Charles Luanga Mu Dayosizi Ya Zomba

Akhristu a mpingo wakatolika mu dayosizi ya Zomba awayamikira kamba kokhadzikitsa mulozo wa mapulani a ntchito zoyendetsera parishiyo. Episikopi wa mpingo wakatolika mu dayosizi ya Zomba olemekezeka...

View Article

Cardinal Filoni arrives in the country for Karonga Cathedral Consecration

At exactly 2:15 pm, His Eminence Fernando Cardinal Filoni arrived at Kamuzu International Airport (KIA) ahead of the consecration of St Joseph the Worker Cathedral of the Catholic Church in Karonga...

View Article


Papa Franciso Alimbikitsa Akhristu Kulimbika Popemphera Mapemphero A Kolona.

M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse papa Francisco walimbikitsa akhristu a mpingo wakatolika pa dziko lonse kuti asafooke koma kudzipereka pochita mapemphero a Kolona tsiku ndi tsiku. Papa...

View Article

Mayi Wina ku Neno Amugwira Kamba Kopha Mwana Yemwe Anabereka.

Apolisi ku Zalewa m’boma la Neno akusunga m’chitolokosi mai wina kaamba komuganizira kuti anapha mwana wake wongobadwa kumene. Ofalitsa nkhani za apolisi m’bomali Sergeant Raphael Kaliati watsimikiza...

View Article

Atsogoleri A Ndale Awapempha Kuti Azipewa Mchitidwe Wokolezera Ziwawa.

Atsogoleri a ndale m’dziko muno awapempha kuti azichita ntchito zabwino osati kulimbikitsa ziwawa. Wapampando wa bungwe la ma episikopi a mpingo wakatolika m’dziko muno la Episcopal Conference Of...

View Article


Papa Wayamikira Atsogoleri a Zipembezo Zosiyanasiyana

M'tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wayamikira atsogoleri a zipembedzo zosiyanasiyana kaamba kofika ku msonkhano umene iye anayitanitsa ku likulu la mpingowu ku Vatican. Papa...

View Article


Antchito a Mtsogoleri wa Dziko la South Korea Amangidwa

Apolisi otengera nkhani ku bwalo la milandu mdziko la South Korea apereka chilolezo kuti apolisi amange antchito awiri a mtsogoleri wa dzikolo ngati mbali imodzi yofufuza katangale amene akuchitika...

View Article

Bambo Wafa Ali Mkati Mwa Makina Osakanizira Cement Mu Mdzinda Wa Lilongwe.

Bambo wina wafa atalowa mkati mwa makina osakanizira cement a kampani ya Capital Food ku Kanengo mu m’dzinda wa Lilongwe. Malingana ndi ofalitsa nkhani za apolisi ku Kanengo a Salome Chibwana ati...

View Article

Bambo Wina Amunjata Kamba Komuganizira Kuti Wapha Mkazi Wake.

Apolisi m’boma la Mangochi akusunga m’chitokosi bambo wina amene akumuganizira kuti wapha mkazi wake . Malingana ndi wachiwiri kwa ofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo Sergent Amina Tepani Daudi bamboyu...

View Article

Msonkhano Wa ukulu wa Inclusive Education Wachitika Mboma La Mangochi

Msonkhano wa ukulu wokambilana njira zopititsira patsogolo maphunziro okomera mwana aliyense (Inclusive Education) wayamba lero m’boma la Mangochi. Unduna wa za maphunziro sayansi ndi technology...

View Article


Papa Wayamikira Atsogoleri a Zipembezo Zosiyanasiyana

M'tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wayamikira atsogoleri a zipembedzo zosiyanasiyana kaamba kofika ku msonkhano umene iye anayitanitsa ku likulu la mpingowu ku Vatican. Papa...

View Article

Antchito a Mtsogoleri wa Dziko la South Korea Amangidwa

Apolisi otengera nkhani ku bwalo la milandu mdziko la South Korea apereka chilolezo kuti apolisi amange antchito awiri a mtsogoleri wa dzikolo ngati mbali imodzi yofufuza katangale amene akuchitika...

View Article


Azaumoyo Akuyembekezeka Kuyeza Frozy

Akuluakulu zaumoyo mdziko la Mozambique ati akuyembekezeka kuti ayeze zakumwa zoziziritsa kukhosi za Frozy patangotha masiku ochepa dziko la Malawi litaletsa chakumwachi. Posachedwapa dziko la Malawi...

View Article

Awapempha Kuti Azikhala Ndi Chidwi Chotsatira Bwino Chiphunzitso Cha Mpingo

Mamembala a bungwe la Young Christian Workers (YCW) mu dayosizi ya mpingo wakatolika ya Zomba awapempha kuti azikhala ndi chidwi chotsatira bwino chiphunzitso cha mpingo wawo zomwe zingawathandize kuti...

View Article


Ambuye Msusa Apepesa Amayi kamba ka Nkhanza Zomwe Akukomana Nazo.

Arch-Dayosizi ya mpingo wakatolika ya Blantyre yati ndiyokhudzidwa kwambiri ndi nkhanza zomwe zikupitilira kuchitika pakati pa amayi m’dziko muno. Arch-Episikopi wa mpingowu mu Arch-Dayosizi-yi ,...

View Article

Dr Chilima Alimbikitsa Za Mpingo Wodzidalira .

Akhristu a mpingo wakatolika mu dayosizi ya Mangochi awapempha kuti apitilize kudzipereka pothandiza mpingo-wu molowa manja . Wachiwiri kwa m’tsogoleri wa dziko lino Dr Saulosi Chilima walankhula izi...

View Article

Athokoza Akhristu Kaamba Kozipeleka Pothandiza Mpingo

Episikopi wa Arch-Dayosizi ya Blantyre, olemekezeka Ambuye Thomas Luke Msusa wayamikira akhristu a mpingo-wu mu Arch-Dayosizi-yi kamba kodzipeleka pa mwambo wa Dinner and Dance yomwe mpingo-wu unakonza...

View Article
Browsing all 1875 articles
Browse latest View live


<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>