Radio Maria Iyamikira Akhristu a ku Mangochi Cathedral
Akhristu a mu Parish ya St.Augustine Mangochi Cathedral mu dayosizi ya Mangochi awayamikira chifukwa chothandiza Radio Maria Malawi. Mkulu woona za chithandizo ku wailesiyi Mayi Veronica Manyozo ndi...
View ArticleMpingo wa Katolika Mdziko la Iraq Wapempha Akhristu Kusala Zakudya
Mpingo wa katolika mdziko la Iraq wapempha anthu mdzikolo kuti asale zakudya lisanafike tsiku la khirisimasi, pofuna kupempha chifundo cha Mulungu pakati pa akhristu omwe athawa kuzunzidwa mdzikolo...
View ArticleYESU ADZBWERA
YESU ADZABWERA BY ST MARYS WOMEN CHOIR BANGWE PARISH ARCHDIOCESE YA BLANTYRE
View ArticlePapa Francisco Wapempha Anthu kuti Awonjezere Mapemphero Awo.
Mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco,wapempha anthu kuti apemphelere anthu omwe akhudzidwa ndi ziwembu zomwe zachitika mmaiko a Australia ndi Pakistan ,zomwe zaphetsa anthu...
View ArticleAnsembe a Chibadwiri mu Diocese ya Mangochi Achita Mbindikiro.
M’bindikiro wa sabata imodzi wa ansembe a chibadwiri mudayosizi ya Mangochi utha mawa. M’bindikirowu unayamba lolemba sabata ino ndipo ukuchitika pofuna kukonzekera kubadwa kwa Yesu Khristu, kuti nawo...
View ArticleAMATIPATSA ZABWINO
AMATIPATSA ZABWINO BY ST BERNADETTA CHOIR BANGWE PARISH BLANTYRE ARCHDIOCESE
View ArticleBungwe la Catholic Women Organization(C.W.O.) ku Malawi Lichita Msonkhano...
Msonkhano wawukulu wa bungwe la amayi la Catholic Women Organisation (CWO) wayamba dzulo ku sukulu ya sekondale ya asungwana ya Mary Mount mu mzinda wa Mzuzu. Msonkhanowu unatsekulilidwa lachinayi ndi...
View ArticleZigawenga Zipha Anthu Oposa Makumi Atatu Mdziko la Nigeria
Anthu oposa makumi atatu aphedwa ndinso ena pafupifupi zana limodzi, abedwa ndi zigawenga mmudzi wina mdziko la Nigeria. Mmodzi mwa anthu omwe apulumuka pachiwembucho,wawuza wayilesi ya BBC kuti...
View ArticleApempha Anthu Kuthandiza pa Ngongole ya Montfort Press
Arkdayosizi ya Blantyre yapempha anthu akufuna kwabwino kuti athandize arkdayosiziyi pobweza ngongole yomwe kampani yake yotsindikiza mabuku ya Montfort Press ili nayo. Arkidayosiziyi yapereka pempholi...
View ArticleAnthu 15 Mwa Anthu 100 Akusiyira Panjira Mankwala a ARV Mdziko muno.
Nthambi yowona za matenda a Edzi mu unduna wa za umoyo yati anthu khumi ndi asanu 15 mwa anthu 100 aliwonse mdziko muno akumasiyira panjira kumwa mankhwala otalikitsa moyo a ARV pa zifukwa...
View ArticleBungwe la CILIC Liyendera Odwala ndi Amndende.
Bungwe la Civil Liberties Committee (CILIC),lapempha anthu akufuna kwabwino kuti adzipereke pothandiza anthu osowa panthawi ino ya chikondwerero cha Khirisimasi ndi chaka chatsopano. Mkulu woyendetsa...
View ArticleMfumu Mlumbe Iyamikira Diocese ya Zomba.
Diocese ya Zomba ayiyamikira chifukwa chotenga gawo lalikulu lothandiza kupititsa patsogolo ntchito zokweza umoyo wa ana mu Diocese-yo. Mfumu yayikulu Mlumbe ya m’boma la Zomba ndi imene yanena izi...
View ArticleRadio Maria Malawi Ichita Chotheka Kukonza Mavuto omwe Ikukumana Nawo
Wachiwiri kwa mkulu wowona za ma programme ku Radio Maria Malawi Bambo Charles Kaponya, wati wailesiyi ichita chotheka kukonza mavuto omwe ma studio ang’onoang’ono a wailesiyi akukumana nawo mdziko...
View Article