Ark diocese Ya Blantyre Ilonjeza Kupitiriza Kuthandiza Radio Maria Malawi
Ark diocese ya Blantyre yati ipitiriza kuthandiza ntchito za Radio Maria Malawi, pofuna kuti ntchito zake zofalitsa Uthenga wa bwino zipitilire kupita patsogolo. Mkulu wowona za utumiki mu...
View ArticleKudzidalira kwa Amayi pa Chuma Kungachepetse Nkhaza zomwe Amakumana Nazo
Kudzidalira kwa amayi pa chuma akuti kungathandize kuthetsa nkhanza zochitika pakati pa amayi ndi ana m'dziko muno. Mkulu oyendetsa ntchito za bungwe la Centre for Altenatives for Victimised Women...
View ArticleBungwe la Amayi Litsindika Kufunika kwa Misonkhano ya Amayi
Amayi a mu Parish ya Kausi mu diocese ya Mangochi atsindika kufunika kwa misonkhano ya amayi yomwe ikuchitika mu dioceseyo kamba koti ikuwathandiza kukhala olimbika ndi odzipereka pa chikhristu chawo....
View ArticleArchdayosizi ya Blantyre Ichita Ubale ndi Dayosizi ya Mdziko la Mozambique
Archdayosizi ya Blantyre yayamikira ubale wabwino womwe ulipo pakati pa dayosiziyi ndi dayosizi ya Lichinga mdziko la Mozambique. Arch Episkopi wa archdayosiziyo Ambuye Thomas Luke Msusa ndi omwe...
View ArticleA Malawi Apempherere Mvula
Mtsogoleri wadziko lino professor Arthur Peter Mutharika,wapempha a Malawi kuti apemphere kuti mvula iyambe kugwa. Pulezidenti Mutharika wanena izi kudzera mchikalata chomwe nthambi yofalitsa nkhani...
View ArticleBoma Latsutsa za Kusalabadira kwa a Mutharika ku Mavuto a Dziko Lino
Boma lati sizowona kuti mtsogoleri wa dziko lino Professor Arthur Peter Mutharika sakulabadira za mavuto omwe anthu mdziko muno akukumana nawo omwe adza chifukwa cha mavuto a zachuma. Boma lanena izi...
View ArticleDayosizi ya Chikwawa Yayamikira Ntchito za Mabungwe Mpingo Wakatolika
Dayosizi ya Chikwawa yayamikira ntchito zomwe mabungwe a mu mpingo wa katolika akhala akugwira mchaka chomwe chikuthachi. Mlembi wamkulu mu dayosiziyo Bambo Patrick Jambo,ndi omwe ayamikira mabungwewa...
View ArticleAna Awiri a Banja Limodzi Afa ndipo Ena Awiri Avulala Khoma la Nyumba...
Ana awiri a banja limodzi afa ndipo ena awiri avulala khoma la nyumba yomwe anagona litagumuka ndikuwapsinja ku Machinjiri mu mzinda wa Blantyre. Anawo, Agness ndi Pemphero Chaona omwe amakhala ku...
View ArticleMu Mpingo Wakatolika Mulibe Kugawikana, Watero Papa Francisco
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati kusiyana maganizo kwa ma episikopi pa nkhani zokhudza banja,sizikutanthauza kuti mu mpingowu muli kugawikana. Papa Francisco...
View ArticleMaphunziro Angachepetse Nkhanza Pakati pa Amayi ndi Atsikana
Kulimbikitsa maphunziro a atsikana ndi njira yabwino yomwe ingathandize dziko lino pothana ndi m’chitidwe wa nkhanza pakati pa amayi ndi atsikana. M’modzi mwa aphungu omwe ali ndi luso la mayimbidwe ku...
View ArticleAna Awiri Afa Atamira pa Dziwe la Madzi
Ana awiri a banja limodzi m’boma la Dowa afa atamira padziwe la madzi m’bomalo. Ofalitsa nkhani za apolisi mbomalo Sergent Richard Kaponda watsimikiza za nkhaniyi ndipo wati anawo anamwalira...
View ArticleMa episkopi Mdziko la America Adzudzula Apolisi
Maepisikopi a mdziko la America adzudzula apolisi ku mchitidwe omawopseza anthu oganiziridwa milandu omwe akuti wakula kwambiri mdzikolo. Ma episikopiwa adzudzula apolisiwo zitamveka kuti iwo...
View ArticleMakolo M’boma la Nsanje Apitiriza Kutsatira Myambo ina Yoyipa.
Makolo ena ku nsanje akupitirizabe kuchita miyambo ina yoipa monga kukwatiwitsa ana akadali achichepere komanso kuwagwiritsa ntchito zokhwima zomwe ati zikumakolezera ana ambiri kusiya sukulu. Mkulu...
View ArticleHostel ya Atsikana Imangidwa pa Secondary ya Liwonde M’boma la Machinga.
Kumangidwa kwa hostel ya atsikana pa sukulu ya Secondary ya Liwonde m’boma la Machinga kuthandiza kuti atsikana ambiri ayambe kuchita bwino pa maphunziro awo. Mphunzitsi wa mkulu pa sukuluyi a Welson...
View ArticleKusowa kwa Mauthenga pa Nkhani za HIV ndi AIDS Kukulimbikitsa Kufala kwa...
Mafumu m'boma la Mwanza apempha boma ndi mabungwe kuti alimbikitse ntchito yolimbana ndi kufala kwa ka chilombo ka HIV komwe kamayambitsa matenda a Edzi. Mfumu yaikulu Kanduku ya m'bomalo ndiyomwe...
View ArticleKupempherera Atumiki Ampingo ndi Udindo wa Akhirisitu
Akhristu ampingo wa katolika ati ali ndi udindo opepherela atumiki a mumpingowu kuti asataye utumuki wawo. Episcope wa arkdiyosizi ya Blantyre Ambuye Luke Msusa ndiwo anena izi pamwambo wa malumbiro...
View ArticleApempha Thandizo La Ana Osamva Komanso Osalankhula
Sukulu ya ana osamva ndi kulankhula ya Chisombezi m’boma la Chiladzulu yapempha anthu m’dziko muno kuti azikonda kulimbikitsa ntchito zopeleka thandizo kwa anthu olumala ndikuti nawo azitha kukhala...
View ArticleBungwe la CRECCOM Liyamikira Mafumu Mboma a Mangochi
Bungwe la CRECCOM layamikira gawo lomwe mafumu akutenga m’boma la Mangochi polimbikitsa maphunziro a asungwana. Mkulu wa bungweli mayi Ziwone Mussa ndi yemwe wanena izi pamwambo opereka mphatso kwa...
View Article