Papa Francisco Akumana ndi Mtsogoleri wa Dziko la Palestine
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse papa Fransiscoanakomana ndi mtsogoleri wa dziko la Palestine ku Vatican pa ulendo wake wokakomana ndi nduna yaikulu ya mdziko la Italy. Malinga ndi...
View ArticleTaliban Yatulutsa Kanema Wa Amuna Awiri Amene Akuwasunga
Gulu la za uchifwamba la Taliban ati latulutsa kanema amene akuwonetsa amuna awiri omwe zigawengazi zinawaba ndipo zikuwasunga mokakamiza. Malipoti a wailesi ya BBC ati Kelvin King wa mdziko la America...
View ArticleBambo Hernandez Apezeka Atafa
Wansembe yemwe anasowa masiku apitawa mdziko la Mexico akuti wapezeka atafa mdera lina lotchedwa Parras mdzikolo. Malinga ndi malipoti a CNA wansembeyu Joaqui’n Hernandez yemwe amatumikira mu dayosizi...
View ArticleMwana Afa Mtengo wa Papaya Utamugwera
Mwana wina wa zaka zitatu wafa mtengo wa zipatso za mapapaya utamugwera m’mudzi mwa Kang’ombe m’dera la mfumu yayikulu Kasakula m’boma la Ntchisi. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo,SergeantGladson...
View ArticleZipani Zotsutsa Zidzudzula ma Bank, MRA
Zipani zotsutsa boma m’dziko muno zati zipitiliza ndi ganizo lokakamiza boma kuti lidziunika ndondomeko zomwe ma Bank komanso bungwe lotolera misonkho m’dziko muno la Malawi Revenue Authority...
View ArticleApempha Makhonsolo Athandize Anthu Okhudzidwa Ndi Ngozi Zogwa Mwadzidzidzi
Akuluakulu a makhonsolo onse m’dziko muno awalangiza kuti akonze ndondomeko zabwino zothandizira anthu okhudzidwa ndi ngozi zogwa mwadzidzidzi. Wachiwiri kwa m’tsogoleri wa dziko lino Dr. Saulos...
View ArticleMZIHA Ilimbikitsa Ntchito Zokopa Alendo
Bungwe lolimbikitsa za chikhalidwe cha Angoni la Mzimba Heritage Association (MZIHA),lati ligwilitsa bwino ntchito malo odziwika mu mbiri ya mtundu-wu pa ntchito zokopa alendo. Wapampando wa bungweli,...
View ArticlePapa Apepesa Okhudzidwa pa Ngozi ya Ndege Mdziko la Hong-Kong
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonsePapa Franciscowapereka uthenga wa chipepeso kwa anthu amene akhudzidwa pa ngozi ya ndege yomwe yagwa mu mzinda waKyrgyzstanmdziko laHong-Kong. Malipoti a...
View ArticleNtchito Yofufuza MH370 Yaimitsidwa
Ntchito yofufuza ndege ya MH370 ya mdziko la Malaysia yomwe inasowa zaka zitatu zapitazo ati ayamba ayiyimitsa. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC, mayiko a Australia, Malaysia komanso China aganiza...
View ArticleApempha Anthu Apitirize Kugwirana Manja ndi Apolisi
Anthu okhala mdera la mfumu yayikulu Bvumbwe m’boma la Thyolo awapempha kuti apitirize kugwirana manja ndi apolisi pa ntchito yolimbikitsa chitetezo cha ku madera. Mkulu wa apolisi ya m’delari a...
View ArticleSister Mpandira a Chipani Cha Teresian Amwalira
Akulikulu la chipani cha asisisteri chaTeresianmdziko muno alengeza za imfa ya Sister Everina Mpandiraochokera mu parishi yaKanyamamu dayosizi yaDedza. Malinga ndi akulikulu-wa, SisterEverinaanabadwa...
View ArticleCardinal Law Alowa M’manda
Mwambo woyika m’manda m’modzi mwa ma Cardinal a mpingo wakatolika amene anamwalira pa 20 mwezi uno wachitika lero ku likulu la mpingowu ku Vaticanmdziko laItaly. Malinga ndi malipoti a wailesi...
View ArticleDayosizi Ya Mangochi Ichita Chaka Cha Epifania
Mwambo wa chaka cha utumiki wa ana mu dayosizi ya Mangochiwachitikaku parishyaKochemu dayosizi-yi. Malingana ndi mkulu wowona za utumiki wa ana mu dayosizi-yi, mwambo-wu unayamba ndi mwambo wa nsembe...
View ArticleKhosolo Igwiritsa Ntchito Njira Zamakono Pofalitsa Uthenga Wa Edzi
Ofesi yoona za matenda a Edzi mu mzinda wa Mzuzu yati idzipereka pomwaza mauthenga othandiza pa ntchito zolimbana ndi kufala kwa kachilombo koyambitsa matenda a Edzi ka HIVpogwilitsa ntchito njira...
View ArticleJammeh Watuluka Mdziko la Gambia
Mtsogoleri wakale wa dziko la Gambia, Yahya Jammeh wachoka mdzikolo atavomereza kugonja kwake pa chisankho atalamulira dzikolo kwa zaka 22. Malipoti a wailesi ya BBC ati Jammeh pakadali pano ali mdziko...
View ArticlePapa Apempha Akhristu Alimbikitse Umodzi, Apemphelera Okhudzidwa Ndi Zivomerezi
Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse papa Francisco wapempha akhristu kuti agwirane manja popemphelera umodzi pakati pawo. Malinga ndi malipoti a wailesi ya Vatican ati papa wanena izi...
View ArticleRadio Maria Malawi Yakonzeka Kutumikira Omvera Ake Mchaka Cha 2017
Radio Maria Malawiati yakonza ndondomeko zosiyanasiyana pofuna kupititsa patsogolo ntchito za wailesiyi ndi cholinga choti itumikire bwino omvera ake mchaka cha 2017. Mkulu woyendetsa mapologalamuku...
View ArticleAnthu 18 Afa Kamba ka Nyengo Yoipa Mdziko la America
Anthu pafupifupi 18 afa ndipo ena ambiri avulala kutsatira nyengo yoipa kum’mwera kwa dziko la America. Malipoti a wailesi ya BBC ati gavanala wa ku Georgia walengeza kuti madera asanu ndi awiri 7...
View ArticleAkagwira Jere Zaka Zinayi Kaamba Koba Mbuzi
Bwalo lachiwiri la milandu m’boma la Mangochi, lalamula amuna awiri kuti akakhale kundende ndi kukagwira ntchito yakalavulagaga kwa zaka zinayikaamba kopezeka ndi mulandu wakuba mbuzi. Wapolisi...
View ArticlePapa Apempha Akhristu Alimbikitse Umodzi, Apemphelera Okhudzidwa Ndi Zivomerezi
Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse papa Francisco wapempha akhristu kuti agwirane manja popemphelera umodzi pakati pawo. Malinga ndi malipoti a wailesi ya Vatican ati papa wanena izi...
View Article