Radio Maria Malawi Yakonzeka Kutumikira Omvera Ake Mchaka Cha 2017
Radio Maria Malawiati yakonza ndondomeko zosiyanasiyana pofuna kupititsa patsogolo ntchito za wailesiyi ndi cholinga choti itumikire bwino omvera ake mchaka cha 2017. Mkulu woyendetsa mapologalamuku...
View ArticleAnthu 18 Afa Kamba ka Nyengo Yoipa Mdziko la America
Anthu pafupifupi 18 afa ndipo ena ambiri avulala kutsatira nyengo yoipa kum’mwera kwa dziko la America. Malipoti a wailesi ya BBC ati gavanala wa ku Georgia walengeza kuti madera asanu ndi awiri 7...
View Article11 Million Dollars Zasowa Mdziko la Gambia
Ndalama zoposa 11 million za America akuti zasowa mdziko la Gambia kutsatira kuchoka kwa mtsogoleri wa kale wa dzikolo a Yahya Jammeh. Malipoti a wailesi ya BBC ati pali chisonyezo chakuti a Jammeh aba...
View ArticleMoto Utentha Chipatala cha Boma la Ntcheu
Ntchito za pachipatala cha Ntcheu akuti zasokonekera kaamba ka ngozi ya moto umene wasakaza nyumba ndi zina pa chipatalachi. Wofalitsa nkhani za pa chipatala-chi mayi Stella Kawalala ati akukhulupilira...
View ArticleAfa Atagwera mu Mtsinje ndi Njinga
Mnyamata wina wa zaka khumi ndi zinayi (14) wafa atagwera mu mtsinje wina m’boma la Mangochi. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo, Inspector Rodrick Maida, wati m’mawa wa lero pa 4 January 2018,...
View ArticleObama Awonjezera Ndalama Za Chikho
Nduna ya zophunzitsa anthu, chikhalidwe ndi chitukuko cha ku midzi, mayiGrace Chiumiayawonjezera ndalama za mu ligi ya mpira wa miyendo yomwe imadziwika ndi kuti Obama Football League, yomwe...
View ArticleRed Cross Ipempha Mabungwe Agwilire Ntchito Limodzi
Bungwe laMalawi Red Cross Societylapempha mabungwe omwe siaboma kuti azilumikizana pomwe akugwira ntchito zosiyanasiyana zokhudza ngozi zogwa mwadzidzi. Mkulu wa bungweli m’boma la Zomba, aBlessings...
View ArticlePapa wati Mauthenga Azibweretsa Kusintha
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco walimbikitsa anthu kuti akhale ndi kuthekera kwabwino kopereka mauthenga ndi cholinga chofuna kuti dziko lonse liziyenda mu chowona komanso...
View ArticleMaepiskopi a Mdziko la America Sakugwirizana ndi Maganizo a Trump
Maepiskopi a Mdziko la America Sakugwirizana ndi Maganizo a Trump Bungwe la maepiskopi a mpingo wakatolika mdziko la America la United States Conference of Catholic Bishops latsutsa maganizo a...
View ArticleMphunzitsi Azipha Pozimangilira M’boma la Dedza
Bambo wina wa zaka 47zakubadwawadzipha podzimangilira m’boma la Dedza. Malingana ndi ofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo Edward Kabango, bambo-yu ndi Ives Kumankhamba ndipo anali mphunzitsi pa sukulu...
View ArticleDziko La Zimbabwe Likufufuza Momwe Grace Mugabe Anapezera PhD Yake
Bungwe lothana ndi katangale ndi ziphuphu mdziko laZimbabwelikuchita kafukufuku wofuna kupeza ngati mkazi wa mtsogoleri wakale wa dzikolo aGrace Mugabeanapeza certificate yake yaPhDmwachinyengo....
View ArticleKuphwera kwa Nyanja ya Chilwa Kwadzetsa Njala
Anthu okhala mdera lozungulira nyanja ya Chirwa m’boma la Zomba ati ali pa mavuto a njala ya dzawoneneni kutsatira kuphwera kwa nyanja ya Chilwa. Mfumu Njala ya kwa Sub T/A Nkagula m’bomalo yauza Radio...
View ArticleMkwamba Akhala Nambala 2 Polemba Nkhani Za Masewero
Wolemba nkhani zamasewero ku Radio Maria Malawi Foster Mkwamba wakhala m’modzi mwa atolankhani omwe achita bwino polemba nkhani za masewero mu mpikisano wa FIFA/FAM Under 20, mchaka cha 2017. Mkwamba...
View ArticleMipingo ya M’dera la Chimwala Ichita Mwambo wa Umodzi wa Akhristu
Mipingo ya chikhristu yopezeka m’dera la aSenior Chief Chimwalam’boma laMangochiayiyamikira kamba kodzipeleka pa ntchito zolimbikitsa umodzi pakati pawo. Mkulu woyendetsa ntchito za umodzi wa mipingo...
View ArticleNRB Ikupitiriza Kulemba Anthu Mkaundula wa Unzika
Bungwe lowona za kalembera mdziko muno la National Registration Bureau (NRB) lalengeza kuyambiranso kwa ntchito yolemba anthu mu kaundula wauzika mdziko muno. Wofalitsa nkhani ku bungweli a Norman...
View ArticleEthiopia Yaletsa Kupereka Ana Mmaiko Ena
Dziko la Ethiopia laletsa mchitidwe opereka ana kwa mzika za m’maiko ena, zomwe zimafika mdzikolo kufuna ana oti adzikawasamalira. Ganizoli, ladza, boma litalandira malipoti oti ana otengedwa ndi...
View ArticleKuchuluka Kwa Zipani Kulibe Vuto, Koma...
Mtsogoleri wa chipani chotsutsa boma cha Umodzi, Professor John Chisi wati sakuwonapo vuto pa kuchulukana kwa zipani za ndale mdziko muno. Professor Chisi wanena izi polankhula ndi Radio Maria Malawi....
View ArticleMipingo ya M’dera la Chimwala Ichita Mwambo wa Umodzi wa Akhristu
Mipingo ya chikhristu yopezeka m’dera la aSenior Chief Chimwalam’boma laMangochiayiyamikira kamba kodzipeleka pa ntchito zolimbikitsa umodzi pakati pawo. Mkulu woyendetsa ntchito za umodzi wa mipingo...
View ArticlePapa Ayamikira Ziwonetsero Zoteteza Moyo Mdziko La America
Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Francisco wayamikira onse omwe anatenga nawo mbali pa ulendo wa ndawala woteteza ufulu wa moyo womwe wachitika dzulo lachisanu mu mzinda wa...
View ArticleCADECOM Iwonetsetsa Kuti Anthu Akukhala ndi Chakudya Chokwanira
Bungwe la CADECOM mu dayosizi ya Zombalati liwonetsetsa kuti anthu mu dayosiziyo akukhala ndi chakudya chokwanira ngakhale nyengo ikusintha. Mkulu wa bungwe la CADECOM mu dayosizi yo bambo Patrick...
View Article