Bungwe la PMS Layamikira Makolo ndi Atsogoleri a Mpingo Pokometsa Utumiki wa Ana
Mkulu woyan’ganira mabungwe a utumiki wa a Papa m’dziko muno, wayamikira makolo ndi atsogoleri a mpingo chifukwa chothandiza kukometsa chaka cha utumiki wa ana chomwe chachitika lamulungu la...
View ArticleAkhristu Adzipereke Popititsa Patsogolo Moyo wa Miphakati
Akhristu a mparish ya St Martin Chirimba mu Archdayosizi ya Blantyre awapempha kuti adzipereke popititsa patsogolo moyo wa miphakati mparishiyi. A Robert Msakambewa omwe ndi wapampando wa Parishiyi...
View ArticleEpiskopi wa Dayosizi ya Mangochi Walimbikitsa Akhristu a ku Mvunguti kuti...
Episkopi wa dayosizi ya Mangochi Ambuye Montfort Sitima, alimbikitsa akhristu aku Mvunguti mparishi ya Nankhwali mudayosiziyi,kuti asafowoke pa chikhristu chawo ngakhale akukumana ndi mavuto...
View ArticleAkhristu Akuyenera Kukometsa Moyo Wawo wa Uzimu mu Chaka Chatsopanochi
Akhristu a mpingo wa katolika awapempha kuti pamene chaka chatsopano chayamba ayambiretu kutekeseka mu njira zosiyanasiyana pofuna kukometsa moyo wawo wauzimu. Wansembe owona za utumiki mu Archdayosizi...
View ArticleWapampando wa Bungwe la AMECEA Asankhidwa Kukhala Kadinala
Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Francis, wakweza paudindo wampando wa bungwe la maepiskopi a mdera kumvuma kwa Africa la AMECEA olemekezeka Ambuye Berhaneyesus Demerew Souraphiel...
View ArticleEpiskopi wa Dayosizi ya Mangochi Wathokoza Akhristu Podzipereka mu Chaka Chatha
Episkopi wa Dayosizi ya Mangochi Ambuye Montfort Stima wayamikira akhristu a mpingowu mu Dayosiziyi kamba kodzipeleka pothandiza mpingo mu njira zosiyanasiyana m’chaka changothachi. Ambuye Stima...
View ArticleAkhristu ndi Anthu Akufuna Kwabwino Apitirize Kuthandiza Radio Maria Malawi
Akhristu ndi anthu ena akufuna kwabwino m`dziko muno awapempha kuti athandize Radio Maria Malawi mu nyengo ino kuti ithe kupitiliza kutumikira anthu moyenera. Wapampando wa Parish ya Mzedi mu...
View ArticleDziko la Canada Lakhazikitsa Lamulo Lolemekeza Malemu Papa Yohane Paulo...
Nyumba ya malamulo mdziko la Canada yakhadzikitsa tsiku lachiwiri m’mwezi wa April chaka chilichonse kuti anthu mdzikolo, adzikumbulira mtsogoleri wakale wa mpingo wakatolika malemu Papa Yohane Paulo...
View ArticleZokonzekera Mwambo wa Chikondwelero cha Kachebere Seminale Zikuyenda Bwino
Zokonzekera mwambo otsekulira chikondwelero chakuti sukulu yosulira ansembe ya Kachebere m’boma la Mchinji yatha zaka 75 chiyambire ntchito zake akuti zikuyenda bwino. Wapampando wa komiti yomwe...
View ArticleMakhansala Apempha Boma kuti Liwapatse Ngongole
Bungwe la makhansala mdziko muno la Malawi Local Government Association (MALGA), lapempha boma kuti lipereke ngongole yogulira njinga za moto yomwe lidalonjeza kuti lipereka kwa makhansala pofuna kuti...
View ArticleAmbuye wabadwa
Ambuye wabadwa by St Tereza Chikalimbo choir Magomero Parish Zomba Diocese
View ArticlePapa Francisco wakhuzidwa ndi za chiwembu zomwe zachitika mdziko la France.
M’tsogoleri wa mpingo wa Katolika pa dziko lonse Papa Francisco wati ndi wokhudzidwa ndi imfa ya atolankhani a ku kampani ina yolemba nkhani omwe aphedwa lachitatu mu mzinda wa Paris m’dziko la...
View ArticleMchitidwe Wozembetsa Anthu Akuti Ukupitilirabe M`boma la Mangochi
Bungwe la Rights Advice Center m’boma la Mangochi lati lakonza mapulani omwe athandize kuthana ndi m’chitidwe wozembetsa anthu m’bomalo. Mkulu wa bungweli m’bomalo a Madalitso Masache ndi yemwe wanena...
View ArticleMadzi Apha Munthu M`modzi Ndikuvulaza ena Atatu M`boma la Zomba.
Munthu m’modzi wafa ndipo ena atatu akuti avulala ndi madzi osefukira mu m’tsinje wa Likangala m’boma la Zomba. Malinga ndi Wofalitsa nkhani za apolisi m`boma la Zomba Constable Patricio Supliano...
View Article