Bambo Kamela ndi Wansembe Watsopano Woona za Utumiki Ku ECM
Bungwe la ma episkopi a mpingo wakatolika mdziko muno la Episcopal Conference of Malawi ECMlalengeza kuti lasankha bambo Regis Kamela kukhala wansembe woona za utumiki ku bungweli. Malinga ndi kalata...
View ArticleAnsembe Sakuloledwa Kutsogolera Miyambo ya Maliro ya Anthu Odzipha
Mpingo wakatolika m’dziko la CANADA wati ansembe ampingowu sakuloledwa kutsogolera miyambo ya maliro aanthu amene amwalira mwakufuna kwawo. Ma-episikopi a mpingo-wu anena izi kudzera mu uthenga wawo....
View ArticleStation ya Sitima ya Nkaya Itha mu November
Gawo lachiwiri lomanga station ya sitima za pamtunda ya NKAYA m’boma la BALAKA akuti ikuyembekezeka kutha mwezi wa NOVEMBER chaka chino. Wofalitsa nkhani ku bungwe loona za sitima za pamtunda la...
View ArticleMariatona wa Lokolo Atsekulidwa pa 15 October
Mwambo wotsekulira Mariatona wa lokolo akuti udzachitika loweruka pa 15 mwezi uno ku likulu kwa Radio Maria Malawi ku Mangochi. M’modzi mwa akulu akulu oyendetsa ntchito za Radio Maria Malawi a...
View ArticleAnthu 5600 Apulumutsidwa pa Ngozi ya pa Nyanja
Magulu opulumutsa anthu pa ngozi za pa madzi a m’dziko la Italy apulumutsa anthu othawa kwao oposera 5600 pa ngozi ya pa nyanja ya Mediterranean. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC anthuwa anakwera...
View ArticlePapa Ayendera Dera lomwe Linakhudzidwa ndi Chivomerezi Mdziko la Italy
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco anakayendera madera omwe anakhudzidwa ndi ngozi ya chivomerezi mdera la Amatrice mchigawo cha pakati cha dziko la Italy. Malinga ndi...
View ArticlePapa Watsiriza Ulendo Wake wa Nambala 16 Atayendera Mayiko a Georgia ndi...
Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Francisco wamaliza ulendo wake wa nambala 16 oyendera maiko akunja kwa dziko la Italyatayendera maiko a Georgia komansoAzerbaijan. Malinga ndi...
View ArticleGulu la Al-Shabab Lichitira Chiwembu Akhristu
Gulu la za uchifwamba la chisilamu la al-shabab lavomera kuti ndi lomwe lachita chiwembu chomwe chaphetsa akhristu pafupifupi asanu ndi m’modzi 6 ndi kuvulaza m’modzi modetsa nkhawa kumpoto...
View ArticlePapa Alimbikitsa Ubale wa Pakati pa Mpingo Wakatolika ndi Anglican
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha akhristu a mpingo wa katolika ndi Anglican kuti azigwilira ntchito limodzi ndi cholinga chofuna kulimbikitsa umodzi pakati pawo....
View ArticleAna 47 mwa 100 Aliwonse ndi Onyetchera M’boma la Ntchisi
Komiti yolimbikitsa kadyedwe kabwino m’boma la Ntchisi yati ikuyesetsa kugwira ntchito ndi magulu osiyanasiyana pofuna kuchepetsa chiwerengero cha ana omwe ali ndi vuto la ku nyetchera m’bomalo. Mkulu...
View ArticleMagazi ndi Aulere Mzipatala Zonse za Boma-MoH
Boma latsutsa malipoti akuti limagulitsa magazi kwa odwala mzipatala zosiyanasiyana za boma m’dziko muno. M’modzi mwa akuluakulu mu unduna wa za umoyo a Joseph Bitilinyu Bangoli anena izi pa maphunziro...
View ArticlePapa Wasankha Macardinal 17 Atsopano
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse papa franciso wasankha amsembe khumi, asanu ndi awiri 17 kukhala ma cardinal mu mpingo-wu. Mwa makadinalawa 13 ali ndi zaka za makadino amene amapatsidwa...
View ArticleEpiskopi Apempha Akhristu Atsatire Moyo Wa Francis Wa Ku Assisi Woyera
Akhristu a mpingo wa katolika m’dziko muno awapempha kuti akhale olimba pa chikhristu chawo komanso achifundo kwa ovutika monga ankachitira Francis wa ku Assisi woyera. Poyankhula pa mwambo womwe...
View ArticleAnthu Alandira Ziphaso Zoyamba za Umzika Mwezi Uno
Bungwe lowona za kalembera m’dziko muno la Malawi National Registration Bureau (MNRB)lati latsiriza gawo loyamba lolembera ziphaso mzika za dziko lino. Mneneri wa bungweli a Norman Fulatira ati anthu...
View ArticleAtsikana Ena Omwe Anagwidwa ndi Boko Haram Akumana ndi Abale Awo
Ena mwa atsikana okwana makumi awiri ndi m’modzi 21 omwe anagwidwa ndi zigawenga za chisilamu za Boko Haram mu tawuni ya Chibok mdziko la Nigeria ati akumana ndi abale awo. Malinga ndi malipoti a...
View ArticlePapa Wati Anthu Agwirane Manja Pothetsa Umphawi
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha anthu akufuna kwabwino kuti agwirane manja pofuna kuthetsa umphawi pokhazikitsa malamulo othandiza mabanja komanso kupereka mwai...
View ArticleAnthu Awiri Afa pa Ngozi M’boma la Mangochi
Amuna awiri afa atakhudzidwa ndi ngozi zapansewu ziwiri zosiyana zomwe zachitika dzulo m’boma la Mangochi. Wachiwiri kwa w Amuna awiri afa atakhudzidwa ndi ngozi zapansewu ziwiri zosiyana zomwe...
View ArticleChigawenga cha IS Chaphedwa
Munthu wina yemwe akumuganizira kuti ndi wa gulu la zigawenga za Islamic State IS akuti amupha pomuombera mdziko la Turkey. Malinga ndi malipotia wailesi ya BBC, mkuluyu wagwidwa mu mzinda wa Ankara,...
View ArticlePapa Wapempha Anthu Athandize Osowa Chakudya, Malo Abwino
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse PapaFransisco wapempha anthu akufuna kwabwino kuti azithandiza anthu amene akusowa chakudya komanso malo okhala abwino. Papa wanena izi pa bwalo la St....
View ArticleAnthu Akhale Odzidalira-DMI
Anthu mdziko muno awapempha kuti azikhala olimbikira ndi odzidalira pofuna kupititsa patsogolo chitukuko cha m’madera omwe akukhala. M’modzi mwa akuluakulu oyendetsa ntchito zaDMIWomen’s Worldm’boma la...
View Article