I am a Catholic and I am Proud Mangochi Diocese Cheers Prisoners
Proud catholics in the Diocese of Mangochi cheered prisoners at Mangochi prison today 17th September 2016. It was wonderful charity activity. By the grace of God they managed to share to each of them a...
View ArticleMakwaya Akufalitsa Uthenga wa Mulungu
Ma kwaya a mpingo wa katolika mdziko muno awapempha kuti pamene akuyimba nyimbo zawo azidzindikira kuti nawonso akufalitsa uthenga wa Mulungu. AmbuyeMontfort Sitima a dayosizi ya mpingo wakatolika ya...
View ArticlePapa Alangiza Nthumwi Zake Zisatengeke ndi Ndale
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisko wapempha nthumwi zake za m’maiko osiyanasiyana padziko lonse kuti zitumikire anthu modzichepetsa komanso kuti zisamataye nthawi yawo pa...
View ArticleAtolankhani ali ndi Udindo Wodziwa za Kadyedwe Kabwino
Boma lati atolankhani m’dziko muno ali ndi udindo wodziwa za kadyedwe kabwino kaamba koti ndi anthu omwe amafalitsa mauthenga mosavuta. Mlangizi wamkulu wowona za kadyedwe kabwino, HIV ndi edzi mu...
View ArticleApolisi Akufunafuna Anthu Amene Afukula Manda M’boma la Machinga
Apolisi m’boma la Machinga ati akufunafuna anthu ena omwe sakudziwika omwe afukula manda m’mudzi mwa Chinguwo kwa Sub TA Mchiguza m’bomali. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomali Constable DavieSulumba...
View ArticleMabungwe Omwe si Aboma ali ndi Gawo Lothandiza pa Chitukuko
Mabungwe omwe si a boma awapempha kuti azikumanakumana ndi cholinga choti azitha kukambirana zinthu zina zomwe zingathandize kupititsa patsogolo ntchito za chitukuko cha dziko lino. Wapampando wa...
View ArticleNtchito Yomanga Chidzanja Parish Ikuyenda Bwino
Ntchito yomanga tchalitchi latsopano la St. Francis of Assis Chidzanja Parish mu dayosizi ya Mangochi ati ikuyenda bwino. Bambo mfumu a parishiyi bambo Kizito Khauya anena izi polankhula ndi Radio...
View ArticleMANEB Yakweza Malipiro a Mayeso
Bungwe lowona za mayeso m’dziko muno la Malawi National Examinations Board (MANEB) lakweza ndalama zomwe ophunzira a standade 8 komanso a form 4 akuyenera kulipilira ku bungweli kuti alembe mayeso....
View ArticleUtolankhani Chisakhale Chida Chowonongera Zinthu-Papa
Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse papa Francisco wapempha atolankhani kuti asagwiritse ntchito yawo kukhala chida chowonongera zinthu. Papa Francisco wanena izi ku Vaticanpa mkumano omwe...
View ArticleBICO Yapereka 500 Sauzande Kuchipatala cha Mangochi
Bungwe la za umoyo lomwe si la boma la Blantyre Institute for Community Ophthalmology (BICO) lapeleka thandizo la ndalama zokwanira 5 Hundred Thousand Kwacha ku chipatala cha boma la Mangochi....
View ArticleApempha Chakwera Athetse Kusamvana mu MCP
Anthu otsatira chipani chotsutsa boma cha Malawi Congress(MCP)okhala m’dera la kum’poto cha kumadzulo m’boma la Salima apempha mtsogoleri wa chipanichi Dr. Lazarus Chakwera kuti athetse kusamvana...
View ArticleAbwenzi a Radio Maria Malawi Nguludi Parish Alonjeza Kupitiriza Kuthandiza...
Abwenzi a Radio Maria Malawi ochokera ku parishi ya Nguludi mu arkidayosizi ya Blantyre alonjeza kuti apitiriza kuthandiza wailesiyi mu zosowa zake ndi cholinga choti ipitirize kufalitsa uthenga wa...
View ArticleAlimi Aleke Kudalira Mbewu ya Fodya
Pamene malonda afodya akupitilira kuvuta pa msika wa Auction, alimi mdziko muno awapempha kuti asiye kudalira mbewu ya fodya ndipo m’malo mwake apeze mbewu zina m’malo mwa mbewuyi. M’modzi mwa...
View ArticleAnthu Okwiya Aphwanya Kampani ya Tea ya Mphezu
Anthu okwiya awononga katundu pa kampani yolima tea ya Mphezu kwa Bvumbwe m’boma la Thyolo potsatira imfa ya munthu wina yemwe wafa atamenyedwa ndi alonda a pa malowa. Malinga ndi mtolankhani wathu...
View ArticleWansembe Wapezeka Atafa Mdziko la Mexico
Wansembe wina wa mpingo wa katolika m’dziko la Mexicoyemwe anasowa atatengedwa ndi zigawenga wapezeka atafa pa malo ena mdzikolo. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC, thupi la wansembeyi Jose Alfred...
View ArticleBoma Lichite Kafukufuku Okhudzana ndi Kupsa kwa Misika
Bungwe lomenyera ufulu wa anthu mdziko muno la Human Rights Defender lapempha boma kuti lichite kafukufuku okwanira okhuzana ndi kupsa kwa misika m’dziko muno. Mkulu wa bungweli a Billy Mayaya ndi omwe...
View ArticleAnthu a ku Salima Northwest Atsutsa Zoti Sakugwirizana ndi Phungu Wawo
Anthu otsatira chipani chotsutsa boma mdziko muno cha Malawi congress (MCP) ku mpoto cha kumadzulo kwa boma la Salima atsutsa zomwe zakhala zikumveka kuti anthu a mderali sakumufuna phungu wawo wa ku...
View ArticleRights Advice Center Ikudzipereka Pothetsa Human Trafficking
Bungwe la Rights Advice Center m’boma la Mangochi aliyamikira kamba kodzipeleka pa ntchito yodziwitsa anthu zambiri zokhudza m’chitidwe wogulitsa ndi kuzembetsa anthu (Human Trafficking)m'bomalo. Mkulu...
View ArticleAnthu ali ndi Udindo Woyezetsa Magazi
Anthu ati ali ndi udindo wokayezetsa magazi ndi cholinga choti adziwe momwe mthupi mwao mulili. M’modzi mwa dotolo wa pa chipatala cha Mwaiwathu Dr.Simon Chiumia anena izi mu mzinda wa Blantyre pa...
View ArticleAnthu Agwilitse Ntchito Bwino Zinthu Zomwe ali Nazo-ECM
Bungwe la ma episikopia mpingo wakatolika m’dziko muno la Episcopal Conference of Malawi (ECM) lati anthu m’dziko muno angachite bwino pa chitukuko cha miyoyo yawo ngati angachilimike pogwilitsa bwino...
View Article