Ana Atatu Afa Ndipo Anthu Ena 16 Ali Mchipatala Atadya Chakudya cha P
Ana atatu a banja limodzi amwalira m’boma la Ntchisi ndipo anthu ena 16, awagoneka pa chipatala cha boma m’bomalo atadya chakudya chomwe akuchiganizira kuti chinali ndi poyizoni. M’neneri wa apolisi...
View ArticleMabungwe a mu Mpingo Wakatolika Apeza Njira Zodzetsa Umodzi
Msonkhano wa mabungwe ang’onoang’ono a mumpingo wakatolika omwe wakonzedwa ndi mabungwe a ma episkopi mmayiko a Madagascar ndi Africa uli m’kati mdziko la Ghana. Zina mwa mfundo zomwe nthumwi ku...
View ArticleDziko la Malawi Lichita Mwambo Wokumbukira Kulimbana ndi Nkhanza pa Dziko Lonse
Masiku 16 oganizira komanso kulimbana ndi nkhanza za m’banja padziko lonse ayamba lachiwiri pa 25 November. M’masikuwa mayiko amakhala akukumbukira komanso kulingalira nkhanza zosiyanasiyana zomwe...
View ArticleKhansa ya Khomo la Chiberekero, Chiwopsezo Cha Miyoyo ya Amayi
Nthenda ya khansa ya mchiberekero akuti ndi imodzi mwa matenda omwe akupitilira kutenga miyoyo ya amayi kamba koti amayi ambiri samapita kukayezetsa kuti adziwe ngati ali ndi matendawa kapena ayi....
View ArticleNthumwi ku Msonkhano wa PAC Zilephera Kumvana Maganizo pa Ulamuliro wa...
Nthumwi kumsonkhano womva maganizo a akuluakulu pankhani yokhudza ulamuliro wamzigawo womwe umachitikira mumzinda wa Blantyre masiku awiri apitawa,zalephera kumvana chimodzi pankhaniyi. Msonkhanowu...
View ArticleUnduna Wowona Za Ntchito, Udzudzula za Mchitidwe Wonyanyala Ntchito
Unduna wowona za ntchito m’dziko muno wapempha anthu ogwira ntchito m’boma kuti adzitsatira malamulo akafuna kunyanyala ntchito pamavuto omwe akukumana nawo. Nduna mu undunawu wolemekezeka a Henry...
View ArticleVuto la Madzi Lakula Mdera la Mchesi
Anthu okhala ku Mchesi m’boma la Lilongwe apempha boma kuti liyambe msanga kupereka madzi awukhondo pogwiritsa ntchito mipopi yomwe idamangidwa kale mderalo. Malinga ndi m’modzi mwa anthu okhudzidwa...
View ArticleMabungwe Osakhala a Boma Awuza Akuluakulu a NAC kuti Atule Pansi Maudindo
Mabungwe osiyanasiyana omwe si aboma apempha akuluakulu a bungwe lowona za matenda a Edzi mdziko muno la National Aids Commission NAC,kuti atule pansi maudindo awo kaamba kolephera ntchito. Mabungwewa...
View ArticleNthambi za Chitetezo Zidzudzula za Imfa ya Msilikali
Nthambi za chitetezo mdziko muno za Polisi ndi Army zadzudzula imfa ya msilikali wa Army yemwe anaphedwa ndi apolisi loweruka pa 22 November nthawi ya 11 koloko usiku mumzinda wa Zomba. Akuluakulu...
View ArticleAnthu 15 Afa ndipo 10 Avulala Atawomberedwa
Anthu khumi ndi asanu aphedwa ndinso ena khumi avulala atawomberedwa ndi anthu ena omwe anakwera ngamila mdziko la Sudan. Mmodzi mwa anthu omwe avulala pachiwembucho wawuza atolankhani kuchipatala...
View ArticleZipembedzo Zidzudzula Mchitidwe wa Uchifwamba Mdzina la Chipembedzo
Nthambi zowona ubale wa mipingo ndi zipembedzo kulikulu la mpingo wakatolika komanso kuchisilamu, zadzudzula magulu osiyanasiyana omwe akuchitira anthu zamtopola mudzina la chipembedzo. Magulu awiriwa...
View ArticleNkhanza za Mbanja Zikukolezera Kufala kwa Matenda a Edzi
Bungwe la Southern Africa Aids Trust SAAT lati nkhanza za m’banja ndi vuto limodzi lomwe likukolezera kufala kwa kachilombo ka HIV komwe kamayambitsa matenda a Edzi. Mkulu wabungweli a Robert Mangwazu...
View ArticleSinatusi ya Legio ya Maria Ayikhazikitsa ku Maula Cathedral
Episkopi wa Arch dayosizi ya Lilongwe ya mpingo wakatolika Ambuye Tarsizius Ziyaye walimbikitsa ma membala a bungwe la Legio kuti apitilize kudzipereka pogwira ntchito zawo mu mpingo. Ambuye Ziyaye...
View ArticleA ku Banja Adzudzula Madonna Polephera Kusunga Lonjezo
Katswiri woyimba nyimbo za chamba cha POP wa mdziko la America Madonna, amudzudzula kamba kolephera kusunga lonjezo lomwe anapereka kwa makolo a mwana yemwe anamutenga mdziko muno kuti akamulere mdziko...
View ArticleSukulu ya Ukachenjede ya DMI Itengapo Mbali Pokweza Maphunziro a Ana
Ena mwa mabungwe omwe siaboma m’boma la Mangochi ayamikira sukulu ya ukachenjede ya St.John The Batist, DMI,kamba koyikanso chidwi pantchito zosula ana msukulu za pulayimale m’bomalo. Mkulu wabungwe la...
View Article2014 World AIDS Day Message From The Catholic Health Commission of The...
THEME: GETTING TO ZERO 1.0 Preamble Today in the liturgical calendar of the Catholic Church is the first Sunday of Advent. The Church begins a new Liturgical Year, a new journey of faith. The...
View ArticleRadio Maria Malawi Ithokoza Akhristu
Wachiwiri kwa mkulu woyang’anira ma pulogalamu ku Radio Maria Malawi Bambo Charles Kaponya wayamikira akhristu kamba ka chidwi chawo potenga gawo lothandiza wailesiyi. Bambo Kaponya amalankhula izi...
View ArticleAphunzitsi a Bungwe la Wild Life Society of Malawi Apindula ndi Ulendo Wawo
Gulu la aphunzitsi a bungwe la Wild Life Society of Malawi lochokera ku Mvera m’boma la Dowa lati kuyenda ndi mbali imodzi ya maphunziro. Mkulu wagululi a Morgan Chafulumira Mwale ndi amene alankhula...
View ArticleMRA Ichepetsa Mavuto a Msonkho kwa Eni Minibus
Mavuto okhudza misonkho omwe anthu ochita bizinezi ya ma minibus amakumana nawo ati akuyembekezeka kuchepa kamba koti bungwe lotolera misonkho mdziko muno la Malawi Revenue Authority (MRA) lati...
View Article