Dziko la Gambia Ndi Lokonzeka Kuthetsa Mgwirizano Ndi Bungwe la EU
Dziko la Gambia lati ndilokonzeka kuthetsa mgwilizano wake ndi bungwe la European Union (EU) ngati bungweli lipitilize kukakamiza dzikolo, kuvomeleza kuti anthu azichita maukwati apakati pa amuna...
View ArticleAnthu Achitepo Kanthu Polimbana ndi Matenda a Edzi
Tsiku lokumbukira matenda a Edzi padziko lonse ati likuyenera kukhala tsiku limene anthu akuyenera kukumbukira kuti matenda a Edzi alipodi, pochitapo kanthu polimbana ndi matendawa. Wachiwiri kwa...
View ArticleMabungwe a Achinyamata Mdziko Muno Adzudzula Bungwe la NAC
Mabungwe omenyelera ufulu wa achinyamata mdziko muno apereka masiku khumi ndi anayi 14, kuti mabungwe omwe analandira ndalama kuthumba la bungwe lowona za matenda a Edzi la National Aids Commission...
View ArticleMpingo wa Katolika Susintha Chiphunzitso Chake pa Banja
Episkopi wa Arkidayosizi ya Sydney mdziko la Australia Ambuye Anthony Fisher, atsimikizira a khristu a mpingo wakatolika mdzikolo kuti anthu asayembekezere kuti mpingowu, usintha chiphunzitso chake...
View ArticleAnthu Olumala Akusowa Zipangizo Zamakono Zogwiritsa Ntchito
Bungwe lowona za ufulu wa anthu olumala la Federation of Disability Organisation in Malawi FEDOMA ladandaula chifukwa cha kusowa kwa zipangizo za makono zomwe anthu olumala angamagwiritse ntchito....
View ArticleMabungwe Apempha Nthambi ya Ukazitape, Beam, Mulhako kuti Abweze Ndalama za NAC
Mabungwe Manet+, Manerela+,Cedep,Mehen komanso CHRR,alangiza mabungwe omwe adalandira ndalama kubungwe la NAC mosavomerezeka kuti abweze ndalamazi pasanathe sabata imodzi. Mabungwewa anena izi...
View ArticleBungwe la CAMA Layimitsa Ziwonetsero za BWB
Bungwe lomenyera ufulu wa anthu ogula la Consumers Association of Malawi CAMA, layamba layimitsa ziwonetsero zomwe linakonza kuti zichitike lachinayi pokwiya ndi vuto la madzi lomwe lafika poyipa...
View ArticleDziko la Philippines Likhazikitsa Masiku a Tchuthi Pamene Papa Francisco...
Pamene mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco akuyembekezeka kukacheza mdziko la Philippines mwezi wa mawa, meya wa mzinda wa Manila mdzikolo walamula kuti anthu mu mzindawo...
View ArticlePapa Francisco Wati Mchitidwe Wozembetsa Anthu ndi Ukapolo Wamakono
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati mchitidwe wozembetsa anthu ndi ukapolo wamakono womwe anthu akukumana nawo. Papa Francisco wanena izi lachiwiri kulikulu la mpingo wa...
View ArticleUnduna Wofalitsa Nkhani Wapereka Zotsatira za Kafukufuku wa Kubedwa kwa...
Unduna wofalitsa nkhani lachinayi wapereka zotsatira za kafukufuku yemwe amachitika kunyumba ya boma pankhani ya kubedwa kwa ndalama za boma. Kafukufukuyu wasonyeza kuti mtsogoleri wakale wa dziko lino...
View ArticleNkhanza za kwa Ana Zikusokoneza Maphunziro
Ana ambiri akuti akulephera kuchita bwino pa maphunziro awo kamba ka nkhaza zomwe amakumana nazo pa moyo wawo wa tsiku ndi tsiku. Mkulu woona za chitetezo cha ana ku bungwe la Plan International Malawi...
View ArticleMugabe Wachenjeza kuti Achotsa Ntchito omwe Akumukonzera Chiwembu
Mtsogoleri wa dziko la Zimbabwe Robert Gabriel Mugabe wachenjeza kuti achotsa ntchito komanso kulanga aliyense yemwe angadziwike kuti akukonza zomuchitira chiwembu. Pulezidenti Mugabe wanena izi...
View ArticleMabungwe a Ufulu wa Achinyamata Awopseza kuti Achita Ziwonetsero
Mabungwe anayi owona za ufulu wa achinyamata omwe akugwilira ntchito zawo mchigawo chakumpoto, awopseza kuti achita ziwonetsero ngati mabungwe omwe adatenga ndalama kubungwe la NAC mosavomerezeka,...
View ArticleAtsikana omwe Anasiyira Sukulu Panjira Ali ndi Mwayi Wopitiriza Maphunziro
Atsikana amene anasiyira sukulu panjira kamba ka zifukwa zosiyanasiyana akuti ali ndi mwayi wotha kukapitiliza maphunziro awo ndi thandizo lochokera ku bungwe lomwe angolikhadzikitsa kumene la...
View ArticleBungwe la Chilungamo ndi Mtendere CCJP Silikukhutira ndi Kayendetsedwe ka...
Bungwe la Chilungamo ndi Mtendere CCJP mu mpingo wakatolika lati silokhutira ndi momwe boma likuyendetsera ntchito zake pofuna kutukula miyoyo ya anthu mdziko muno. Bungweli lanena izi kudzera...
View ArticleAkhristu a Parish ya St.Charles Lwanga ku Zomba Athandiza Radio Maria Malawi
Akhristu a mu Parish ya St.Charles Lwanga mu dayosizi ya Zomba awayamikira chifukwa chothandiza Radio Maria Malawi. Bambo Patrick Mwaliwa amalankhula izi pa mwambo wa misa ya promotion womwe...
View ArticleA Polisi Asanu ndi Anayi Amwalira Pangozi Ya Panseu
Mtsogoleri wadziko lino Professor Arthur Peter Mutharika wati ndi wokhumudwa kwambiri ndi imfa ya apolisi asanu ndi anayi omwe amwalira loweruka pangozi ya galimoto m’boma la Balaka. Malinga ndi...
View Article