Mphunzitsi Amangidwa Kamba Kogwilirira Mwana wa Sukulu
Apolisi m’boma la Ntchisi amanga mphunzitsi wa pa sukulu ina ya pulayimale kamba kogwirira ophunzira wina pa sukulupo wa zaka 16 zakubadwa. Mneneri wa apolisi m’bomalo Sergent Gladson M’bumpha...
View ArticleDayosizi Ya Mangochi Ilimbikitsa Ana Kupewa Malungo
Dayosizi ya mpingo wa katolika ya Mangochi kudzera mu nthambi yoona za umoyo ya Catholic Health Commission mu dayosiziyo yati ipitiriza kuphunzitsa ana njira zimene angapewere matenda a malungo. Vicar...
View ArticleApempha Amayi Azitanganidwa Kukweza Dziko, Miyoyo Yawo
Amayi ochokera m’mipingo yosiyanasiyana m’dziko muno awapempha kuti azikonda kutanganidwa ndi zinthu zomwe zingathandize pa chitukuko cha miyoyo yawo ndi dziko lino. Mayi Trizer Masauli omwe...
View ArticleAmayi a Katolika Awapempha Azamitse Moyo wa Mapemphero
Amayi a chikatolika mu arkidayosizi ya Blantyre awapempha kuti azamitse moyo wawo wa mapemphero ngati njira imodzi yosinkhasinkha moyenera masautso a ambuye yesu khristu. Mlembi wa za utumiki mu...
View ArticleMa Episkopi Mdziko la South Africa Adzudzula Ziwawa Mdzikolo
Maepiskopi a mpingo wakatolika mdziko la South Africa adzudzula mchitidwe wa ziwawa omwe ukuchitika mdzikolo potsatira chisankho cha makhansala chomwe chikuyembekezeka kuchitika mwezi wa mawa. Malinga...
View ArticleAtsogoleri a mdziko la Nigeria Ateteze Maufulu a Anthu
Ma episkopi a mpingo wa katolika m’dziko la Nigeria apempha atsogoleri a dzikolo kuti ayesetse kuteteza ufulu wa anthu m’dzikomo. Malingana ndi malipoti a Catholic News Agencyma episkopiwa alankhula...
View ArticlePapa Akumana ndi Pulezidenti wa Dziko la Lebanon
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco ati anachita zokambirana ndi mtsogoleri wa dziko la Lebanon Michel Aoun yemwe anakayendera likulu la mpingo wakatolikali. Malinga ndi...
View ArticleAnthu Asamalire Chilengedwe Pofuna Kupewa Njala
Anthu mdziko muno ati akuyenera kutenga mbali yaikulu yoteteza chilengedwe pofuna kupewa vuto la kusowa kwa chakudya lomwe padakali pano lakhudza kwambiri dziko la Malawi. Vicar General wa dayosizi ya...
View ArticleWoyimira Anthu pa Milandu Wapezeka Atafa Mdziko la Kenya
Loya wina yemwe amayimilira munthu wina pamlandu woti apolisi m`dziko la Kenyaakumachitira nkhanza anthu m`dzikolo wapezeka atafa munzinda wa Nairobi m`dzikolo. Loyayu, Willie Kimani wa zaka 32,...
View ArticleMa Episkopi Mdziko la South Africa Adzudzula Ziwawa Mdzikolo
Maepiskopi a mpingo wakatolika mdziko la South Africa adzudzula mchitidwe wa ziwawa omwe ukuchitika mdzikolo potsatira chisankho cha makhansala chomwe chikuyembekezeka kuchitika mwezi wa mawa. Malinga...
View ArticleChitukuko Chingapite Patsogolo Ngati Adindo ndi Mzika Akulumikizana
Kulumikizana pa nkhani za chitukuko cha m’madera pakati pa adindo komanso mzika ati ndi njira yokhayo yomwe ingapititse patsogolo chitukuko cha dziko lino. Wachiwiri kwa mfumu ya mzinda wa Blantyre, a...
View ArticlePresident wa Dziko la Phillipines Wakana Maukwati a Amuna, Akazi Okhaokha
Mtsogoleri wa dziko la Phillipines Rodrigo Duterte wakanitsitsa kuvomeleza maukwati a amuna kapena akazi okhaokha. Malipoti a wailesi ya BBC mtsogoleriyu wakanitsitsa kuti sangavomereze mchitidwewu...
View ArticlePapa Apempha Ansembe Ayike Patsogolo Sakramenti la Kulapa
Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Francisko wapempha ansembe kuti ayike sakramenti la kulapa patsogolo kuti alimbikitse umoyo wa uzimu mma parishi mwawo. Papa Francisko amalankhula...
View ArticleAmbuye Msusa Apempha Amayi Azipereke Potukula Uzimu
Arkiepiskopi wa arkidayosizi ya mpingo wa katolika ya Blantyre Ambuye Thomas Luke Msusa walimbikitsa amayi mu arkidayisizi-yi kuti azipeleke potukula uzimu pakati pa anthu. Ambuye Msusa apeleka...
View ArticleMaepiskopi Mdziko la USA ati Miyoyo ya Anthu Osauka ili pa Chiopsezo
Maepiskopi a mpingo wa katolika mdziko la United States of America ati miyoyo ya anthu ovutika mdzikolo ili pa chiopsezo potsatira ndondomeko yatsopano ya zaumoyo yomwe yakhazikitsidwa mdzikolo....
View ArticlePapa Wapepesa Anthu Amene Akhuzidwa Ndi Chiwembu Mdziko la Bangladesh
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Fransisko wapereka uthenga wa chipepeso kwa anthu omwe akhudzidwa ndi chiwembu chomwe chaphetsa anthu makumi awiri mu mzinda wa Dhaka mdziko la...
View ArticleMutharika Wati Atukula Mzinda wa Zomba
President wa dziko lino Professor Arthur Peter Mutharika wati boma lake likhazikitsa zitukuko zosiyanasiyana mu mzinda wa Zomba ndi cholinga choti mzindawu udzifanafana ndi mizinda ina ya mdziko...
View ArticleApempha Wailesi Zifalitse Nthenga Wothetsa Kufala Kwa Kolera
Nyumba zowulutsa mawu za m’madera a kumidzi (Community Radio) azipempha kuti zizipereke pa ntchito yofalitsa mauthenga a njira zopewera matenda a kolera omwe amafala kwambiri mu nyengo ya mvula....
View ArticleKaliati Apempha Mabanja Athandize Radio Maria Malawi
Nduna ya zophunzitsa anthu mai Patricia Kaliati wapepha mabanja kuti athandizire Radio Maria Malawi kufalitsa nthenga wa chipulumutso mu njira zosiyanasiyana. Mai Kaliati amalankhula izi ku parish ya...
View ArticleDayosizi ya Mangochi Ikufuna Akhristu Apindule ndi Nyumba Zake Zowulutsira Mawu
Dayosizi ya mpingo wa katolika ya Mangochi yati ikufuna igwiritse bwino ntchito nyumba zowulutsira mawu zomwe ili nazo pofalitsa nthenga wa Mulungu. Episkopi wa dayosiziyi Ambuye Montfort Stima ndi...
View Article