Papa Francisco Apereka Ubatizo kwa Ana
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco lamulungu lomwe ndi tsiku la chaka cha Ubatizo wa Ambuye Yesu Khristu, wapereka Sacrament la Ubatizo kwa ana makumi atatu ndi atatu {33}....
View ArticleAnsembe ndi Asemino Akhale Okonda Kupemphera
Ansembe komanso Asemino m`dziko muno awalimbikitsa kuti azipemphera mosalekeza kuti akhristu athe kupulumutsidwa. Mkulu woyang`anira ma seminale mu mpingo wa Katolika Ambuye Martin Mtumbuka ndi womwe...
View ArticleMakwaya a Amayi Awalimbikitsa kuti Apitilize Kudzipereka mu Mpingo
Mamembala a makwaya a amayi mu mpingo wakatolika mu dinale ya Thyolo awalimbikitsa kuti apitirize kudzipereka pogwira ntchito zotumikira Mulungu kudzera mu mphatso ya mayimbidwe. Mlembi wa mu komiti ya...
View ArticleAna Aziwonetserana Chikondi Pamene Akumana
Episkopi wa ArchdayosiziyaLilongwe wolemekezeka AmbuyeTarcizio Ziyaye walimbikitsa ana mu mpingowu kuti azikhala okondana nthawi zonse pomwe akumana malo amodzi. Ambuye Ziyaye anena izi ku parish ya...
View ArticleBoma la Chikwawa Lakhudzidwa Kwambiri ndi Ngozi za Madzi
Nthambi yowona za ngozi zogwa mwadzidzidzi yati boma la Chikwawa ndi lomwe lakhudzidwa kwambiri ndi ngozi ya madzi poyerekeza ndi maboma ena pamene mvula yamphamvu ikugwa mmadera ambiri mdziko muno....
View ArticleApolisi Agwira Mzika Zina za Mdziko la DRC
Apolisi ku Chiponde m’boma la Mangochi, agwira mzika 34 za mdziko la Democratic Republic of Congo zomwe zimafuna kulowa mdziko la Mozambique kudzera mdziko muno mosavomerezeka. Wofalitsa nkhani za...
View ArticleLikulu la Mpingo Wakatolika Lilamula Wansembe kuti Apitilize Utumiki Wake
Likulu la mpingo wa Katolika ku Vatican lalamula likulu la mpingowu ku Iraq, kuti ulole wansembe yemwe anachoka ku parish yake mdzikolo powopa ulamuliro wachisilamu kuti apitilize utumiki wake....
View ArticleGulu la Al Qaeda Liwopseza Dziko la France ndi Ziwembu
Gulu la za uchifwamba la Al Qaeda mchigawo chakumpoto kwa Africa, lawopseza dziko la France ndi ziwembu, pambuyo pa za mtopola zomwe anthu ena, achita mdzikolo sabata yapitayi. Malinga ndi chikalata...
View ArticlePapa Francisco Apempha kuti Ufulu wa Anthu Uzilemekezedwa
Mtsogoleri wa mpingo wa Katolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha magulu osiyanasiyana kuti azilemekeza ufulu wa anthu komanso kuwonetsa umodzi pa zochitika zawo. Papa Francisco wanena izi...
View ArticleMabungwe omwe si Aboma Achita Ziwonetsero
Ziwonetsero zofuna kukakamiza mabungwe omwe analandira thandizo la ndalama kuchokera ku bungwe lowona za matenda a Edzi mdziko muno la National Aids Commission NAC kuti abweze ndalamazi zachitika...
View ArticleAnthu 153 Afa ndi Mvula Yamphamvu Mboma la Nsanje
Lipoti lomwe khonsola ya boma la Nsanje latulutsa, lati pafupifupi anthu 153 afa kuyambira pomwe mvula ya mphamvu yayamba mmadera ambiri mdziko muno. Bwanamkubwa wa bomalo a Harry Phiri,anena izi...
View ArticlePapa Francisco Ayendera Dziko la Phillipines
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco, wafika mdziko la Phillipines paulendo wake wa masiku asanu ndi limodzi oyendera mayiko aku Asia. Pakadali pano akhristu a mpingowu ndi ena...
View ArticleEpiskopi wa Dayosizi ya Mzuzu Wamwalira
Bungwe la ma Episkopi a mpingo wa katolika mdziko muno la Episcopal Conference of Malawi (ECM) likudziwitsa za imfa ya Olemekezeka Ambuye Joseph Mukasa Zuza amene anali Episkopi wa dayosizi ya Mzuzu...
View ArticlePapa Francisco Alangiza Akhristu kuti Akhale Ofalitsa Uthenga
Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Francisco,walangiza a khristu a mpingowu mdziko la Philippines kuti adzikhala a kazembe a Yesu Khristu pofalitsa uthenga wa Mulungu ndi chikondi...
View ArticleBungwe la YCW mu Dayosizi ya Zomba Iathandiza Anthu Okhudzidwa ndi Madzi...
Bungwe la Young Christian Workers ku St Charles Lwangwa mu dayosizi ya Zomba, lapereka katundu wa ndalama zokwana 100 thousand kwacha kwa mabanja ena omwe akhudzidwa ndi madzi osefukira m’boma la...
View ArticleMwambo Woyika Mmanda Ambuye Zuza Uchitika Lolemba
Mwambo oyika m`manda thupi la yemwe anali Episkopi wa dayosizi ya Mzuzu Ambuye Joseph Mukasa Zuza,uchitika lolemba pa 19 January,2015 nthawi ya 10 koloko m`mawa ku St Peters Cathedral mu dayosiziyo....
View ArticlePapa Francisco Asonkhanitsa Anthu Oposa 6 Miliyoni mu Mzinda wa Manila
Malipoti ochokera mdziko la Phillipines ati anthu oposa 6 miliyoni ndi omwe adali nawo pa mwambo wa nsembe ya ukalistia yomwe mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Francisco anatsogolera...
View ArticlePapa Francisco Akacheza Mdziko la America M’mwezi wa September
Mtsogoleri wa mpingo wa Katolika pa dziko lonse Papa Francisco watsimikiza za ulendo wake wokacheza mdziko la America m’mwezi wa September chaka chino. Polankhula kwa atolankhani omwe anali nawo...
View ArticleMzika za Mdziko la Ethiopia Azigamula kuti ndi Zolakwa
Bwalo loyamba la Magistrate m’boma la Dowa lalamula mzika 71 zaku Ethiopia kuti zipereke chindapusa cha ndalama zokwana 5 sauzande kwacha aliyense komanso kukakhala ku ndende kwa miyezi itatu,...
View ArticleAchiwembu Mdziko la Niger Apha Anthu ndi Kutentha Matchalitchi ndi Nyumba za...
Malipoti ochokera mdziko la Niger ati anthu khumi aphedwa, ndipo maparishi ochuluka komanso nyumba za ansembe ndi asisiteri, zatenthedwa mdziko la Niger pa chiwembu chomwe anthu omwe sakudziwika achita...
View Article