Papa Francisco Akacheza Mdziko la America M’mwezi wa September
Mtsogoleri wa mpingo wa Katolika pa dziko lonse Papa Francisco watsimikiza za ulendo wake wokacheza mdziko la America m’mwezi wa September chaka chino. Polankhula kwa atolankhani omwe anali nawo...
View ArticlePapa Wapereka Uthenga wa Chipepeso Mmayiko a Afghanistan ndi Pakistan
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapereka uthenga wachipepeso kwa anthu omwe akhudzidwa ndi ngozi ya chivomerezi mmayiko a Afghanistan ndi Pakistan. Mu uthenga womwe Papa...
View ArticleUmbuli pa Matenda a Cancer Ukuphetsa Anthu
Kusadziwa komanso ulesi opita kuchipatala kukayezetsa nthenda ya Cancer ndi zina mwanjira zomwe zikupititsa patsogolo chiwerengero cha anthu odwala matendawa m'dziko muno. M'modzi mwa madotolo...
View ArticleChiwerengero cha Achinyamata Omwa ma ARV Chakwera M’boma la Mangochi
Chiwerengero cha achinyamata omwe amalandira mankhwala otalikitsa moyo a ARV ati chikukwera m’boma la Mangochi. Mkulu oyang’anira anthu omwe amamwa mankhwalawa pa chipatala chachikulu cha Mangochi a...
View ArticleBungwe la AU Lakhazikitsa Kafukufuku wa Maufulu Ophwanyidwa Mdziko la Burundi
Bungwe la United Nations lati likugwirizana ndi mfundo yomwe bungwe la African Union lakhazikitsa, lochita kafukufuku wa maufulu a anthu omwe akhala akuphwanyidwa mdziko la Burundi. Bungweli ati ndi...
View ArticleAchiwembu Mdziko la Niger Apha Anthu ndi Kutentha Matchalitchi ndi Nyumba za...
Malipoti ochokera mdziko la Niger ati anthu khumi aphedwa, ndipo maparishi ochuluka komanso nyumba za ansembe ndi asisiteri, zatenthedwa mdziko la Niger pa chiwembu chomwe anthu omwe sakudziwika achita...
View ArticleBank ya Standard Imanga Midada Yophunziliramo M’boma la Chiradzulu
Boma ati likuyenera kumanga makalasi okwana 38 sauzande kuti likwaniritse kupereka maphunziro apamwamba m`dziko muno. Mlembi wamkulu wa mu unduna wa zamaphunziro sayansi ndi luso Mayi Lonely Magareta...
View ArticlePapa Francisco Alimbikitsa Ansembe Kuthandiza Akhristu pa Mavuto
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse PapaFrancisco walimbikitsa ansembe mu mpingowu kuti azikhala okhudzidwa ndi kuthandiza pa mavuto omwe akhristu akukumana nawo. Papa wati ansembe...
View ArticleDziko la Germany Litseka Zipata Zake ndi Dziko la Australia
Dziko la Germany lati litseka zina mwa zipata zake ndi dziko la Australia pofuna kuchepetsa anthu othawa kwawo omwe akulowa m`dzikolo kudzera mdziko la Australia lo. Akuluakulu a dziko la Germany ati...
View ArticleMnyamata wa Zaka 27 Amupeza Wolakwa pa Mlandu Wogwilira
Bwalo loyamba la milandu m’boma la Ntchisi lagamula sing’anga wina wa zaka 27 zakubadwa kuti akakhale ku ndende kwa zaka khumi ndi kukagwira ntchito ya kalavula gaga kamba kopezeka olakwa pa mulandu...
View ArticleAmbuye Ziyaye Alimbikitsa Pakati pa Akhristu
Ark Episkopi wa Arch Dayosizi ya Lilongwe Ambuye Tarsizius Ziyaye apempha akhristu a m’parishi ya St Kizito mu Ark dayosiziyo kuti alimbikitse m’gwirizano wabwino pakati pawo. Ambuye Ziyaye anena izi...
View ArticleBambo wina M’boma la Ntchisi Wafa ndi Chiphaliwali
Bambo wina wa zaka 40 zakubadwa wamwalira atawombedwa ndi mphenzi m’boma la Ntchisi. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomalo Sergent Gladson M’bumpha watsimikiza za nkhaniyi. Iye wati chiphaliwalichi...
View ArticlePapa Wapepesa Dziko la Romania Kamba ka Ngozi ya Moto
Mtsogoleri wa Mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapepesa Pulezident wa dziko la Romania potsatira ngozi ya moto yomwe yapha anthu makumi atatu ndi awiri, ndikuvulaza ena 130 mu m’dzinda...
View ArticleAnthu 11 Avulala pa Ngozi ya Galimoto
Anthu khumi ndi m’modzi avulala pa ngozi ya galimoto m’boma la Ntchisi. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomali Sergent Gladson Mb’umpha wati pa anthu omwe avulalawo, anayi avulala kodetsa nkhawa ndipo...
View ArticleAlimi Apewe Kugula Mbeu Wamba
Kampani yogulitsa mbeu mdziko muno ya Mosanto Malawi yachenjeza alimi kuti apewe kugula mbeu kwa mavendor. Mkulu wa zamalonda ku kampaniyi a Denis Kachikho ndi omwe anena izi potsatira kumangidwa...
View ArticleDziko la Nigeria Lalephera Kuteteza Mzika Zake
Bungwe lowona za ufulu wa anthu padziko lonse la Amnesty International,lati dziko la Nigeria lalephera kuteteza mzika zake zomwe zikukhala mdera la Baga,pamene gulu la zigawenga la Boko Haram lawopseza...
View ArticleMabungwe Achitepo Kanthu kwa Anthu Okhudzidwa ndi Kusefukira kwa Madzi
Bungwe lowona ma ufulu a anthu mchipembedzo cha Chisilamu la Muslim Forum for Democracy lalangiza mabungwe omenyera ufulu wa anthu mdziko muno,kuti athandize anthu omwe akhudzidwa ndi mvula ya mphamvu...
View ArticleDziko la Malawi Lipundula pa Ntchito Yofalitsa Uthenga Wabwino
Dziko la Malawi ati likuyembekezeka kupindula pa ntchito yofalitsa uthenga wabwino komanso yotukula dziko lino potsatira msonkhano waukulu wanyumba zofalitsa nkhani za Radio Maria womwe wachitikira...
View ArticleBwalo Lalikulu la Milandu Mdziko la Kenya Lakana Kuwonjezera Malipiro...
Bwalo lalikulu lamilandu mdziko la Kenya lakana kuwonjezera malipiro a aphunzitsi a mdzikolo ndi ma peresenti 60 monga momwe bwalo la milandu lowona za kagwiridwe komanso kalembedwe ka ntchito...
View ArticleJOINT MEDIA AND ADVOCACY STATEMENT
1.0. PREAMBLE The Catholic Commission for Justice and Peace (CCJP) which is a social justice and advocacy arm; and the Research and Social Commission which is the communication arm of the Episcopal...
View Article