Ambuye Sitima ati Makwaya Azipeka Nyimbo za Tanthauzo
Episkopi wa Dayosizi ya Mangochi ya mpingo wakatolika Ambuye Montfort Sitima wapempha makwaya mdziko muno kuti aziwonetsetsa nthawi zonse kuti pamene akupeka nyimbo zizikhala za tanthauzo. Ambuye...
View ArticleDziko la Sierra Leone Likondwelera Kutha kwa Matenda a Ebola
Anthu m’dziko la Sierra Leone akupitiliza kuchita chisangalalo chokondwelera kutha kwa matenda a Ebola m’dzikomo. Bungwe la za umoyo pa dziko lonse la World Health Organization ndi lomwe lalengeza...
View ArticleNsika wa Kasungu Ukufunika Ndalama Zokwana 10 miliyoni Kwacha
Nsika wa Kasungu omwe unapsa mwezi wa October ati ukufunika ndalama zoposa 10 Million Kwacha kuti ukozedwenso. Wachiwiri kwa Meya wa Manicipality ya Kasungu a Ephate Joshua ndi yemwe wanena izi pomwe...
View ArticlePulezidenti Kagame Adzudzula Dziko la Burundi
Mtsogoleri wa dziko la Rwanda Paul Kagame wadzudzula ziwawa zomwe zikuchitika m`dziko la Burundi zomwe zikuphetsa anthu ankhanikhani. Pulezidenti Kagame wati anthu m`dzikolo akungophedwa...
View ArticleAtolankhani Azilemba Nkhani za Matenda Osapatsirana
Atolankhani mdziko muno awapempha kuti azilemba nkhani zokwanira zokhudza matenda osapatsirana omwe ndi kuphatizapo a shuga pofuna kuchepetsa imfa zomwe zimachitika kudzera mmatendawa Mkulu wa bungwe...
View ArticleUlendo wa Papa Wokacheza Mdziko la CAR Upereka Chiyembekezo kwa akhristu a...
Akhristu a mpingo wa katolika a m’dziko la Central African Republic omwe akhala akuphana tsiku ndi tsiku kamba ka nkhondo ati akuyembekezera kuti ulendo wa mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko...
View ArticleBungwe la Community of St Egidio Layamba Kuphunzitsa Anthu Kufunika Kolembesa...
Bungwe la mpingo wa Akatolika la Community of St Egidio m’dziko muno layamba ntchito yophunzitsa anthu kufunika kwa kalembera wa ana omwe angobadwa kumene.Polankhula pa mwambo otsegulira maphunziro a...
View ArticleApolisi Ati Anthu Azigwiritsa Ntchito Malamulo MoyeneraApolisi Ati Anthu...
Apolisi apempha anthu m’dziko muno kuti azitengera kupolisi anthu onse omwe akuwaganizira kuti apalamula milandu osati kuwalanga okha. Wachiwiri kwa mneneri wa apolisi ku Limbe mu mzinda wa Blantyre...
View Articlenthu ena Anakawombera Mdera la Kumpoto kwa Mzinda wa Paris
Pomwe apolisi mu mzinda wa Paris mdziko la France akupilizabe kuchita kafukufuku wa anthu omwe anachita chiwembu chomwe chinapha anthu pafupifupi 1 hundred 30 mdzikolo, anthu ena omwe sakudziwika ati...
View ArticleMatenda a Ebola Akuyembekezeka Kutha Mdziko la GuineaMatenda a Ebola...
Munthu wotsiriza yemwe amadwala matenda a Ebola m`dziko la Guinea wachira ndipo amutulutsa mchipatala. Malinga ndi wofalitsa nkhani ku nthambi yomwe imayang`anira ntchito zothana ndi matendawa...
View ArticleDziko la Canada Lichepetsa Chiwerengero Chosunga Anthu Othawa Kwawo
Dziko la Canada lati lisunga anthu othawa kwao okwana 10 sauzande ochokera mdziko la Syria chikamatha chaka chino. Malipoti a wailesi ya BBC ati dzikoli poyamba linalonjeza kuti lisunga anthu othawa...
View ArticleAnthu Odwala Matenda a Edzi Asasalidwe
Bungwe la National AIDS Commission NAC lati anthu omwe anapezeka ndi kachilombo koyambitsa matenda a Edzi sayenera kusalidwa . Mmodzi mwa akuluakulu ku bungweli a Ahmidu Tung'ande ndi omwe anena...
View ArticleBungwe la MBTS Lipempha Anthu kuti Agwirane Nalo ManjaBungwe la MBTS Lipempha...
Bungwe lotolera magazi la Malawi Blood Transfussion Service MBTS lamemeza anthu kuti agwirane nalo manja powonetsetsa kuti zipatala za m'dziko muno zili ndi magazi okwanira komanso a ukhondo. Mkulu...
View ArticleBungwe la Community of Saint Egidio Likondwelera Zaka 47 Chilikhazikitsire
Bungwe la Community of Saint Egidio lati ndi lokondwa kuti tsopano lakwanitsa zaka 47 kuchokera pomwe bungweli linayamba kugwira ntchito zake zolimbikitsa moyo wa mapemphero ndi kudzipeleka pogwira...
View ArticleBambo Corna a Mdziko la Italy Amwalira
A ku Likulu la chipani cha Mofolo Woyera ku Rome mdziko la Italy alengeza za imfa ya Bambo Attilio Corna omwe anamwalira lachiwiri pa 10 February 2015 mu mzinda wa Bergamo mdzikolo. Bambo Corna...
View ArticleSister Martha Clemence Manuel Makhasa a Chipani cha SBVM Amwalira
Sister Martha Clemence Manuel Makhasa a Chipani cha Servants of Blessed Virgin Mary (SBVM), amwalira lachisanu. Malinga ndi akulikulu la chipanichi Sister Martha anabadwa pa 8 September 1932 ndipo...
View ArticleKUTHETSA MLILI WA HIV: KUWUNIKA UDINDO WA MPINGO PA NDONDOMEKO YA 90-90-90
- Osatopa ndikuchita zinthu zabwino- (2 Thess. 3:13) Uthenga wa HIV ndi EDZI m’chaka cha 2015 From ECM Health Commission 1.0 CHIYAMBI Lero ndi lamulungu loyamba munyengo ya Adventi....
View ArticlePapa Francisco Alimbikitsa Achinyamata Kuzamitsa Moyo wa Uzimu
Muuthenga wachaka cha achinyamata chaka chino, mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco, wapempha akhristu mumpingowu kuti azamitse moyo wawo wauzimu poyeretsa mitima yawo....
View ArticleZigawenga za Boko Haram Zilepheretsa Zisankho Mdziko la Nigeria
Mtsogoleri wa gulu la zigawenga za Boko Haram Abubakar Shekau, wanenetsa kuti alepheretsa zisankho za atsogoleri zomwe dzikolo likuyembekezeka kukhala nazo pa 28 March chaka chino. Iye wanena izi...
View ArticleMpingo wa Katolika ku Vatican Uganizira Anthu Osowa
Mpingo wa katolika ku Vatican wakhazikitsa malo ometera awulele a anthu osowa kwawo. Pa mwambowu womwe unatsekuliridwa ndi mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco kunafika anthu...
View Article