Anthu 6.5 Million Ayamba Kulandira Chakudya
Anthu pafupifupi 6.5 million omwe akhudzidwa ndi vuto njala mdziko muno ati apindula ndi thandizo la chakudya lomwe boma kudzera ku bungwe lowona za chakudya pa dziko lonse la World Food Programme...
View ArticleUnited Nations Yadudzula Boko Haram
Bungwe la mgwirizano wa maiko pa dziko lonse la United Nations (UN) ladzudzula gulu la zauchifwamba la Boko Haram kaamba ka zamtopola zomwe likuchitira anthu a m’dziko la Nigeria. M’modzi mwa...
View ArticlePapa Fransisko Wapempha Dziko la Poland Lizilandira Anthu Othawa Kwawo
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha atsogoleri a zipani mdziko la Poland kuti azilandira anthu othawa kwao ochokera m’maiko osiyanasiyana. Papa amalankhula izi...
View ArticleCatholic Charasmatic Renewal Movement Ikondwelera Zaka 25
Mwambo wa msembe ya misa wokondwelera kuti bungwe la Catholic Charasmatic Renewal Movement (CCRM) lampingo wakatolika lakwanitsa zaka 25 chilikhazikitsileni m’dziko muno wachitika ku Maula Cathedral mu...
View ArticleAnthu Oposa 2,000 Akuthawira Ku Uganda Tsiku Ndi Tsiku
Anthu oposera 2 sauzande ochokera mdziko la South Sudan ati akumalowa kumpoto kwa dziko la Uganda tsiku ndi tsiku pothawa nkhondo yapachiweniweni yomwe ikuchitika mdzikolo. Malinga ndi malipoti a...
View ArticleAnthu 14 Akuyembekeza Kunyongedwa Mdziko La Indonesia
Dziko la Indonesia lapereka chilango chakupha kwa anthu khumi ndi anayi (14) omwe anapezeka olakwa pa mlandu wopezeka ndi makhwala ozunguza bongo. Anthuwa omwe atatu ndi mzika za mdziko la Nigeria...
View ArticleAnthu Azikanena Ku Khonsolo Akachitiridwa Nkhanza
Khosolo ya mzinda wa Blantyre yapempha anthu malonda mu mzindawu kuti azikanena ku khosoloyi pa nkhanza zina zili zonse zomwe angachitiridwe ndi anthu ogwira ntchito kukhosoloyi. Wofalitsa nkhani ku...
View ArticleChiphwanya ndi Mlembi Watsopano wa CCJP
Aku likulu la mpingo wakatolika mdziko muno alengeza za kusankhidwa kwa a Martin Chiphwanya kukhala mlembi wa bungwe la chilungamo ndi mtendere m’dziko muno. A kulikulu la mpingo-wu ndi omwe alengeza...
View ArticleChaka cha Achinyamata pa Dziko Lonse 2019 Chidzachitikira Mdziko la Panama
Mpingo wakatolika m’dziko la Panama wati ndi wokondwa ndi uthenga umene walandira woti chaka cha achinyamata mu mpingowu pa dziko lonse chidzachitikire mdzikomo. M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa...
View ArticleAchinyamata Omwe Anakayimilira Mpingo Wakatolika M’dziko Muno Ku Chaka Cha...
Polankhula moyimira achinyamata-wa bambo Frank Mwinganyama omwe ndi mlangizi wa achinyamata mu Arch-Dayosizi ya Blantyre omwenso anali nawo pa ulendowu ati ndi okhutira ndi momwe chakachi chayendera....
View ArticleKabwira Akufunitsitsa Apolisi Afufuze Mokwanira za Kuwotchedwa kwa Galimoto Lake
Phungu wa kunyumba yamalamulo m’chingawo chakumpoto cha kumvuma kwa boma la Salima, olemekekezeka Dr. Jessie Kabwira wati akufunitsitsa kuti apolisi afufuze mokwanira nkhani ya kuotchedwa kwa...
View ArticleKuyenderana Kungathandize Kukweza Ntchito za Bungwe la YCW
Kuyenderana pakati pa achinyamata a m`bungwe la Young Christian Workers (YCW) ati kungathandize kuti ntchito za bungweri zipite patsogolo. Wapampando wa bungwe la YCW ku St. Charles Luangwa m`dayosizi...
View ArticlePhalombe Catholic Parish in the Archdiocese of Blantyre has called upon well...
The Parish Priest father Clifford Chiwanda made the call during a Fundraising paper Sunday that was held on Sunday 7th August 2016. The fundraising activity was aimed at sourcing funds to finish the...
View ArticleMzika ya Dziko la DRC Yafa Itamwa Mowa Osadyera M’boma la Dowa
Mzika ina ya dziko la Democratic Republic of Congo (DRC), yafa itamwa mowa osadyera kumalo osungirako anthu othawa kwawo a Dzaleka m`boma la Dowa. Wofalitsa nkhani za apolisi m`boma la DowaSergent...
View ArticleApezeka ndi Minyanga ya Njovu
Apolisi munzinda wa Lilongwe amanga mwamuna wina wazaka 27 atampeza ndi minyanga ya njovu. Malinga ndi wofalitsa nkhani za apolisi munzindawu, Inspector Kingsley Dandaula, mkuluyi Ackim Bwanali...
View ArticleFashion and Glams Lapereka Katundu Wokwana 1.2 Million ku Bungwe la APAM
Gulu la Fashion and Glams lapereka katundu wokwana 1.2Million kwacha kuti bungwe lomenyera ufulu wa anthu a mtundu wachialubino la Association with People with Albinism (APAM) . M`modzi mwa membala wa...
View ArticleApezeka ndi Nyanga za Njovu
Apolisi munzinda wa Lilongwe amanga mwamuna wina wazaka 27 atampeza ndi nyanga za njovu. Malinga ndi wofalitsa nkhani za apolisi munzindawu, Inspector Kingsley Dandaula, mkuluyi Ackim Bwanali...
View ArticleChiwerengero cha Milandu Chakwera ndi 9.2% ku Chigawo cha Kum’mawa kwa Dziko...
Apolisi ku m’chigawo cha kum’mawa kwa dziko lino ati chaka chino chiwerengero cha milandu chakwera kwambiri m’miyezi isanu ndi umodzi (6) yapitayi poyerekeza ndi momwe zinaliri m’miyeziyi chaka chatha....
View ArticlePapa ndi Okhudzidwa ndi Kusowa kwa Mtendere Mdziko la Syria
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Fransiskowati ndi wokhudzidwa ndi mavuto akusowa kwa mtendere omwe anthu a m’dziko la Syria akupitilira kukumana nawo. Papa wati magulu omwe...
View ArticleNyumba Zotsindika ndi Kuwulutsa Nkhani ati Zikuyenera Kuphunzitsa...
Nyumba zotsindika ndi kuwulutsa nkhani za mpingo wakatolika mdziko muno azipempha kuti nthawi zonse pamene zikugwira ntchito yake zizitsatira chiphunzitso chomwe mpingo wakatolika umaphunzitsa....
View Article