Chidutswa cha Ndege ya MH 370 Chapezeka Mdziko la Mozambique
Anthu omwe akhala akuchita kafukufuku wa ndege yomwe inasowa m’chaka cha 2014 ati apeza chidutswa cha ndegeyo m’dziko la Mozambique. Ndegeyo yomwe nambala yake inali MH370 yomwe imachokera ku Kuala...
View ArticlePapa Achita Zokambirana ndi Pulezidenti wa Dziko la Costa Rica
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisko anakumana ndi Pulezidenti wa dziko la Costa Rica a Luis Guillermo Solis komwe anakambirana za ubale wa pakati pa dzikoli ndi likulu la...
View ArticlePapa Wati Akhristu Apemphelere Tsiku la pa 1 June
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisko wapempha akhristu kuti apemphelere tsiku la pa 1 June lomwe ndi tsiku lokumbukira ana pa dziko lonse, mwapadera pokumbukira ana a mdziko la...
View ArticleDayosizi ya Zomba Ilimbikitsa Maphunziro kwa Ana Ozungulira Nyanja ya Chilwa
Dayosizi ya mpingo wakatolika ya Zomba yapempha makolo ozungulira Nyanja ya Chilwa kuti alimbikitse ana awo pa maphunziro pofuna kukonza tsogolo lawo. Episkopi wa dayosiziyi Ambuye George Desmond...
View ArticlePapa Wapempha Madikoni Asatengere Nthawi Potumikira
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wapempha anthu omwe anasankha kutumikira Mulungu ngati madikoni, kuti azikhala okonzera kutumikira nthawi ina iliyonse posatengera nthawi...
View ArticleHabre Alamulidwa kuti Akakhale ku Ndende Moyo Wake Onse
Bwalo la milandu mdziko la Senegal lalamula mtsogoleri wakale wa dzikolo a Hissene Habre kuti akakhale ku ndende moyo wao onse kamba kopezeka olakwa pa milandu yophwanya maufulu a anthu. Malipoti a...
View ArticleAnthu awiri afa pa Ngozi ya Galimoto M’boma la Mwanza
Anthu awiri afa ndipo ena asanu ndi mmodzi avulala atagundidwa ndi galimoto ya mtundu wa traki m’boma la Mwanza. Wofalitsa nkhani za apolisi m’bomali Sub Inspector Edwin Kaunda watsimikiza za nkhaniyi....
View ArticleDziko la Kenya lati Litseka Malo Aakulu Osungirako Anthu Othawa
Dziko la Kenya lati litseka malo aakulu osungirako anthu othawa kwao omwe ali mdzikolo mmwezi wa November chaka chino. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC malowa omwe akusunga anthu oposera 3 hundred...
View ArticleMayeso A JCE Ayamba
Ophunzira a Form 2 msukulu za sekondale m’dziko muno ayamba lachiwiri kulemba mayeso awo a Junior Certificate of Education (JCE). Malingana ndi ofalitsa nkhani za bungwe lowona za mayeso m’dziko muno...
View ArticleCharity of Ottawa Ipempha Atsikana kuti Atumikire Mulungu Kudzera Mu Usisitere
Atsikana mu mpingo wakatolika awapempha kuti adzipereke ku moyo wotumikira Mulungu kudzera mu njira ya usisteri kuti nawo akhale zida zenizeni zothandizira pa ntchito yofalitsa uthenga wabwino...
View ArticlePapa Wati Mulungu Amachitira Chifundo anthu a Chilungamo ndi Odzichepetsa
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisco wati pemphero lowona limachokera mu mtima mwa munthu amene amazindikira kulakwitsa kwake ndi kulapa. Papa amalankhula izi pa bwalo la St...
View ArticleAnthu 250 Apulumuka pa Ngozi ya pa Nyanja ya Meditereanean
Anthu othawa kwao pafupifupi mazana awiri ndi makumi asanu (250) ati apulumitsidwa bwato lomwe anakwera litagubuduzika pa nyanja yaikulu ya Mediterranean m’dziko la Greece. Malinga ndi malipoti a...
View ArticleAkhristu Akhale Olimba Mtima pa Chikhristu Ngati Amalitiri a ku Uganda
Akhristu a mpingo wakatolika awapempha kuti atengere chitsanzo cha kulimba mtima pa chikhristu chawo monga momwe anachitira Amalitiri 22 a ku Uganda polora kuphedwa kamba chikhulupiliro chawo. Episkopi...
View ArticleSukulu ya Mary View Ikusowa Thandizo
Sukulu ya ana omwe ali ndi vuto losamva ku Mary View m’boma la Chiradzuluyapempha anthu m’dziko muno kuti azidzipeleka pa ntchito yothandiza ana ndi sukuluyi. Sister Monica Cham’munda omwe ndi m’modzi...
View ArticleKaliati Wayamikira Mpingo Wakatolika Podzipereka Kufalitsa Uthenga Wabwino
Mpingo wakatolika m’dziko muno awuyamikira kamba kodzipereka pa ntchito zofalitsa uthenga wabwino. Nduna ya zofalitsa nkhani ndi kuphunzitsa anthu zinthu zosiyanasiyana mayiPatricia Kaliati ndi omwe...
View ArticleChilima Wapempha Akatolika kuti Adzipereke Pothandiza mpingo Mozidalira
Akhristu a mpingo wakatolika m’dziko muno awapempha kuti apitirize kudzipereka pa ntchito yothandiza mpingo modzidalira. Wachiwiri kwa m’tsogoleri wa dziko lino Dr. Saulos Klaus Chilima ndi amene izi...
View ArticleMamuna Wina Wamira M’boma la Ntchisi
Mamuna wina m’boma la Ntchisi ati wafa atamira mu mtsinje wa Bua komwe anapita kukawedza nsomba. Wofalitsa nkhani za apolisi mbomali Sergent Gladson M’bumpha watsimikiza za nkhaniyi. Sergent M’bumpha...
View ArticlePapa Francisko Wakhazikitsa Stanislaus ndi Maria Elizabeti Kukhala Oyera
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Francisko wakhazikitsa Stanislaus wa Yosefe ndi Maria komanso Maria Elizabeti Hesselblad kukhala oyera. Papa wakhazikitsa awiriwa kukhala oyera...
View ArticleAnthu Asanu Ochita Masewero Opalasa Njinga Afa Atagundidwa Ndi Galimoto
Anthu asanu ochita masewero opalasa njinga afa ndipo ena anayi avulala galimoto lina litawaomba ku Michigan m’dziko la America. Anthu-wa ati agundidwa ndi galimoto la mtundu wa Pick Up lomwe pa...
View ArticlePapa Wati Akhristu Apempherere Mtendere wa Mmaiko Onse
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Franciskowapempha anthu ndi akhristu a mpingowu kuti lachitatu akumbukire kupemphelera mtendere wa m’mayiko pa dziko lonse. Malinga ndi malipoti a...
View Article