Akhristu 49 akuno ku Malawi ankhala nawo pa Mwambo wa Misa Wokumbukila...
Akhristu 49 a mpingo wakatolika akuno ku Malawi, lachitatu anakhala nawo pamwambo wamapemphero okumbukira a maritiri 22 ku Namugongo Shrine mdziko la Uganda. Mmodzi mwa amaritiriwa Charles Lwanga Oyera...
View ArticleChiwelengelo cha Akhristu Achikatolika Chikukula
Lipoti lomwe nthambi yowona zakafukufuku pa sukulu ina ya ukachenjede mdziko la America yatulutsa lati chiwerengero cha akhristu a mpingo wakatolika padziko lonse chikukwera kwambiri maka mmaiko a mu...
View ArticleCadecom Inkhazikitsa Tchito Yonthandiza Anthu Mboma la Chikhwawa.
Dayosizi ya mpingo wakatolika ya Chikhwawa yati iwonetsetsa kuti ntchito za Bungwe lowona zachitukuko mumpingowu la CADECOM zikupindulira anthu onse mu Dayosiziyo. Episikopi wa Dayosiziyi wolemekezeka...
View ArticleApolisi M’dziko la New Guinea Akuwaganizira Kuti Apha Ophunzira Anayi Omwe...
Apolisi m’dziko la New Guinea akuwaganizira kuti apha ophunzira anayi a pa sukulu ina ya ukachenjede omwe amachita chionetsero chosonyeza kusakondwa ndi zochita za nduna yaikulu ya dzikolo. Malingana...
View ArticleAnthu Makumi Atatu Afa Zigawenga za Islamic State Zitaphulitsa Bomba La Timke...
Anthu makumi atatu afa, ndipo ena 80 avulala gulu la zigawenga la Islamic State litaphulitsa mabomba awiri atinkenawo munzinda wa Baghdad m`dziko la Iraq Malinga ndi malipoti awailesi ya BBC, bomba...
View ArticleECM Yasankha Bambo Likutcha Kukhala Mlangizi wa Apolisi
Bungwe la ma episkopi mdziko muno la Episcopal Conference Of Malawi [ECM] lasakha Bambo Steven Likhucha kukhala mlangizi wa apolisi mumpingowu m’dziko muno. Bungweli lanena izi kudzera muchikalata...
View ArticleKanyongolo Wapempha Boma Libwezeretse Maubale Ndi Maiko Ena
Katswiri wa malamulo yemwenso ndi mphunzitsi wa malamulo pa sukulu ya ukachenjende ya Chancellor, Professor Edge Kanyongolo wapempha boma kuti libwezeretse ubale womwe unasokonekera pakati pa boma la...
View ArticlePolisi ya Kanengo Iyenda Ulendo Wandawala Pofuna Kuzindikiritsa Anthu za...
Ngati njira imodzi yotenga nawo gawo pa ntchito yothana ndi m`chitidwe wopha anthu a mtundu wa chi alubino, apolisi a Kanengomu m’zinda wa Lilongwe akonza ulendo wa ndawala womwe cholinga chake...
View ArticleAlshabaab Yapha Asilikali Makumi Anayi a AU ku Somalia
Gulu la zigawenga la Al-Shabaab lati lapha asilikali okwana makumi anayi pachiwembu chomwe linachita kumalo a asilikali a African Union m`chigawo chapakati pa dziko la Somalia. Bungwe la...
View ArticleMgwirizano wa Apolisi ndi Amalonda Ungapititse Patsogolo Chitetezo cha Dziko...
Chitetezo cha dziko lino ati chingalimbikitsidwe ngati pali ubale wabwino pakati pa apolisi ndi anthu amalonda. Wachiwiri kwa mkulu wa apolisi ya Bvumbwe , SupretendantMoses Katanda walankhula izi ndi...
View ArticleAbungwe la Amayi Akatolika Akonzekere Bwino Msonkhano wa Padziko Lonse
Amayi ampingo wakatolika mdziko muno awapempha akuti adzipeleke pa ntchito yokonzekera msonkhano wawo wapaziko lonse umene udzachike mwezi wa September m’dziko muno. Msonkhanowu ndi wa amayi pa dziko...
View ArticleMOAM Ipempha Boma Liwunikenso Misonkho
Bungwe la eni minibus m`dziko muno la Minbus Owners Association of Malawi(MOAM) lapempha boma kuti liwunikenso misonkho pofuna kuti ikhale yokomera anthu ochita malonda ang’onoang’ono omwe ambiri...
View ArticleMkulu wa Bungwe la Community of Saint Egidio Mdziko Muno Wamwalira
Bungwe la Community of Saint Egidio lati lili mkati mokonza dongosolo la mwambo woyika m'manda yemwe anali mkulu wa bungweli m'dziko muno a Ellard Alumando. Malemu-yi Ellard Alumando anamwalira masiku...
View ArticleAchinyamata Azigwiritsa Bwino Ntchito Luso la Makono Pofalitsa Uthenga wa...
Achinyamata a bungwe la Young Christian Workers (YCW) mumpingo wa katolika awalangiza kuti azigwiritsa bwino ntchito maluso atsopano omwe akubwera mdziko muno monga ma computer komanso internet...
View ArticleMa Episkopi Apempha Mzika Kuti Zipempherere Dziko la Nigeria Pofuna Kuthetsa...
Bungwe la ma episkopi mdziko la Nigeria la Catholic Bishops’ Conference of Nigeria lapempha mzika za dzikolo kuti zipitilize kupemphelera dzikolo pofuna kuthana ndi mchitidwe wa katangale komanso...
View ArticleBoma Lati Lipereka Chilango Chokhwima kwa Opezeka ndi Mlandu Wopha ma Alubino
M’tsogoleri wa dziko lino Professor Arthur Peter Mutharika wati boma lake lionetsetsa kuti aliyense wopezeka ndi mulandu wakupha kapena kuchitira nkhanza anthu a mtundu wa chi Alubino m’dziko muno...
View ArticleEye Of The Child Ikhazikitsa Bukhu Lozindikiritsa Mavuto Omwe Ana Amakumana Nawo
Bungwe la Eye ofthe Child m’dziko muno lalemba bukhu lomwe lili ndi mfundo zothandiza kuzindikira mavuto omwe ana amakumana nawo monga kugwililidwa mosavuta. Polankhula ndi Radio Maria Malawi, mkulu...
View ArticleDziko la Malawi Lichita Mwambo wa Tsiku Loganizira Mchitidwe Wogwiritsa Ana...
Dziko la Malawi lachisanu lichita mwambo wa tsiku loganizira m’chitidwe woyipa wogwilitsa ntchito ana (World Day Against Child Labour). Dziko la Malawi lidzachita mwambowu pogwilizana ndi mayiko pa...
View ArticleMfumu Kachule Ikulimbikitsa Maphunziro Kwa Ana Mdera Lake
Mfumu Kachule ya m’dera la mfumu yayikulu Kachere m’boma laDedza yati ipitiliza kudzipeleka pa chisamaliro ndi chitetezo cha ana a m’dera lake ndi cholinga choti azikhala ndi kukula ndi makhalidwe...
View ArticleBungwe la Episcopal Conference of Malawi Liri ndi Mlembi Watsopano.
Mlembi watsopano wabungwe la maepiskopi mdziko muno la Episcopal conference of Malawi Bambo Henry Saindi ati apitiliza kudzipereka potumikira Mulungu pogwiritsa ntchito mphatso zomwe ali nazo pofunanso...
View Article