Zigawenga Zina za Boko Haram Zikufera ku Ndende
Anthu omwe anamangidwa kaamba kowaganizira kuti ali mgulu la Boko Haram ati akufa kundende kaamba ka matenda osiyanasiyana monga onyetchera. Malinga ndi lipoti lomwe bungwe la Amnersty...
View ArticleChipatala cha Praises Chikupereka Thandizo Laulere
Chipatala cha Praises chati chakonza dongosolo lopeleka thandizo lina la zachipatala mwaulele pofuna kuthandiza anthu a m’dera lomwe kuli chipatalachi. Mkulu wa chipatalachi Dr. Nelson Munthali wanena...
View ArticleChipani cha Umodzi Chalangiza President Asavomereze Bilu ya Malo
Chipani chotsutsa boma cha umodzi chalangiza m’tsogoleri wa dziko lino Professor Arthur Peter Mutharikakuti asavomereze Bilo yatsopano yokhudza malo yomwe nyumba ya malamulo yakhala ikukambirana....
View ArticleSukulu ya St. John Nursery Yati Ipitirira Kutukula Maphunziro
Sukulu ya m’mera mpoyamba ya St. John m’boma la Mangochi yati ipitiriza kudzipeleka pa ntchito zokweza maphunziro a ana a m’dera la Senior Chief Chimwala ndi madera ena m’boma la Mangochi. A Martin...
View ArticleBambo Chimbwanya Apempha Achinyamata Adzipereke Pa Utumiki
Achinyamata mu mpingo wakatolika awapempha kuti adzipereke polowa m’mautumiki osiyanasiyana opezeka mu mpingowu. Bambo Medrick Chimbwanya anena izi ku Parish ya Ulongwe m’boma la Balaka pomwe amachita...
View ArticleDziko la Morocco Likufuna Lilowenso mu AU
Dziko la Morocco latumiza thumwi kuti zikambirane ndi atsogoleri a abungwe la mgwirizano wa maiko a mu Africa la African Union(AU) kuti dzikolo lilowenso m`gulu la AU patatha 32 dzikola Morocco...
View ArticlePapa Ndiwokhudzidwa Ndi Imfa Ya Anthu 80 Mdziko La France
M’tsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Fransisko wati ndi wokhudzidwa ndi imfa ya anthu 80 omwe anaphedwa pa chiwembu china chomwe chachitikanso m’dziko la France sabata ikongothayi. Pa...
View ArticleApempha Aphunzitsi Akhale Olimbikira Ntchito
Aphunzitsi achikatolika mu dayosizi ya Dedza awapempha kuti akhale olimbika ndi okhulupilika pa ntchito yawo. Mlembi wa za maphunziro msukulu za chitolika mu dayosizi-yo a Zakaliya Pengapenga ndi omwe...
View ArticleMafumu Ena Sakukondwa ndi Bilu ya Malo
Pomwe aphungu akunyumba ya malamulo avomereza bilo yokhudza malo lachinayi pa 13 July 2016, Anthu ena ati sakugwirizana ndi biloyi ponena kuti ithetsa ufumu chifukwa popanda malo ntchito ya ufumu...
View ArticleCADECOM Yapempha Atolankhani Afalitse Mauthenga a Ndondomeko Zomwe Boma...
Bungwe la zachitukuko mu mpingo wakatolika la Catholic Development Commission in Malawi (CADECOM)lapempha atolankhani mdziko muno kuti atenge gawo lalikulu pofalitsa mauthenga a ndondomeko...
View ArticleUsi Wapempha Mutharika Asasainire Bilu ya Malo
Katswiri pankhani ya zisudzo m`dziko muno Michael Usi, wapempha mtsogoleri wadziko lino ProfessorArthurPeter Mutharika asasainile lamulo latsopano lokhudza malo kamba koti a Malawi ambiri kuphatikizapo...
View ArticleAna Omwe Anagwidwa ndi Gulu la Book Haram Akhudzidwa ndi Matenda
Ana pafupifupi 1 Million omwe ali ku malo a gulu la zigawenga za Boko Haram m’dziko la Nigeria akuti akhudzidwa ndi matenda osiyanasiyana kumalowa. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC ngati thandizo...
View ArticleOphunzira a Chanco Ati Apitiriza Kunyanyala Maphunziro
Ophunzira pa sukulu ya ukachenjede ya Chancellor ati apitiliza kunyanyala maphunziro awo pokhapokha akulu-akulu a mu khonsolo yowona za maphunziro pa sukulu-yi (University Council) atabwera ndi...
View ArticleAnthu Awiri Afa pa Ngozi ya pa Msewu Mboma la Zomba
Anthu awiri afa ndipo ena 33 avulala m’boma la Zomba galimoto lomwe anakwera litagubuduzika pa malo ena otchedwa Chikupila m’bomalo. Malinga ndi wofalitsa nkhani za apolisi mchigawo chakuvuma...
View ArticleBungwe la APAM Silikuwona Kusintha
Bungwe lomenyera ufulu wa anthu a chi alubino m’dziko muno laAssociation of People with Albinism(APAM) lati ngakhale boma likutsindika kuti lithana ndi mchitidwe wosembetsa ndi kupha anthu a...
View ArticleSakorzy Wadzudzula Boma Polephera Kupereka Chitetezo Chokwanira
Mtsogoleri wakale wa dziko la France a Nicholus Sarkozy wadzudzula boma la dzikolo kamba kolephera kupereka chitetezo chokwanira mdzikolo. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC mtsogoleri wakaleyu...
View ArticleAmbuye Warduni Ati ndi Okhudzidwa ndi Mavuto Omwe Anthu Othawa Kwao Akukumana...
Episkopi wa mpingo wakatolika mdziko la Iraq, Ambuye Shlemon Warduni wati ndi okhudzidwa ndi mavuto omwe anthu othawa kwao akukumana nawo m’malo omwe akukhala. Malinga ndi malipoti a Catholic Culture,...
View ArticleAmalawi Aleke Kudalira Ulimi Wamakolo – Mvula
Anthu mdziko muno awapempha kuti aleke kudalira ulimi wa makolo wodalira khasu komanso mvula ndipo m’malo mwake azigwiritsa ntchito njira za makono pa ulimi. Mmodzi mwa amkhalakale pa ndale mdziko muno...
View ArticleAsilikali 17 Aphedwa Mdziko la Mali
Asilikali pafupifupi 17 aphedwa ndipo ena makumi atatu 30 avulazidwa mu mzinda wa Nampala mdziko la Mali potsatira chiwembu china chomwe chachitika kumalo komwe asilikaliwa amakhala. Malinga ndi...
View ArticleMa Episkopi Adzudzula Apolisi Mdziko la Phillipines
Bungwe la maepiskopi a mpingo wakatolika mdziko la Philippines la Catholic Bishops Conference of the Philippines ladzudzula apolisi mdzikolo kamba ka mchitidwe wakupha anthu a mdzikolo omwe...
View Article