Boma la Iraq Lalanda Nyumba Momwe Mumakhala Zigawenga za Islamic State
Boma la dziko la Iraq lalanda nyumba yake yomwe mumapezeka zigawenga za chisilamu za Islamic State mu mzinda wa Fallujah mdzikolo. Malinga ndi malipoti a wailesi ya BBC akuluakulu a gulu la zigawengazi...
View ArticleChipatala cha Dedza Chapempha Mafumu Kuti Alimbikitse Uchembere Wabwino
Chipatala cha boma cha Dedza chapempha mafumu kuti apitilize kulimbikitsa amayi oyembekezera kuti azichilira ku chipatala. Ofalitsa nkhani za chipatalachi, a Alnod Ndalira, wanena izi potsekulira...
View ArticleBungwe la YODEP Likukhazikitsa Mabungwe Othana ndi Nkhanza kwa Ana ndi Amayi
Bungwe la Youth Development and Productivity (YODEP)m’boma la Zomba lati ntchito yokhazikitsa ma bungwe a abambo omwe akhale akuteteza amayi ndi ana ku nkhanza zosiyanasiyana ikuyenda bwino. Mmodzi...
View ArticleAmbuye Msusa Ayamikira Akhristu a Parishi ya Bvumbwe
Akhristu a mpingo wakatolika mu arkidayosizi ya Blantyre awayamikira kamba kochilimika pa zampingo wodzidalira pomwe akugwira ntchito za chitukuko m`maparishi awo. Arkiepiskopi wa dayosiziyi, Ambuye...
View ArticleAmbuye Stima Ayamikira Ophunzira Akale a Sukulu ya St. Paul The Apostle
Anthu omwe anaphunzira pa seminale yaying’ono ya St. Paul the Apostle, mu dayosizi ya Mangochi ya mpingo wakatolika, awayamikira kamba kotengapo gawo popititsa patsogolo chitukuko cha dayosiziyi....
View ArticleBungwe la FAWO Lati Amayi Amasiye Akhale Odzidalira
Bungwe lomenyela ufulu wa amayi ndi ana amasiye mdziko muno la Foundation for Widows and Orphans (FAWO) lati nthawi yakwana yoti amayi amasiye akhale odziyimira pawokha pa nkhani za chuma. Polankhula...
View ArticlePapa Wati Chilango cha Kupha ndi Chosayenera
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Fransisko wati chilango chakupha ndi chosayenera kamba koti munthu aliyense ali ndi ufulu wokhala ndi moyo. Papa amalankhula izi potsatira msonkhano...
View ArticleNyumba Zosindikiza Ndi Kuwulutsa Nkhani Zizilemba Mwaukadaulo Nkhani Zokhudza...
Nyumba zotsindikiza ndi kuwulutsa nkhani mdziko muno azilimbikitsa kuti zizifufuza mokwanira komanso kulemba mwaukadaulo nkhani zokhudza anthu olumala. Wachiwiri kwa mkulu wa nthambi yophunzitsa...
View ArticlePRO-LIFE Yati Kupha ma Alubino ndi Kutsutsana ndi Cholinga cha Mulungu
Bungwe loteteza miyoyo ya anthu la mpingo wa katolika la PRO-LIFE lati kupha anthu a mtundu wa chialubino ndi kutsutsana ndi cholinga cha Mulungu kaamba koti iye analenga munthu aliyense m’chifaniziro...
View ArticleMpingo Wakatolika Wati Pasakhale Lamulo Lakupha Munthu Wopha ma Alubino
Mpingo wa katolika mdziko muno wati ukugwirizana ndi ganizo la boma loti pasakhale lamulo lakupha munthu wopezeka olakwa pa mlandu wosowetsa komanso kupha anthu a mtundu wa chialubino. Mlembi wa mkulu...
View ArticleYCW Ikutolera Thandizo la Seminale Ya St. Peters
Bungwe la achinyamata mu mpingo wakatolika m’dziko muno la Young Christian Workers (YCW) lati likutolera thandizo pofuna kuthandiza seminale yaikulu ya St. Peters mu dayosizi ya Zomba yomwe padakali...
View ArticleCCJP Yadzudzula Aphungu Ena Kamba Kosamapita Kunyumba Ya Malamulo
Bungwe la mpingo wakatolika la chilungamo ndi mtendere la Catholic Commission for Justice and Peace (CCJP) ladzudzula aphungu a ku nyumba ya malamulo kamba ka chisankho chomwe ena mwa iwo akuchita...
View ArticleBoma Latsimikiza Kuti Zitukuko Zitha Posachedwa M’boma La Machinga
Anthu a m’madera a mafumu a Chiwalo komanso Kapoloma m’boma la Machinga awatsimikizira kuti zitukuko zomwe zikugwiridwa m’madera awo zifika kumapeto posachedwapa. Nthandizi wa nduna ya za nyumba ndi...
View ArticleTEVETA Yati Ntchito Zake Zotolera Msonkho Ziyamba Kuyenda Bwino
Bungwe la Technical Interprenual Vocational Education and Training Authority (TIVETA) lati ntchito yake yotolera misonkho iyamba kuyenda bwino kaamba ka mgwirizano omwe bungweli wasayinirana ndi bungwe...
View ArticleAtumiki a Radio Maria Malawi Awapempha Akhale Olimbikira Pofalitsa Uthenga wa...
Anthu omwe amagwira ntchito modzipereka ku Radio Maria Malawi awalimbikitsa kuti asamabwelere m’mbuyo pomwe akukumana ndi zovuta pa nthawi yomwe akutumikira. Bambo Edwin Lambulira alankhula izi...
View ArticleMsonkhano wa PMS Watha Lachisanu
M’sonkhano waukulu wa masiku anayi wa atsogoleri oyendetsa ma bungwe a utumiki wa a Papa m’ma dayosizi onse ampingo wakatolika mdziko muno watha lachisanu. Polankhula pambuyo pa msonkhanowu omwe...
View ArticlePapa Walimbikitsa Ubale wa Mpingo wa Katolika ndi Orthodox
Mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse Papa Fransisko wapempha kuti mgwirizano omwe ulipo pakati pa mpingowu ndi mpingo wa Orthodox upitilire kuyenda bwino. Papa amalankhula izi la mulungu...
View ArticleMpingo Wa Anglican Wadzodza Ansembe Atatu
Mpingo wa Anglican mu dayosizi ya Upper Shire loweruka wadzoza madikoni atatu kukhala ansembe. Polankhula pa mwambowu Episkopi wa dayosiziyi Ambuye Brighton Vita Malasa ayamikira ansembe atsopanowa...
View ArticleZigawenga za Boko Haram Zapha Anthu Pafupifupi 150 Sabata Ino
Zigawenga za Boko Haram zapha anthu pafupifupi zana limodzi ndi makumi asanu sabata ino mchigawo cha Borno mdziko la Nigeria. Anthu omwe awona izi zikuchitika awuza wailesi ya BBC kuti anthu a mfuti...
View ArticleMpingo wa Anglican Ukuphunzitsa Anthu za Kuyipa Kozembetsa ndi Kupha ma Alubino
Mpingo wa Anglican mdziko muno wati wayamba ntchito yophunzizitsa ndi kudziwitsa anthu za kuyipa kwa mchitidwe wopha ndi kuzembetsa anthu a mtundu wa chi alubino womwe padakali pano wakula mdziko muno....
View Article