Canon Opuma wa Mpingo wa Anglican Atisiya
A ku likulu la chipani cha Anglican mu dayosizi ya Upper Shire mdziko muno akulengeza za imfa ya Canon Absalom Kasiya opuma omwe amwalira lero pa ngozi ya galimoto ku Liwonde. Maliro akulilira ku...
View ArticleSister Moyo Amwalira
A ku likulu la chipani cha Rosarian Sisters mu dayosizi ya Mzuzu alengeza za imfa ya Sister Maria Rita Moyo. Sister Moyo anabadwa mu chaka cha 1948 ndipo anachita malumbiro awo oyamba mu chipanichi pa...
View ArticleAlamulidwa Kupereka 5 Sauzande Kamba Kopezeka Akugulitsa Malonda Malo Osayenera
Bwalo la milandu la Midima ku Limbe mu mzinda wa Blantyre lalamula anthu khumi ndi awiri 12 kuti apereke chindaputsa cha ndalama zokwana 5 sauzande aliyense kaamba kopezeka akuchita malonda pa malo...
View ArticlePapa Ayikiza M’mapemphero Anthui Okhuzidwa ndi Chiwembu Mdziko la Turkey
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Fransisko anapempha mphindi yokhala chete pofuna kuyikiza mmapemphero anthu onse omwe akhudzidwa ndi chiwembu chomwe chachitika pa bwalo lina la...
View ArticleRadio Maria Malawi Yapempha Anthu Akwaniritse Malonjezo awo a Mariatona
Abwenzi a Radio Maria Malawi komanso anthu akufuna kwabwino awapempha kuti akwaniritse lonjezo lawo lothandiza wailesiyi pamene Mariatona wa chaka chino akupita kumapeto. Wapampando wa Mariatona ya...
View ArticleDziko la Turkey Lakhazikitsa Lachinayi Ngati Tsiku Lapadera
Dziko la Turkey lakhazikitsa tsiku la lachinayi pa 30 June, 2016 kukhala lapadera mdzikolo pofuna kukhudza maliro a anthu 42 omwe afa pa chiwembu chomwe chachitikira pa bwalo la ndege mu mzinda wa...
View ArticleMphunzitsi Amangidwa Kamba Kogwilirira Mwana wa Sukulu
Apolisi m’boma la Ntchisi amanga mphunzitsi wa pa sukulu ina ya pulayimale kamba kogwirira ophunzira wina pa sukulupo wa zaka 16 zakubadwa. Mneneri wa apolisi m’bomalo Sergent Gladson M’bumpha...
View ArticleZokonzekera Kutsekera Radio Maria Malawi Mariatona Zili Mchimake
Pali chiyembekezo chakuti mwambo wotsekera Radio Maria Mariatona ku phiri la Michiru ku Arkdayosizi ya Blantyre ya mpingo wakatolika loweruka ukhala wopambamba kamba koti zonse zokonzera tsikuli ati...
View ArticleMsonkhano Waukulu Wachiri Wa ECM Watha
Msonkhano waukulu wachiwiri wa pachaka wa ma episkopi a mpingo wakatolika mdziko muno watha lero ku likulu la mpingowu mu mzinda wa Lilongwe. Polankhula ndi Radio Maria Malawi pambuyo pa msonkhanowu...
View ArticleWoyimira Anthu pa Milandu Wapezeka Atafa Mdziko la Kenya
Loya wina yemwe amayimilira munthu wina pamlandu woti apolisi m`dziko la Kenyaakumachitira nkhanza anthu m`dzikolo wapezeka atafa munzinda wa Nairobi m`dzikolo. Loyayu, Willie Kimani wa zaka 32,...
View ArticleMa Episkopi Mdziko la South Africa Adzudzula Ziwawa Mdzikolo
Maepiskopi a mpingo wakatolika mdziko la South Africa adzudzula mchitidwe wa ziwawa omwe ukuchitika mdzikolo potsatira chisankho cha makhansala chomwe chikuyembekezeka kuchitika mwezi wa mawa. Malinga...
View ArticleChitukuko Chingapite Patsogolo Ngati Adindo ndi Mzika Akulumikizana
Kulumikizana pa nkhani za chitukuko cha m’madera pakati pa adindo komanso mzika ati ndi njira yokhayo yomwe ingapititse patsogolo chitukuko cha dziko lino. Wachiwiri kwa mfumu ya mzinda wa Blantyre, a...
View ArticleKatsonga Wapempha Akhristu Azithandiza Radio Maria Malawi
Akhristu a mpingo wakatolika m`dziko muno awapempha adzitenga gawo lalikulu pothandiza Radio Maria Malawi. Yemwe anali mlendo wolemekezeka pa mwambo wotsekera ntchito yotolera thandizo la wailesiyi...
View ArticleAmuna Awiri Amangidwa Kamba Kobera Mayeso a MSCE
Amuna awiri ali m’manja mwa apolisi atapezeka akubera mayeso a fomu 4 m’boma la Balaka. M’modzi mwa amunawa a Joseph Makiyi omwe amagwira ntchito ku Prison Fellowship anatenga tchuthi kuntchito kwawo...
View ArticleAlamulidwa Kukakhala ku Ndende Zaka 10 Kamba Kopereka Mimba kwa Mtsikana...
Mwamuna wina wa zaka 18 zakubadwa amulamula kuti akakhale kundende ndikukagwira ntchito ya kalavula gaga kwa zaka khumi (10) kamba kopereka mimba kwa msungwana wa zaka 15 m’boma la Mwanza. Mneneri wa...
View ArticlePapa Wapepesa Anthu Amene Akhuzidwa Ndi Chiwembu Mdziko la Bangladesh
Mtsogoleri wa mpingo wakatolika pa dziko lonse Papa Fransisko wapereka uthenga wa chipepeso kwa anthu omwe akhudzidwa ndi chiwembu chomwe chaphetsa anthu makumi awiri mu mzinda wa Dhaka mdziko la...
View ArticleMutharika Wati Atukula Mzinda wa Zomba
President wa dziko lino Professor Arthur Peter Mutharika wati boma lake likhazikitsa zitukuko zosiyanasiyana mu mzinda wa Zomba ndi cholinga choti mzindawu udzifanafana ndi mizinda ina ya mdziko...
View ArticlePapa Francisco wati Ntchito za Migodi Zikomere Anthu Okhala Moyandikana ndi...
Mtsogoleri wampingo wakatolika padziko lonse Papa Francisco,wapempha mayiko kuti adziwonetsetsa kuti ntchito za migodi zomwe zikuchitika mmayiko awo zikuchitika mokomera anthu onse maka oyandikana ndi...
View ArticleAtsogoleri a Zipani Zotsutsa Sapikisana Nawo pa Chisankho cha Pulezidenti...
Pamene chisankho cha pulezidenti mdziko la Burundi chikuyembekezeka kuchitika lachiwiri, mtsogoleri wa dzikolo Pierre Nkurunziza ati akuyembekezeka kupambana pa chisankhochi zomwe zichititse kuti...
View ArticleAmbuye Musikuwa Apempha Asisiteri Akhale Odzipereka pa Utumiki
Episkopi wa dayosizi ya Chikwawa ya mpingo wakatolika Ambuye Peter Musikuwa wapempha asisteri kuti azikhala odzipereka pa utumiki wao. Ambuye Musikuwa alankhula izi pa mwambo wa malumbiro a ku nthawi...
View Article